Isaiah 40 (BOGWICC)

1 Atonthozeni, atonthozeni anthu anga,akutero Mulungu wanu. 2 Ayankhuleni moleza mtima anthu a ku Yerusalemundipo muwawuzitsekuti nthawi ya ukapolo wawo yatha,tchimo lawo lakhululukidwa.Ndawalanga mokwanirachifukwa cha machimo awo onse. 3 Mawu a wofuwula mʼchipululu akuti,“Konzani njira ya Yehovamʼchipululu;wongolani njira zake;msewu owongoka wa Mulungu wathu mʼdziko lopanda kanthu. 4 Chigwa chilichonse achidzaze.Phiri lililonse ndi chitunda chilichonse azitsitse;Dziko lokumbikakumbika alisalaze,malo azitundazitunda awasandutse zidikha. 5 Ndipo ulemerero wa Yehova udzaonekera,ndipo mitundu yonse ya anthu idzawuona,pakuti wanena zimenezi ndi Yehova.” 6 Wina ananena kuti, “Lengeza.”Ndipo ine ndinati, “Kodi ndifuwule chiyani? “Pakuti anthu onse ali ngati udzundipo kukongola kwawo kuli ngati maluwa akuthengo. 7 Udzu umanyala ndipo maluwa amafotachifukwa cha kuwomba kwa mpweya wa Yehova.”Mawu aja anatinso, “Ndithudi anthu sasiyana ndi udzu. 8 Udzu umanyala ndipo maluwa amafota,koma mawu a Mulungu wathu adzakhalapo mpaka muyaya.” 9 Iwe amene ukulengeza nkhani yabwino ku Ziyoni,kwera pa phiri lalitali.Iwe amene ukulengeza nkhani yabwino ku Yerusalemu,fuwula kwambiri,kweza mawu, usachite mantha;uza mizinda ya ku Yuda kuti,“Mulungu wanu akubwera!” 10 Taonani, Ambuye Yehova akubwera mwamphamvu,ndipo dzanja lake likulamulira,taonani akubwera ndi mphotho yakewatsogoza zofunkha zako za ku nkhondo. 11 Iye adzasamalira nkhosa zake ngati mʼbusa:Iye adzasonkhanitsa ana ankhosa aakazi mʼmanja mwakendipo Iye akuwanyamula pachifuwa chakendi kutsogolera bwinobwino nkhosa zoyamwitsa. 12 Kodi ndani akhoza kuyeza kuchuluka kwa madzi a mʼnyanja ndi chikhatho chake,kapena kuyeza kutalika kwa mlengalenga ndi dzanja lake?Ndani akhoza kuyeza dothi lonse la dziko lapansi mʼdengu,kapena kuyeza kulemera kwamapiri ndi zitunda ndi pasikelo? 13 Ndani anapereka malangizo kwa Mzimu wa Yehovakapena kumuphunzitsa Iye monga phungu wake? 14 Kodi Yehova anapemphapo nzeru kwa yani kuti akhale wopenya,kapena kuti aphunzire njira yoyenera ndi nzeru?Iye anapempha nzeru kwa yanindi njira ya kumvetsa zinthu? 15 Ndithudi mitundu ya anthu ili ngati dontho la madzi ochoka mu mtsuko.Iwo akungoyesedwa ngati fumbi chabe pa sikelo;mʼmanja mwa Yehova zilumba nʼzopepuka ngati fumbi. 