Joel 3 (BOGWICC)
1 “Masiku amenewo ndiponso nthawi imeneyo,nditadzabwezeretsanso Yerusalemu ndi Yuda mʼchimake, 2 ndidzasonkhanitsa anthu a mitundu yonsendipo ndidzawabweretsa ku Chigwa cha Yehosafati.Kumeneko ndidzawaweruzachifukwa cha cholowa changa, anthu anga Aisraeli,pakuti anabalalitsa anthu anga pakati pa mitundu ya anthundikugawa dziko langa. 3 Anagawana anthu anga pochita maerendipo anyamata anawasinthanitsa ndi akazi achiwerewere;anagulitsa atsikana chifukwa cha vinyokuti iwo amwe. 4 “Kodi tsopano inu a ku Turo ndi Sidoni ndi madera onse a Filisitiya, muli ndi chiyani chotsutsana nane? Kodi mukundibwezera pa zinthu zimene ndakuchitirani? Ngati inu mukundibwezera, Ine ndidzabwezera zochita zanu mofulumira ndi mwachangu pa mitu yanu. 5 Pakuti munatenga siliva ndi golide wanga ndi kupita nacho chuma changa chamtengowapatali ku nyumba zanu zopembedzera mafano. 6 Inu munagulitsa anthu a ku Yuda ndi Yerusalemu kwa Agriki, kuti apite kutali ndi malire a dziko lawo. 7 “Taonani, Ine ndidzawachotsa kumalo kumene munawagulitsako, ndipo ndidzabwezera zimene mwachita pa mitu yanu. 8 Ndidzagulitsa ana anu aamuna ndi ana anu aakazi kwa anthu a ku Yuda, ndipo iwo adzawagulitsa kwa Aseba, mtundu wa anthu okhala kutali.” Yehova wayankhula. 9 Lengezani izi pakati pa anthu a mitundu ina:Konzekerani nkhondo!Dzutsani ankhondo amphamvu!Asilikali onse afike pafupi ndipo ayambe nkhondo. 10 Sulani makasu anu kuti akhale malupangandipo zikwanje zanu zikhale mikondo.Munthu wofowoka anene kuti,“Ndine wamphamvu!” 11 Bwerani msanga, inu anthu a mitundu yonse kuchokera ku mbali zonse,ndipo musonkhane kumeneko. Tumizani ankhondo anu Yehova! 12 “Mitundu ya anthu idzuke;ipite ku Chigwa cha Yehosafati,pakuti kumeneko Ine ndidzakhalandikuweruza anthu a mitundu yonse yozungulira. 13 Tengani chikwakwa chodulira tirigu,pakuti mbewu zakhwima.Bwerani dzapondeni mphesa,pakuti mopsinyira mphesa mwadzazandipo mitsuko ikusefukira;kuyipa kwa anthuwa nʼkwakukulu kwambiri!” 14 Chigulu cha anthu, chigulu cha anthu,mʼchigwa cha chiweruzo!Pakuti tsiku la Yehova layandikiramʼchigwa cha chiweruzo. 15 Dzuwa ndi mwezi zidzadetsedwa,ndipo nyenyezi sizidzawalanso. 16 Yehova adzabangula kuchokera mu Ziyonindipo mawu ake adzamveka ngati bingu kuchokera mu Yerusalemu;dziko lapansi ndi thambo zidzagwedezeka.Koma Yehova adzakhala pothawira pa anthu ake,linga la anthu a ku Israeli. 17 “Pamenepo inu mudzadziwa kuti Ine Yehova Mulungu wanu,ndimakhala mu Ziyoni, phiri langa lopatulika.Yerusalemu adzakhala wopatulika;alendo sadzamuthiranso nkhondo. 18 “Tsiku limenelo mapiri adzachucha vinyo watsopano,ndipo zitunda zidzayenderera mkaka;mitsinje yonse ya ku Yuda idzadzaza ndi madzi.Kasupe adzatumphuka mʼnyumba ya Yehovandipo adzathirira Chigwa cha Sitimu. 19 Koma Igupto adzasanduka bwinja,Edomu adzasanduka chipululu,chifukwa cha nkhondo imene anathira anthu a ku Yudamʼdziko limene anakhetsa magazi a anthu osalakwa. 20 Koma Yuda adzakhala ndi anthu mpaka muyayandi Yerusalemu ku mibadomibado. 21 Kukhetsa magazi kwawo kumene Ine sindinakhululukendidzakhululuka.” Yehova amakhala mu Ziyoni!
