Proverbs 30 (BOGWICC)
1 Nawa mawu a Aguri mwana wa Yake wa ku Masa:Munthuyo anati kwa Itieli, “Inu Mulungu, ine ndatopa.Inu Mulungu, ine ndatopa. Ndalefukiratu. 2 “Ine ndine munthu wopusa kuposa anthu onse;ndilibe nzeru zomvetsa zinthu zonga za munthu. 3 Sindinaphunzire nzeru,ndipo Woyerayo sindimudziwa. 4 Kodi ndani anakwera kumwamba ndi kutsikako?Ndani anafumbatapo mphepo mʼmanja mwake?Ndani anamanga madzi mʼchovala chake?Ndani anakhazikitsa mathero onse a dziko lapansi?Dzina lake ndani? Ndiwuze ngati ukudziwa!Ndipo mwana wake dzina lake ndani? 5 “Mawu ali wonse a Mulungu ndi opanda cholakwika;Iye ndi chishango kwa amene amathawira kwa Iye. 6 Usawonjezepo kanthu pa mawu ake,kuopa kuti Iye angadzakudzudzule ndi kukupeza kuti ndiwe wabodza.” 7 “Inu Yehova, ndikukupemphani zinthu ziwirimusandimane zimenezo ndisanafe: 8 Choyamba, mundichotsere kutali nane mabodza ndi chinyengo.Chachiwiri, ndisakhale mʼmphawi kapena munthu wachuma.Koma muzindidyetsa chakudya chondikwanira tsiku ndi tsiku 9 kuopa kuti ndikakhuta kwambiri ndingayambe kukukanani,nʼkumanena kuti, ‘Yehova ndiye yaninso?’Kuopanso kuti ndikakhala wosauka ndingayambe kuba,potero nʼkuyipitsa dzina la Mulungu wanga.” 10 “Usamusinjirire wantchito kwa mbuye wakekuopa kuti angakutemberere ndipo iweyo nʼkupezeka wolakwa.” 11 “Alipo ena amene amatemberera abambo awo,ndipo sadalitsa amayi awo. 12 Pali ena amene amadziyesa okha oyera mtimakomatu sanachotse zoyipa zawo. 13 Pali ena ndi odzitukumula kwambiri,amene amakweza zikope modzitukumula. 14 Pali ena amene mano awo ali ngati malupangandipo zibwano zawo zili ngati mipenimoti amadya amphawi ndi kuwachotsa pa dziko lapansi.Amachotsanso anthu osauka pakati pa anzawo.” 15 “Msundu uli ndi ana aakazi awiriiwo amalira kuti, ‘Tipatseni! Tipatseni!’ ” “Pali zinthu zitatu zimene sizikhuta,zinthu zinayi zimene sizinena kuti, ‘Takhuta!’ 16 Manda, mkazi wosabala,nthaka yosakhuta madzindiponso moto womangoyakirayakira!” 17 Aliyense amene amanyoza abambo ake,ndi kunyozera kumvera amayi ake,makwangwala a ku chigwa adzamukolowola masondipo mphungu zidzadya mnofu wake. 18 Pali zinthu zitatu zimene zimandidabwitsa,zinthu zinayi zimene ine sindizimvetsetsa. 19 Ndipo ndi izi: mmene chiwulukira chiwombankhanga mlengalenga;mmene iyendera njoka pa thanthwe;mmene chiyendera chombo pa nyanja;ndiponso mmene mwamuna achitira akakhala ndi namwali. 20 Umu ndi mʼmene mkazi amachitira atachita chigololo:Atatha kudya ndi kupukuta pakamwa pakeiye amanena kuti “Sindinachite kalikonse kolakwa.” 