Isaiah 2 (BOGWICC)
1 Nazi zinthu zokhudza Yuda ndi Yerusalemu, zimene Yesaya mwana wa Amozi anaziona mʼmasomphenya: 2 Mʼmasiku otsiriza,phiri la Nyumba ya Yehova adzalikhazikitsakukhala lalitali kuposa mapiri ena onse,lidzaonekera pamwamba pa mapiri ena onse,ndipo mayiko onse adzathamangira kumeneko. 3 Anthu ambiri adzabwera ndikunena kuti,“Tiyeni tikwere ku phiri la Yehova,ku nyumba ya Mulungu wa Yakobo.Iye adzatiphunzitsa njira zake,ndipo tidzayenda mʼnjira zakezo.”Malangizo adzachokera ku Ziyoni,mawu a Yehova adzachokera ku Yerusalemu. 4 Iye adzaweruza pakati pa mayiko,ndipo adzathetsa kusamvana pakati pa anthu ambiri.Anthuwo adzasandutsa malupanga awo kukhala makasundiponso mikondo yawo kukhala zomwetera.Mtundu wina sudzatenganso lupanga kumenyana ndi mtundu wina,kapena kuphunziranso za nkhondo. 5 Inu nyumba ya Yakobo, bwerani,tiyeni tiyende mʼkuwala kwa Yehova. 6 Inu Yehova mwawakana anthu anu,nyumba ya Yakobo.Iwo adzaza ndi zamatsenga zochokera Kummawa;amawombeza mawula ngati Afilisti,ndipo amayanjana ndi anthu osapembedza Mulungu. 7 Dziko lawo ndi lodzaza ndi siliva ndi golide;ndipo chuma chawo ndi chosatha.Dziko lawo ndi lodzaza ndi akavalo;ndipo magaleta awo ankhondo ngosawerengeka. 8 Dziko lawo ndi lodzaza ndi mafano;iwo amapembedza ntchito ya manja awo,amagwadira zomwe anapanga ndi zala zawo. 9 Tsono munthu aliyense adzachepetsedwandi kutsitsidwa.Inu Yehova musawakhululukire. 10 Lowani mʼmatanthwe,bisalani mʼmaenje,kuthawa kuopsa kwa Yehovandi ulemerero wa ufumu wake! 11 Kudzikuza kwa anthu kudzatha,ndipo kudzitama kwa anthu kudzawonongedwa;Yehova yekha ndiye adzapatsidwe ulemu pa tsiku limenelo. 12 Yehova Wamphamvuzonse wakonzeratu tsikulimene adzatsitse onse onyada ndi odzitama,ndipo adzagonjetsaonse amphamvu, 13 tsiku la mikungudza yonse ya ku Lebanoni, yayitali ndi yoonekera patali,ndiponso la mitengo yonse ya thundu ya ku Basani, 14 tsiku la mapiri onse ataliatalindiponso la zitunda zonse zazitali, 15 tsiku la nsanja zonse zazitalindiponso malinga onse olimba, 16 tsiku la sitima zapamadzi zonse za ku Tarisisindiponso la mabwato onse okongola. 17 Kudzikuza kwa munthu kudzathandipo kudzitama kwa anthu kudzawonongedwa,Yehova yekha ndiye adzapatsidwe ulemu tsiku limenelo, 18 ndipo mafano onse adzatheratu. 19 Anthu adzathawira mʼmapanga a matanthwendi mʼmaenje a nthaka,kuthawa mkwiyo wa Yehova,ndiponso ulemerero wa ufumu wake,pamene Iye adzuka kugwedeza dziko lapansi. 20 Tsiku limenelo anthu adzatayiramfuko ndi milememafano awo asiliva ndi mafano awo agolide,amene anawapanga kuti aziwapembedza. 21 Adzathawira mʼmapanga a matanthwendiponso mʼmingʼalu ya nthakakuthawa mkwiyo wa Yehovandiponso ulemerero wa ufumu wake,pamene Iye adzuka kugwedeza dziko lapansi. 22 Lekani kudalira munthu,amene moyo wake sukhalira kutha.Iye angathandize bwanji wina aliyense?