In Other Versions
Joel 3 in the ANGEFD
Joel 3 in the ANTPNG2D
Joel 3 in the AS21
Joel 3 in the BAGH
Joel 3 in the BBPNG
Joel 3 in the BBT1E
Joel 3 in the BDS
Joel 3 in the BEV
Joel 3 in the BHAD
Joel 3 in the BIB
Joel 3 in the BLPT
Joel 3 in the BNT
Joel 3 in the BNTABOOT
Joel 3 in the BNTLV
Joel 3 in the BOATCB
Joel 3 in the BOATCB2
Joel 3 in the BOBCV
Joel 3 in the BOCNT
Joel 3 in the BOECS
Joel 3 in the BOHCB
Joel 3 in the BOHCV
Joel 3 in the BOHLNT
Joel 3 in the BOHNTLTAL
Joel 3 in the BOICB
Joel 3 in the BOILNTAP
Joel 3 in the BOITCV
Joel 3 in the BOKCV
Joel 3 in the BOKCV2
Joel 3 in the BOKHWOG
Joel 3 in the BOKSSV
Joel 3 in the BOLCB
Joel 3 in the BOLCB2
Joel 3 in the BOMCV
Joel 3 in the BONAV
Joel 3 in the BONCB
Joel 3 in the BONLT
Joel 3 in the BONUT2
Joel 3 in the BOPLNT
Joel 3 in the BOSCB
Joel 3 in the BOSNC
Joel 3 in the BOTLNT
Joel 3 in the BOVCB
Joel 3 in the BOYCB
Joel 3 in the BPBB
Joel 3 in the BPH
Joel 3 in the BSB
Joel 3 in the CCB
Joel 3 in the CUV
Joel 3 in the CUVS
Joel 3 in the DBT
Joel 3 in the DGDNT
Joel 3 in the DHNT
Joel 3 in the DNT
Joel 3 in the ELBE
Joel 3 in the EMTV
Joel 3 in the ESV
Joel 3 in the FBV
Joel 3 in the FEB
Joel 3 in the GGMNT
Joel 3 in the GNT
Joel 3 in the HARY
Joel 3 in the HNT
Joel 3 in the IRVA
Joel 3 in the IRVB
Joel 3 in the IRVG
Joel 3 in the IRVH
Joel 3 in the IRVK
Joel 3 in the IRVM
Joel 3 in the IRVM2
Joel 3 in the IRVO
Joel 3 in the IRVP
Joel 3 in the IRVT
Joel 3 in the IRVT2
Joel 3 in the IRVU
Joel 3 in the ISVN
Joel 3 in the JSNT
Joel 3 in the KAPI
Joel 3 in the KBT1ETNIK
Joel 3 in the KBV
Joel 3 in the KJV
Joel 3 in the KNFD
Joel 3 in the LBA
Joel 3 in the LBLA
Joel 3 in the LNT
Joel 3 in the LSV
Joel 3 in the MAAL
Joel 3 in the MBV
Joel 3 in the MBV2
Joel 3 in the MHNT
Joel 3 in the MKNFD
Joel 3 in the MNG
Joel 3 in the MNT
Joel 3 in the MNT2
Joel 3 in the MRS1T
Joel 3 in the NAA
Joel 3 in the NASB
Joel 3 in the NBLA
Joel 3 in the NBS
Joel 3 in the NBVTP
Joel 3 in the NET2
Joel 3 in the NIV11
Joel 3 in the NNT
Joel 3 in the NNT2
Joel 3 in the NNT3
Joel 3 in the PDDPT
Joel 3 in the PFNT
Joel 3 in the RMNT
Joel 3 in the SBIAS
Joel 3 in the SBIBS
Joel 3 in the SBIBS2
Joel 3 in the SBICS
Joel 3 in the SBIDS
Joel 3 in the SBIGS
Joel 3 in the SBIHS
Joel 3 in the SBIIS
Joel 3 in the SBIIS2
Joel 3 in the SBIIS3
Joel 3 in the SBIKS
Joel 3 in the SBIKS2
Joel 3 in the SBIMS
Joel 3 in the SBIOS
Joel 3 in the SBIPS
Joel 3 in the SBISS
Joel 3 in the SBITS
Joel 3 in the SBITS2
Joel 3 in the SBITS3
Joel 3 in the SBITS4
Joel 3 in the SBIUS
Joel 3 in the SBIVS
Joel 3 in the SBT
Joel 3 in the SBT1E
Joel 3 in the SCHL
Joel 3 in the SNT
Joel 3 in the SUSU
Joel 3 in the SUSU2
Joel 3 in the SYNO
Joel 3 in the TBIAOTANT
Joel 3 in the TBT1E
Joel 3 in the TBT1E2
Joel 3 in the TFTIP
Joel 3 in the TFTU
Joel 3 in the TGNTATF3T
Joel 3 in the THAI
Joel 3 in the TNFD
Joel 3 in the TNT
Joel 3 in the TNTIK
Joel 3 in the TNTIL
Joel 3 in the TNTIN
Joel 3 in the TNTIP
Joel 3 in the TNTIZ
Joel 3 in the TOMA
Joel 3 in the TTENT
Joel 3 in the UBG
Joel 3 in the UGV
Joel 3 in the UGV2
Joel 3 in the UGV3
Joel 3 in the VBL
Joel 3 in the VDCC
Joel 3 in the YALU
Joel 3 in the YAPE
Joel 3 in the YBVTP
Joel 3 in the ZBP