Isaiah 14 (BOGWICC)

1 Yehova adzachitira chifundo Yakobo;adzasankhanso Israelindi kuwalola kuti akhalenso mʼdziko lawo.Alendo adzabwera kudzakhala nawondi kudziphatika okha kukhala ngati a mʼnyumba ya Yakobo. 2 Anthu a mitundu ina adzaperekeza a Israeliku dziko lawo.Tsono Aisraeli adzasandutsa anthu a mitundu ina ajakukhala antchito awo aamuna ndi aakazi mʼdziko la Yehova.Ndiye kuti Aisraeli adzasandutsa akapolo anthu amene kale anali ambuye awo.Iwo adzasandutsa akapolo anthu amene kale ankawalamulira ndi kuwazunza. 3 Yehova akadzakupumitsani ku zowawa ndi mavuto, ndiponso kuntchito yakalavulagaga imene ankakugwiritsani, 4 mudzayankhula monyogodola mfumu ya Babuloni kuti,Wopsinja uja watha!Ukali wake uja watha! 5 Yehova wathyola chikwapu cha anthu oyipa,Iye waphwanya ndodo ya olamulira. 6 Mfumu ya ku Babuloni inkakantha mitundu ya anthu mwaukalipowamenya kosalekeza,Iyo inkagonjetsa anthu a mitundu ina mwaukalindikuwazunza kosalekeza. 7 Koma tsopano mayiko onse ali pa mpumulo ndi pa mtendere;ndipo akuyimba mokondwa. 8 Ngakhale mitengo ya payini ndi mikungudza ya ku Lebanoniikuyimba za iwe mokondwa ndipo ikuti,“Chigwetsedwere chako pansi,palibe wina anabwera kudzatigwetsa.” 9 Ku manda kwatekesekakuti akulandire ukamabwera;mizimu ya anthu akufa, aja amene anali atsogoleria dziko lapansi, yadzutsidwa.Onse amene anali mafumu a mitundu ya anthuayimiritsidwa pa mipando yawo. 10 Onse adzayankha;adzanena kwa iwe kuti,“Iwenso watheratu mphamvu ngati ife;Iwe wafanana ndi ife.” 11 Ulemerero wako wonse walowa mʼmanda,pamodzi ndi nyimbo za azeze ako;mphutsi zayalana pogona pakondipo chofunda chako ndi nyongolotsi. 12 Wagwa pansi bwanji kuchoka kumwamba,iwe nthanda, mwana wa mʼbandakucha!Wagwetsedwa pansi pa dziko lapansi,Iwe amene unagonjetsapo mitundu ya anthu! 13 Mu mtima mwako unkanena kuti,“Ndidzakwera mpaka kumwamba;ndidzakhazika mpando wanga waufumupamwamba pa nyenyezi za Mulungu;ndidzakhala pa mpando waufumu pa phiri losonkhanirako,pamwamba penipeni pa phiri la kumpoto. 14 Ndidzakwera pamwamba pa mitambo;ndidzafanana ndi Wammwambamwamba.” 15 Koma watsitsidwa mʼmandapansi penipeni pa dzenje. 16 Anthu akufa adzakupenyetsetsanadzamalingalira za iwe nʼkumati,“Kodi uyu ndi munthu uja anagwedeza dziko lapansindi kunjenjemeretsa maufumu, 17 munthu amene anasandutsa dziko lonse chipululu,amene anagwetsa mizinda yakendipo sankalola kuti anthu ogwidwa abwerere kwawo?” 