21 Pali zinthu zitatu zimene zimanjenjemeretsa dziko lapansi,pali zinthu zinayi zimene dziko lapansi silingathe kuzipirira: 22 Kapolo amene wasanduka mfumu,chitsiru chimene chakhuta, 23 mkazi wonyozeka akakwatiwandiponso wantchito wamkazi akalanda mwamuna wa mbuye wake. 24 Pali zinthu zinayi zingʼonozingʼono pa dziko lapansi,komatu ndi zochenjera kwambiri: 25 Nyerere zili ngati anthu opanda mphamvu,komatu zimasungiratu chakudya chake nthawi ya chilimwe; 26 mbira zili ngati anthu opanda mphamvukomatu zimakonza pokhalapo pawo mʼmiyala; 27 dzombe lilibe mfumu,komatu lonse limakhala mʼmagulumagulu poyenda. 28 Buluzi ungathe kumugwira mʼmanjakomatu amapezeka mʼnyumba za mafumu. 29 “Pali zinthu zitatu zimene zimayenda chinyachinya,pali zinthu zinayi zimene zimayenda monyadira: 30 Mkango umene uli wamphamvu kuposa nyama zonse,ndipo suthawa kanthu kalikonse. 31 Tambala woyenda chinyachinya, mbuzi yayimuna,ndiponso mfumu yoyenda pakati pa anthu ake. 32 “Ngati wakhala ukupusa ndi kumadzikweza wekha,kapena ngati wakhala ukukonzekera zoyipa,ndiye khala kaye chete, uganizire bwino! 33 Paja pakutha mkaka mafuta amapangidwa,ndipo ukapsinya mphuno, magazi amatuluka,ndipo mikangano imakhalapo ukalimbikira kukwiya.”
In Other Versions
Proverbs 30 in the ANGEFD
Proverbs 30 in the ANTPNG2D
Proverbs 30 in the AS21
Proverbs 30 in the BAGH
Proverbs 30 in the BBPNG
Proverbs 30 in the BBT1E
Proverbs 30 in the BDS
Proverbs 30 in the BEV
Proverbs 30 in the BHAD
Proverbs 30 in the BIB
Proverbs 30 in the BLPT
Proverbs 30 in the BNT
Proverbs 30 in the BNTABOOT
Proverbs 30 in the BNTLV
Proverbs 30 in the BOATCB
Proverbs 30 in the BOATCB2
Proverbs 30 in the BOBCV
Proverbs 30 in the BOCNT
Proverbs 30 in the BOECS
Proverbs 30 in the BOHCB
Proverbs 30 in the BOHCV
Proverbs 30 in the BOHLNT
Proverbs 30 in the BOHNTLTAL
Proverbs 30 in the BOICB
Proverbs 30 in the BOILNTAP
Proverbs 30 in the BOITCV
Proverbs 30 in the BOKCV
Proverbs 30 in the BOKCV2
Proverbs 30 in the BOKHWOG
Proverbs 30 in the BOKSSV
Proverbs 30 in the BOLCB
Proverbs 30 in the BOLCB2
Proverbs 30 in the BOMCV
Proverbs 30 in the BONAV
Proverbs 30 in the BONCB
Proverbs 30 in the BONLT
Proverbs 30 in the BONUT2
Proverbs 30 in the BOPLNT
Proverbs 30 in the BOSCB
Proverbs 30 in the BOSNC
Proverbs 30 in the BOTLNT
Proverbs 30 in the BOVCB
Proverbs 30 in the BOYCB
Proverbs 30 in the BPBB
Proverbs 30 in the BPH
Proverbs 30 in the BSB
Proverbs 30 in the CCB
Proverbs 30 in the CUV
Proverbs 30 in the CUVS
Proverbs 30 in the DBT
Proverbs 30 in the DGDNT
Proverbs 30 in the DHNT
Proverbs 30 in the DNT
Proverbs 30 in the ELBE
Proverbs 30 in the EMTV
Proverbs 30 in the ESV
Proverbs 30 in the FBV
