Proverbs 8 (BOGWICC)
1 Kodi nzeru sikuyitana?Kodi nzeru yomvetsa zinthu sinakweze mawu ake? 2 Nzeru imayima pa zitunda mʼmbali mwa njira,imayima pa mphambano ya misewu. 3 Imafuwula pafupi ndi zipata zolowera mu mzinda,pa makomo olowera imafuwula kuti, 4 Inu anthu, ndikuyitana inu;ndikuyitanatu anthu onse. 5 Inu amene simudziwa kanthunu khalani ochenjera;inu amene ndi opusa, khalani ndi mtima womvetsa zinthu. 6 Mverani, pakuti ndikukuwuzani zinthu zofunika kwambiri;ndatsekula pakamwa panga ndipo payankhula zolungama. 7 Pakamwa panga pamayankhula zoonandimanyansidwa ndi kuyankhula zoyipa. 8 Mawu onse a pakamwa panga ndi olungama;mʼmawu angawo mulibe zokhotakhota kapena zopotoka. 9 Kwa anthu ozindikira, mawu anga onse ndi woona;kwa anthu amene ali ndi nzeru zomvetsa zinthu, mawu angawo ndi okhoza. 10 Landirani malangizo anga mʼmalo mwa siliva,nzeru zomvetsa zinthu mʼmalo mwa golide wabwino. 11 Paja nzeru ndi yabwino kwambiri kuposa miyala yamtengowapatali,ndipo zonse zimene ungazifune sizingafanane ndi nzeru. 12 Ine nzeru, ndimakhala pamodzi ndi kuchenjera.Ine ndimadziwa zinthu ndiponso ndimalingalira zinthu bwino. 13 Kuopa Yehova ndiko kudana ndi zoyipa.Ine ndimadana ndi kunyada, kudzitama,kuchita zoyipa, ndiponso kuyankhula zonyenga. 14 Ndine mwini uphungu ndi maganizo abwino;ndili ndi nzeru yomvetsa zinthu ndiponso mphamvu. 15 Ndine amene ndimathandiza mafumu kulamulira.Ndimawathandiza olamulira kukhazikitsa malamulo olungama. 16 Ndine amene ndimathandiza akalonga polamula.Ndinenso amene ndimathandiza akuluakulu onse kulamulira bwino dziko. 17 Ndimakonda amene amandikonda,ndipo amene amandifunafuna amandipeza. 18 Ine ndili ndi chuma ndi ulemu,chuma ndi kupindula pa ntchito kokhazikika. 19 Chipatso changa ndi chabwino kuposa golide, ngakhale golide wosalala;zimene ine ndimabereka zimaposa siliva wabwino kwambiri. 20 Ndimachita zinthu zolungama.Ine sindipatuka mʼnjira za chilungamo. 21 Ndimapereka chuma kwa amene amandikondandi kudzaza nyumba zawo zosungiramo chuma. 22 “Yehova anandilenga ine nzeru monga ntchito yake yoyamba.Mwa ntchito zake zakalekale yoyamba ndinali ine. 23 Ndinapangidwa kalekalelo,pachiyambi penipeni dziko lapansi lisanalengedwe. 24 Nyanja, akasupe odzaza ndi madzi,zonsezi kulibe pamene ine ndinkabadwa. 25 Mapiri asanakhazikitsidwe pa malo awo,mapiri angʼonoangʼono asanakhalepo, ine ndinali nditabadwa kale, 26 lisanalengedwe dziko lapansi ndi minda yake;lisanalengedwe dothi loyamba la dziko lapansi. 27 Ine ndinalipo pamene Yehova ankakhazikitsa mlengalenga,pamene ankalemba malire a nyanja yozama, 28 pamene anakhazikitsa mitambo ya mlengalengandi kukhazikitsa akasupe a madzi ozama, 29 pamene anayikira nyanja malirekuti madzi asadutse malirewo,ndiponso pamene ankayika malire a dziko lapansi. 30 Tsono ine ndinali pambali pake ngati mmisiri;ndikumukondweretsa tsiku ndi tsiku,kusangalala nthawi zonse pamaso pake. 31 Ndinkasangalala ndi dziko lake lonsendiponso kumakondwera nawo anthu onse.” 32 “Ndiye tsono ana inu, ndimvereni;odala anthu amene amasunga njira zanga. 33 Mverani malangizo anga kuti mukhale ndi nzeru;musanyozere mawu anga. 34 Wodala munthu amene amandimvera,amene amakhala pa khomo panga tsiku ndi tsiku,kudikirira pa chitseko changa. 35 Paja aliyense amene apeza ine wapeza moyondipo Yehova amamukomera mtima. 36 Koma amene alephera kundipeza, amadzipweteka yekha;onse amene amandida amakonda imfa.”