18 Mafumu onse a mitundu ya anthu akugona mwaulemualiyense mʼmanda akeake. 19 Koma iwe watayidwa kunja kwa manda ako,ngati nthambi yowola ndi yonyansa.Mtembo wako waphimbidwa ndi anthu ophedwa;amene anabayidwa ndi lupanga,anatsikira mʼdzenje lamiyalangati mtembo woponderezedwa. 20 Sudzayikidwa nawo mʼmanda mwaulemu,chifukwa unawononga dziko lakondi kupha anthu ako. Zidzukulu za anthu oyipasizidzakumbukika nʼpangʼono pomwe. 21 Konzani malo woti muphere ana ake aamunachifukwa cha machimo a makolo awo;kuti angadzuke ndi kulanda dziko lapansindi kulidzaza dziko lonselo ndi mizinda yawo. 22 Yehova Wamphamvuzonse akuti,“Ine ndidzathira nkhondo mzinda wa Babuloni.Ndidzachotseratu mu Babuloni dzina lake ndi onse otsaliramo.Ndiye kuti sipadzakhala ana kapena zidzukulu,”akutero Yehova. 23 “Ndidzawusandutsa mzindawo malo okhalamo anungundiponso dambo lamatope;ndidzawusesa ndi tsache lowononga,”akutero Yehova Wamphamvuzonse. 24 Yehova Wamphamvuzonse walumbira kuti,“Ndithudi, monga ndaganizira ndidzachitadi choncho,ndipo monga momwe ndatsimikizira zidzakhala momwemo ndithu. 25 Ndidzawawononga Asiriya mʼdziko langa;ndidzawapondereza ndi mapazi pa mapiri anga;ndidzachotsa goli lawo pa anthu anga,ndipo ndidzachotsa katundu wawo pa mapewa awo.” 26 Izi ndizo ndakonza kuti zichitike pa dziko lonse lapansi,ndatambasula dzanja pa anthu a mitundu yonse. 27 Pakuti Yehova Wamphamvuzonse watsimikiza, ndipo ndani angamuletse?Dzanja lake latambasulidwa ndipo ndani angalibweze? 28 Uthenga uwu unabwera chaka chimene mfumu Ahazi anamwalira: 29 Musakondwere inu Afilisti nonsekuti Asiriya amene anali ngati ndodo yokukanthani anathedwa;chifukwa kuchokera ku njoka yomweyi (mfumu ya Aasiriya) mudzatuluka mphiri,ndipo chipatso chake chidzakhala njoka yaliwiro ndiponso yaululu. 30 Osaukitsitsa adzapeza chakudyandipo amphawi adzakhala mwamtendere.Koma anthu ako ndidzawawononga ndi njala,ndipo njalayo idzapha ngakhale opulumuka ako. 31 Lirani kwambiri, anthu a pa chipata! Fuwulani kwambiri, anthu a mu mzinda!Njenjemerani ndi mantha, inu Afilisti nonse!Mtambo wa utsi ukuchokera kumpoto,ndipo palibe wamantha pakati pa ankhondo ake. 32 Kodi tidzawayankha chiyaniamithenga a ku Filisitiya?“Yehova wakhazikitsa Ziyoni,ndipo mu mzinda wakewu, anthu ozunzika apeza populumukira.”