16 Nkhalango ya ku Lebanoni singakwanire nkhuni zosonkhera moto pa guwa lansembe,ngakhale nyama zake sizingakwanire kupereka nsembe zopsereza. 17 Pamaso pa Yehova mitundu yonse ya anthu ili ngati chinthu chopandapake;Iye amayiwerengera ngati chinthu chopanda phindundi cha chabechabe. 18 Kodi tsono Mulungu mungamuyerekeze ndi yani?Kodi mungamufanizire ndi chiyani? 19 Likakhala fano, mʼmisiri ndiye analipangandipo mʼmisiri wa golide amalikuta ndi golidenaliveka mkanda wasiliva. 20 Mʼmphawi amene sangathe kupeza ngakhale chopereka nsembe chotereamasankha mtengo umene sudzawola,nafunafuna mʼmisiri waluso wotiamupangire fano limene silingasunthike. 21 Kodi simukudziwa?Kodi simunamve?Kodi sanakuwuzeni kuyambira pachiyambi pomwe?Kodi simunamvetsetse chiyambire cha dziko lapansi? 22 Yehova amene amakhala pa mpando wake waufumu kumwamba ndiye analenga dziko lapansi,Iye amaona anthu a dziko lapansi ngati ziwala.Ndipo anafunyulula mlengalenga ngati nsalu yotchinga,nayikunga ngati tenti yokhalamo. 23 Amatsitsa pansi mafumu amphamvunasandutsa olamula a dziko kukhala achabechabe. 24 Inde, iwo ali ngati mbewu zimene zangodzalidwa kumenekapena kufesedwa chapompano,ndi kungoyamba kuzika mizu kumenendi pamene mphepo imawombapo nʼkuziwumitsandipo kamvuluvulu amaziwulutsa ngati mankhusu. 25 Woyera uja akuti, “Kodi mudzandiyerekeza Ine ndi yani?Kapena kodi alipo wofanana nane?” 26 Tayangʼanani mlengalenga ndipo onani.Kodi ndani analenga zonsezi mukuzionazi?Yehova ndiye amene amazitsogolera ngati gulu la ankhondo,nayitana iliyonse ndi dzina lake.Ndipo popeza Iye ali ndi nyonga zambiri,palibe ndi imodzi yomwe imene inasowapo. 27 Iwe Yakobo, chifukwa chiyani umanenandi kumadandaula iwe Israeli, kuti,“Yehova sakudziwa mavuto anga,Mulungu wanga sakusamala zomwe zikundichitikira ine?” 28 Kodi simukudziwa?Kodi simunamve?Yehova ndiye Mulungu wamuyaya,ndiyenso Mlengi wa dziko lonse lapansi.Iye sadzatopa kapena kufowokandipo palibe amene angadziwe maganizo ake. 29 Iye amalimbitsa ofowokandipo otopa amawawonjezera mphamvu. 30 Ngakhale achinyamata amalefuka ndi kufowoka,ndipo achinyamata amapunthwa ndi kugwa; 31 koma iwo amene amakhulupirira Yehovaadzalandira mphamvu zatsopano.Adzawuluka ngati chiwombankhanga;adzathamanga koma sadzalefuka,adzayenda koma sadzatopa konse.