In Other Versions
Proverbs 8 in the ANGEFD
Proverbs 8 in the ANTPNG2D
Proverbs 8 in the AS21
Proverbs 8 in the BAGH
Proverbs 8 in the BBPNG
Proverbs 8 in the BBT1E
Proverbs 8 in the BDS
Proverbs 8 in the BEV
Proverbs 8 in the BHAD
Proverbs 8 in the BIB
Proverbs 8 in the BLPT
Proverbs 8 in the BNT
Proverbs 8 in the BNTABOOT
Proverbs 8 in the BNTLV
Proverbs 8 in the BOATCB
Proverbs 8 in the BOATCB2
Proverbs 8 in the BOBCV
Proverbs 8 in the BOCNT
Proverbs 8 in the BOECS
Proverbs 8 in the BOHCB
Proverbs 8 in the BOHCV
Proverbs 8 in the BOHLNT
Proverbs 8 in the BOHNTLTAL
Proverbs 8 in the BOICB
Proverbs 8 in the BOILNTAP
Proverbs 8 in the BOITCV
Proverbs 8 in the BOKCV
Proverbs 8 in the BOKCV2
Proverbs 8 in the BOKHWOG
Proverbs 8 in the BOKSSV
Proverbs 8 in the BOLCB
Proverbs 8 in the BOLCB2
Proverbs 8 in the BOMCV
Proverbs 8 in the BONAV
Proverbs 8 in the BONCB
Proverbs 8 in the BONLT
Proverbs 8 in the BONUT2
Proverbs 8 in the BOPLNT
Proverbs 8 in the BOSCB
Proverbs 8 in the BOSNC
Proverbs 8 in the BOTLNT
Proverbs 8 in the BOVCB
Proverbs 8 in the BOYCB
Proverbs 8 in the BPBB
Proverbs 8 in the BPH
Proverbs 8 in the BSB
Proverbs 8 in the CCB
Proverbs 8 in the CUV
Proverbs 8 in the CUVS
Proverbs 8 in the DBT
Proverbs 8 in the DGDNT
Proverbs 8 in the DHNT
Proverbs 8 in the DNT
Proverbs 8 in the ELBE
Proverbs 8 in the EMTV
Proverbs 8 in the ESV
Proverbs 8 in the FBV
Proverbs 8 in the FEB
Proverbs 8 in the GGMNT
Proverbs 8 in the GNT
Proverbs 8 in the HARY
Proverbs 8 in the HNT
Proverbs 8 in the IRVA
Proverbs 8 in the IRVB
Proverbs 8 in the IRVG
Proverbs 8 in the IRVH
Proverbs 8 in the IRVK
Proverbs 8 in the IRVM
Proverbs 8 in the IRVM2
Proverbs 8 in the IRVO
Proverbs 8 in the IRVP
Proverbs 8 in the IRVT
Proverbs 8 in the IRVT2
Proverbs 8 in the IRVU
Proverbs 8 in the ISVN
Proverbs 8 in the JSNT
Proverbs 8 in the KAPI
Proverbs 8 in the KBT1ETNIK
Proverbs 8 in the KBV
Proverbs 8 in the KJV
Proverbs 8 in the KNFD
Proverbs 8 in the LBA
Proverbs 8 in the LBLA
Proverbs 8 in the LNT
Proverbs 8 in the LSV
Proverbs 8 in the MAAL
Proverbs 8 in the MBV
Proverbs 8 in the MBV2
Proverbs 8 in the MHNT
Proverbs 8 in the MKNFD
Proverbs 8 in the MNG
Proverbs 8 in the MNT
Proverbs 8 in the MNT2
Proverbs 8 in the MRS1T
Proverbs 8 in the NAA
Proverbs 8 in the NASB
Proverbs 8 in the NBLA
Proverbs 8 in the NBS
Proverbs 8 in the NBVTP
Proverbs 8 in the NET2
Proverbs 8 in the NIV11
Proverbs 8 in the NNT
Proverbs 8 in the NNT2
Proverbs 8 in the NNT3
Proverbs 8 in the PDDPT
Proverbs 8 in the PFNT
Proverbs 8 in the RMNT
Proverbs 8 in the SBIAS
Proverbs 8 in the SBIBS
Proverbs 8 in the SBIBS2
Proverbs 8 in the SBICS
Proverbs 8 in the SBIDS
Proverbs 8 in the SBIGS
Proverbs 8 in the SBIHS
Proverbs 8 in the SBIIS
Proverbs 8 in the SBIIS2
Proverbs 8 in the SBIIS3
Proverbs 8 in the SBIKS
Proverbs 8 in the SBIKS2
Proverbs 8 in the SBIMS
Proverbs 8 in the SBIOS
Proverbs 8 in the SBIPS
Proverbs 8 in the SBISS
Proverbs 8 in the SBITS
Proverbs 8 in the SBITS2
Proverbs 8 in the SBITS3
Proverbs 8 in the SBITS4
Proverbs 8 in the SBIUS
Proverbs 8 in the SBIVS
Proverbs 8 in the SBT
Proverbs 8 in the SBT1E
Proverbs 8 in the SCHL
Proverbs 8 in the SNT
Proverbs 8 in the SUSU
Proverbs 8 in the SUSU2
Proverbs 8 in the SYNO
Proverbs 8 in the TBIAOTANT
Proverbs 8 in the TBT1E
Proverbs 8 in the TBT1E2
Proverbs 8 in the TFTIP
Proverbs 8 in the TFTU
Proverbs 8 in the TGNTATF3T
Proverbs 8 in the THAI
Proverbs 8 in the TNFD
Proverbs 8 in the TNT
Proverbs 8 in the TNTIK
Proverbs 8 in the TNTIL
Proverbs 8 in the TNTIN
Proverbs 8 in the TNTIP
Proverbs 8 in the TNTIZ
Proverbs 8 in the TOMA
Proverbs 8 in the TTENT
Proverbs 8 in the UBG
Proverbs 8 in the UGV
Proverbs 8 in the UGV2
Proverbs 8 in the UGV3
Proverbs 8 in the VBL
Proverbs 8 in the VDCC
Proverbs 8 in the YALU
Proverbs 8 in the YAPE
Proverbs 8 in the YBVTP
Proverbs 8 in the ZBP