In Other Versions
Isaiah 2 in the ANGEFD
Isaiah 2 in the ANTPNG2D
Isaiah 2 in the AS21
Isaiah 2 in the BAGH
Isaiah 2 in the BBPNG
Isaiah 2 in the BBT1E
Isaiah 2 in the BDS
Isaiah 2 in the BEV
Isaiah 2 in the BHAD
Isaiah 2 in the BIB
Isaiah 2 in the BLPT
Isaiah 2 in the BNT
Isaiah 2 in the BNTABOOT
Isaiah 2 in the BNTLV
Isaiah 2 in the BOATCB
Isaiah 2 in the BOATCB2
Isaiah 2 in the BOBCV
Isaiah 2 in the BOCNT
Isaiah 2 in the BOECS
Isaiah 2 in the BOHCB
Isaiah 2 in the BOHCV
Isaiah 2 in the BOHLNT
Isaiah 2 in the BOHNTLTAL
Isaiah 2 in the BOICB
Isaiah 2 in the BOILNTAP
Isaiah 2 in the BOITCV
Isaiah 2 in the BOKCV
Isaiah 2 in the BOKCV2
Isaiah 2 in the BOKHWOG
Isaiah 2 in the BOKSSV
Isaiah 2 in the BOLCB
Isaiah 2 in the BOLCB2
Isaiah 2 in the BOMCV
Isaiah 2 in the BONAV
Isaiah 2 in the BONCB
Isaiah 2 in the BONLT
Isaiah 2 in the BONUT2
Isaiah 2 in the BOPLNT
Isaiah 2 in the BOSCB
Isaiah 2 in the BOSNC
Isaiah 2 in the BOTLNT
Isaiah 2 in the BOVCB
Isaiah 2 in the BOYCB
Isaiah 2 in the BPBB
Isaiah 2 in the BPH
Isaiah 2 in the BSB
Isaiah 2 in the CCB
Isaiah 2 in the CUV
Isaiah 2 in the CUVS
Isaiah 2 in the DBT
Isaiah 2 in the DGDNT
Isaiah 2 in the DHNT
Isaiah 2 in the DNT
Isaiah 2 in the ELBE
Isaiah 2 in the EMTV
Isaiah 2 in the ESV
Isaiah 2 in the FBV
Isaiah 2 in the FEB
Isaiah 2 in the GGMNT
Isaiah 2 in the GNT
Isaiah 2 in the HARY
Isaiah 2 in the HNT
Isaiah 2 in the IRVA
Isaiah 2 in the IRVB
Isaiah 2 in the IRVG
Isaiah 2 in the IRVH
Isaiah 2 in the IRVK
Isaiah 2 in the IRVM
Isaiah 2 in the IRVM2
Isaiah 2 in the IRVO
Isaiah 2 in the IRVP
Isaiah 2 in the IRVT
Isaiah 2 in the IRVT2
Isaiah 2 in the IRVU
Isaiah 2 in the ISVN
Isaiah 2 in the JSNT
Isaiah 2 in the KAPI
Isaiah 2 in the KBT1ETNIK
Isaiah 2 in the KBV
Isaiah 2 in the KJV
Isaiah 2 in the KNFD
Isaiah 2 in the LBA
Isaiah 2 in the LBLA
Isaiah 2 in the LNT
Isaiah 2 in the LSV
Isaiah 2 in the MAAL
Isaiah 2 in the MBV
Isaiah 2 in the MBV2
Isaiah 2 in the MHNT
Isaiah 2 in the MKNFD
Isaiah 2 in the MNG
Isaiah 2 in the MNT
Isaiah 2 in the MNT2
Isaiah 2 in the MRS1T
Isaiah 2 in the NAA
Isaiah 2 in the NASB
Isaiah 2 in the NBLA
Isaiah 2 in the NBS
Isaiah 2 in the NBVTP
Isaiah 2 in the NET2
Isaiah 2 in the NIV11
Isaiah 2 in the NNT
Isaiah 2 in the NNT2
Isaiah 2 in the NNT3
Isaiah 2 in the PDDPT
Isaiah 2 in the PFNT
Isaiah 2 in the RMNT
Isaiah 2 in the SBIAS
Isaiah 2 in the SBIBS
Isaiah 2 in the SBIBS2
Isaiah 2 in the SBICS
Isaiah 2 in the SBIDS
Isaiah 2 in the SBIGS
Isaiah 2 in the SBIHS
Isaiah 2 in the SBIIS
Isaiah 2 in the SBIIS2
Isaiah 2 in the SBIIS3
Isaiah 2 in the SBIKS
Isaiah 2 in the SBIKS2
Isaiah 2 in the SBIMS
Isaiah 2 in the SBIOS
Isaiah 2 in the SBIPS
Isaiah 2 in the SBISS
Isaiah 2 in the SBITS
Isaiah 2 in the SBITS2
Isaiah 2 in the SBITS3
Isaiah 2 in the SBITS4
Isaiah 2 in the SBIUS
Isaiah 2 in the SBIVS
Isaiah 2 in the SBT
Isaiah 2 in the SBT1E
Isaiah 2 in the SCHL
Isaiah 2 in the SNT
Isaiah 2 in the SUSU
Isaiah 2 in the SUSU2
Isaiah 2 in the SYNO
Isaiah 2 in the TBIAOTANT
Isaiah 2 in the TBT1E
Isaiah 2 in the TBT1E2
Isaiah 2 in the TFTIP
Isaiah 2 in the TFTU
Isaiah 2 in the TGNTATF3T
Isaiah 2 in the THAI
Isaiah 2 in the TNFD
Isaiah 2 in the TNT
Isaiah 2 in the TNTIK
Isaiah 2 in the TNTIL
Isaiah 2 in the TNTIN
Isaiah 2 in the TNTIP
Isaiah 2 in the TNTIZ
Isaiah 2 in the TOMA
Isaiah 2 in the TTENT
Isaiah 2 in the UBG
Isaiah 2 in the UGV
Isaiah 2 in the UGV2
Isaiah 2 in the UGV3
Isaiah 2 in the VBL
Isaiah 2 in the VDCC
Isaiah 2 in the YALU
Isaiah 2 in the YAPE
Isaiah 2 in the YBVTP
Isaiah 2 in the ZBP