In Other Versions

Isaiah 40 in the ANGEFD

Isaiah 40 in the ANTPNG2D

Isaiah 40 in the AS21

Isaiah 40 in the BAGH

Isaiah 40 in the BBPNG

Isaiah 40 in the BBT1E

Isaiah 40 in the BDS

Isaiah 40 in the BEV

Isaiah 40 in the BHAD

Isaiah 40 in the BIB

Isaiah 40 in the BLPT

Isaiah 40 in the BNT

Isaiah 40 in the BNTABOOT

Isaiah 40 in the BNTLV

Isaiah 40 in the BOATCB

Isaiah 40 in the BOATCB2

Isaiah 40 in the BOBCV

Isaiah 40 in the BOCNT

Isaiah 40 in the BOECS

Isaiah 40 in the BOHCB

Isaiah 40 in the BOHCV

Isaiah 40 in the BOHLNT

Isaiah 40 in the BOHNTLTAL

Isaiah 40 in the BOICB

Isaiah 40 in the BOILNTAP

Isaiah 40 in the BOITCV

Isaiah 40 in the BOKCV

Isaiah 40 in the BOKCV2

Isaiah 40 in the BOKHWOG

Isaiah 40 in the BOKSSV

Isaiah 40 in the BOLCB

Isaiah 40 in the BOLCB2

Isaiah 40 in the BOMCV

Isaiah 40 in the BONAV

Isaiah 40 in the BONCB

Isaiah 40 in the BONLT

Isaiah 40 in the BONUT2

Isaiah 40 in the BOPLNT

Isaiah 40 in the BOSCB

Isaiah 40 in the BOSNC

Isaiah 40 in the BOTLNT

Isaiah 40 in the BOVCB

Isaiah 40 in the BOYCB

Isaiah 40 in the BPBB

Isaiah 40 in the BPH

Isaiah 40 in the BSB

Isaiah 40 in the CCB

Isaiah 40 in the CUV

Isaiah 40 in the CUVS

Isaiah 40 in the DBT

Isaiah 40 in the DGDNT

Isaiah 40 in the DHNT

Isaiah 40 in the DNT

Isaiah 40 in the ELBE

Isaiah 40 in the EMTV

Isaiah 40 in the ESV

Isaiah 40 in the FBV

Isaiah 40 in the FEB

Isaiah 40 in the GGMNT

Isaiah 40 in the GNT

Isaiah 40 in the HARY

Isaiah 40 in the HNT

Isaiah 40 in the IRVA

Isaiah 40 in the IRVB

Isaiah 40 in the IRVG

Isaiah 40 in the IRVH

Isaiah 40 in the IRVK

Isaiah 40 in the IRVM

Isaiah 40 in the IRVM2

Isaiah 40 in the IRVO

Isaiah 40 in the IRVP

Isaiah 40 in the IRVT

Isaiah 40 in the IRVT2

Isaiah 40 in the IRVU

Isaiah 40 in the ISVN

Isaiah 40 in the JSNT

Isaiah 40 in the KAPI

Isaiah 40 in the KBT1ETNIK

Isaiah 40 in the KBV

Isaiah 40 in the KJV

Isaiah 40 in the KNFD

Isaiah 40 in the LBA

Isaiah 40 in the LBLA

Isaiah 40 in the LNT

Isaiah 40 in the LSV

Isaiah 40 in the MAAL

Isaiah 40 in the MBV

Isaiah 40 in the MBV2

Isaiah 40 in the MHNT

Isaiah 40 in the MKNFD

Isaiah 40 in the MNG

Isaiah 40 in the MNT

Isaiah 40 in the MNT2

Isaiah 40 in the MRS1T

Isaiah 40 in the NAA

Isaiah 40 in the NASB

Isaiah 40 in the NBLA

Isaiah 40 in the NBS

Isaiah 40 in the NBVTP

Isaiah 40 in the NET2

Isaiah 40 in the NIV11

Isaiah 40 in the NNT

Isaiah 40 in the NNT2

Isaiah 40 in the NNT3

Isaiah 40 in the PDDPT

Isaiah 40 in the PFNT

Isaiah 40 in the RMNT

Isaiah 40 in the SBIAS

Isaiah 40 in the SBIBS

Isaiah 40 in the SBIBS2

Isaiah 40 in the SBICS

Isaiah 40 in the SBIDS

Isaiah 40 in the SBIGS

Isaiah 40 in the SBIHS

Isaiah 40 in the SBIIS

Isaiah 40 in the SBIIS2

Isaiah 40 in the SBIIS3

Isaiah 40 in the SBIKS

Isaiah 40 in the SBIKS2

Isaiah 40 in the SBIMS

Isaiah 40 in the SBIOS

Isaiah 40 in the SBIPS

Isaiah 40 in the SBISS

Isaiah 40 in the SBITS

Isaiah 40 in the SBITS2

Isaiah 40 in the SBITS3

Isaiah 40 in the SBITS4

Isaiah 40 in the SBIUS

Isaiah 40 in the SBIVS

Isaiah 40 in the SBT

Isaiah 40 in the SBT1E

Isaiah 40 in the SCHL

Isaiah 40 in the SNT

Isaiah 40 in the SUSU

Isaiah 40 in the SUSU2

Isaiah 40 in the SYNO

Isaiah 40 in the TBIAOTANT

Isaiah 40 in the TBT1E

Isaiah 40 in the TBT1E2

Isaiah 40 in the TFTIP

Isaiah 40 in the TFTU

Isaiah 40 in the TGNTATF3T

Isaiah 40 in the THAI

Isaiah 40 in the TNFD

Isaiah 40 in the TNT

Isaiah 40 in the TNTIK

Isaiah 40 in the TNTIL

Isaiah 40 in the TNTIN

Isaiah 40 in the TNTIP

Isaiah 40 in the TNTIZ

Isaiah 40 in the TOMA

Isaiah 40 in the TTENT

Isaiah 40 in the UBG

Isaiah 40 in the UGV

Isaiah 40 in the UGV2

Isaiah 40 in the UGV3

Isaiah 40 in the VBL

Isaiah 40 in the VDCC

Isaiah 40 in the YALU

Isaiah 40 in the YAPE

Isaiah 40 in the YBVTP

Isaiah 40 in the ZBP