Proverbs 30 in the FEB
Proverbs 30 in the GGMNT
Proverbs 30 in the GNT
Proverbs 30 in the HARY
Proverbs 30 in the HNT
Proverbs 30 in the IRVA
Proverbs 30 in the IRVB
Proverbs 30 in the IRVG
Proverbs 30 in the IRVH
Proverbs 30 in the IRVK
Proverbs 30 in the IRVM
Proverbs 30 in the IRVM2
Proverbs 30 in the IRVO
Proverbs 30 in the IRVP
Proverbs 30 in the IRVT
Proverbs 30 in the IRVT2
Proverbs 30 in the IRVU
Proverbs 30 in the ISVN
Proverbs 30 in the JSNT
Proverbs 30 in the KAPI
Proverbs 30 in the KBT1ETNIK
Proverbs 30 in the KBV
Proverbs 30 in the KJV
Proverbs 30 in the KNFD
Proverbs 30 in the LBA
Proverbs 30 in the LBLA
Proverbs 30 in the LNT
Proverbs 30 in the LSV
Proverbs 30 in the MAAL
Proverbs 30 in the MBV
Proverbs 30 in the MBV2
Proverbs 30 in the MHNT
Proverbs 30 in the MKNFD
Proverbs 30 in the MNG
Proverbs 30 in the MNT
Proverbs 30 in the MNT2
Proverbs 30 in the MRS1T
Proverbs 30 in the NAA
Proverbs 30 in the NASB
Proverbs 30 in the NBLA
Proverbs 30 in the NBS
Proverbs 30 in the NBVTP
Proverbs 30 in the NET2
Proverbs 30 in the NIV11
Proverbs 30 in the NNT
Proverbs 30 in the NNT2
Proverbs 30 in the NNT3
Proverbs 30 in the PDDPT
Proverbs 30 in the PFNT
Proverbs 30 in the RMNT
Proverbs 30 in the SBIAS
Proverbs 30 in the SBIBS
Proverbs 30 in the SBIBS2
Proverbs 30 in the SBICS
Proverbs 30 in the SBIDS
Proverbs 30 in the SBIGS
Proverbs 30 in the SBIHS
Proverbs 30 in the SBIIS
Proverbs 30 in the SBIIS2
Proverbs 30 in the SBIIS3
Proverbs 30 in the SBIKS
Proverbs 30 in the SBIKS2
Proverbs 30 in the SBIMS
Proverbs 30 in the SBIOS
Proverbs 30 in the SBIPS
Proverbs 30 in the SBISS
Proverbs 30 in the SBITS
Proverbs 30 in the SBITS2
Proverbs 30 in the SBITS3
Proverbs 30 in the SBITS4
Proverbs 30 in the SBIUS
Proverbs 30 in the SBIVS
Proverbs 30 in the SBT
Proverbs 30 in the SBT1E
Proverbs 30 in the SCHL
Proverbs 30 in the SNT
Proverbs 30 in the SUSU
Proverbs 30 in the SUSU2
Proverbs 30 in the SYNO
Proverbs 30 in the TBIAOTANT
Proverbs 30 in the TBT1E
Proverbs 30 in the TBT1E2
Proverbs 30 in the TFTIP
Proverbs 30 in the TFTU
Proverbs 30 in the TGNTATF3T
Proverbs 30 in the THAI
Proverbs 30 in the TNFD
Proverbs 30 in the TNT
Proverbs 30 in the TNTIK
Proverbs 30 in the TNTIL
Proverbs 30 in the TNTIN
Proverbs 30 in the TNTIP
Proverbs 30 in the TNTIZ
Proverbs 30 in the TOMA
Proverbs 30 in the TTENT
Proverbs 30 in the UBG
Proverbs 30 in the UGV
Proverbs 30 in the UGV2
Proverbs 30 in the UGV3
Proverbs 30 in the VBL
Proverbs 30 in the VDCC
Proverbs 30 in the YALU
Proverbs 30 in the YAPE
Proverbs 30 in the YBVTP
Proverbs 30 in the ZBP