In Other Versions

Isaiah 14 in the ANGEFD

Isaiah 14 in the ANTPNG2D

Isaiah 14 in the AS21

Isaiah 14 in the BAGH

Isaiah 14 in the BBPNG

Isaiah 14 in the BBT1E

Isaiah 14 in the BDS

Isaiah 14 in the BEV

Isaiah 14 in the BHAD

Isaiah 14 in the BIB

Isaiah 14 in the BLPT

Isaiah 14 in the BNT

Isaiah 14 in the BNTABOOT

Isaiah 14 in the BNTLV

Isaiah 14 in the BOATCB

Isaiah 14 in the BOATCB2

Isaiah 14 in the BOBCV

Isaiah 14 in the BOCNT

Isaiah 14 in the BOECS

Isaiah 14 in the BOHCB

Isaiah 14 in the BOHCV

Isaiah 14 in the BOHLNT

Isaiah 14 in the BOHNTLTAL

Isaiah 14 in the BOICB

Isaiah 14 in the BOILNTAP

Isaiah 14 in the BOITCV

Isaiah 14 in the BOKCV

Isaiah 14 in the BOKCV2

Isaiah 14 in the BOKHWOG

Isaiah 14 in the BOKSSV

Isaiah 14 in the BOLCB

Isaiah 14 in the BOLCB2

Isaiah 14 in the BOMCV

Isaiah 14 in the BONAV

Isaiah 14 in the BONCB

Isaiah 14 in the BONLT

Isaiah 14 in the BONUT2

Isaiah 14 in the BOPLNT

Isaiah 14 in the BOSCB

Isaiah 14 in the BOSNC

Isaiah 14 in the BOTLNT

Isaiah 14 in the BOVCB

Isaiah 14 in the BOYCB

Isaiah 14 in the BPBB

Isaiah 14 in the BPH

Isaiah 14 in the BSB

Isaiah 14 in the CCB

Isaiah 14 in the CUV

Isaiah 14 in the CUVS

Isaiah 14 in the DBT

Isaiah 14 in the DGDNT

Isaiah 14 in the DHNT

Isaiah 14 in the DNT

Isaiah 14 in the ELBE

Isaiah 14 in the EMTV

Isaiah 14 in the ESV

Isaiah 14 in the FBV

Isaiah 14 in the FEB

Isaiah 14 in the GGMNT

Isaiah 14 in the GNT

Isaiah 14 in the HARY

Isaiah 14 in the HNT

Isaiah 14 in the IRVA

Isaiah 14 in the IRVB

Isaiah 14 in the IRVG

Isaiah 14 in the IRVH

Isaiah 14 in the IRVK

Isaiah 14 in the IRVM

Isaiah 14 in the IRVM2

Isaiah 14 in the IRVO

Isaiah 14 in the IRVP

Isaiah 14 in the IRVT

Isaiah 14 in the IRVT2

Isaiah 14 in the IRVU

Isaiah 14 in the ISVN

Isaiah 14 in the JSNT

Isaiah 14 in the KAPI

Isaiah 14 in the KBT1ETNIK

Isaiah 14 in the KBV

Isaiah 14 in the KJV

Isaiah 14 in the KNFD

Isaiah 14 in the LBA

Isaiah 14 in the LBLA

Isaiah 14 in the LNT

Isaiah 14 in the LSV

Isaiah 14 in the MAAL

Isaiah 14 in the MBV

Isaiah 14 in the MBV2

Isaiah 14 in the MHNT

Isaiah 14 in the MKNFD

Isaiah 14 in the MNG

Isaiah 14 in the MNT

Isaiah 14 in the MNT2

Isaiah 14 in the MRS1T

Isaiah 14 in the NAA

Isaiah 14 in the NASB

Isaiah 14 in the NBLA

Isaiah 14 in the NBS

Isaiah 14 in the NBVTP

Isaiah 14 in the NET2

Isaiah 14 in the NIV11

Isaiah 14 in the NNT

Isaiah 14 in the NNT2

Isaiah 14 in the NNT3

Isaiah 14 in the PDDPT

Isaiah 14 in the PFNT

Isaiah 14 in the RMNT

Isaiah 14 in the SBIAS

Isaiah 14 in the SBIBS

Isaiah 14 in the SBIBS2

Isaiah 14 in the SBICS

Isaiah 14 in the SBIDS

Isaiah 14 in the SBIGS

Isaiah 14 in the SBIHS

Isaiah 14 in the SBIIS

Isaiah 14 in the SBIIS2

Isaiah 14 in the SBIIS3

Isaiah 14 in the SBIKS

Isaiah 14 in the SBIKS2

Isaiah 14 in the SBIMS

Isaiah 14 in the SBIOS

Isaiah 14 in the SBIPS

Isaiah 14 in the SBISS

Isaiah 14 in the SBITS

Isaiah 14 in the SBITS2

Isaiah 14 in the SBITS3

Isaiah 14 in the SBITS4

Isaiah 14 in the SBIUS

Isaiah 14 in the SBIVS

Isaiah 14 in the SBT

Isaiah 14 in the SBT1E

Isaiah 14 in the SCHL

Isaiah 14 in the SNT

Isaiah 14 in the SUSU

Isaiah 14 in the SUSU2

Isaiah 14 in the SYNO

Isaiah 14 in the TBIAOTANT

Isaiah 14 in the TBT1E

Isaiah 14 in the TBT1E2

Isaiah 14 in the TFTIP

Isaiah 14 in the TFTU

Isaiah 14 in the TGNTATF3T

Isaiah 14 in the THAI

Isaiah 14 in the TNFD

Isaiah 14 in the TNT

Isaiah 14 in the TNTIK

Isaiah 14 in the TNTIL

Isaiah 14 in the TNTIN

Isaiah 14 in the TNTIP

Isaiah 14 in the TNTIZ

Isaiah 14 in the TOMA

Isaiah 14 in the TTENT

Isaiah 14 in the UBG

Isaiah 14 in the UGV

Isaiah 14 in the UGV2

Isaiah 14 in the UGV3

Isaiah 14 in the VBL

Isaiah 14 in the VDCC

Isaiah 14 in the YALU

Isaiah 14 in the YAPE

Isaiah 14 in the YBVTP

Isaiah 14 in the ZBP