Revelation 4 (BOGWICC)
1 Kenaka, nditayangʼana patsogolo panga ndinaona khomo lotsekuka la kumwamba. Ndipo liwu lija ndinalimva poyamba lokhala ngati lipenga linati, “Bwera kuno, ndipo ndidzakuonetsa zimene zichitike zikatha izi.” 2 Nthawi yomweyo ndinatengedwa ndi Mzimu Woyera, ndipo patsogolo panga ndinaona mpando waufumu wina atakhalapo. 3 Ndipo amene anakhalapoyo anali wa maonekedwe ngati miyala ya jasipa ndi sardiyo. Utawaleza wooneka ngati simaragido unazinga mpando waufumuwo. 4 Kuzungulira mpando waufumuwu panalinso mipando ina yaufumu yokwana 24 ndipo panakhala akuluakulu 24 atavala zoyera ndipo anavala zipewa zaufumu zagolide pamutu. 5 Kumpando waufumuwo kunkatuluka mphenzi, phokoso ndi mabingu. Patsogolo pake pa mpando waufumuwo panali nyale zisanu ndi ziwiri zoyaka. Iyi ndiyo mizimu isanu ndi iwiri ya Mulungu. 6 Patsogolo pa mpando waufumu pomwepo panalinso ngati nyanja yagalasi yonyezimira ngati mwala wa krustalo.Pakatinʼpakati, kuzungulira mpando waufumuwo panali zamoyo zinayi zokhala ndi maso ponseponse, kutsogolo ndi kumbuyo komwe. 7 Chamoyo choyamba chinali ngati mkango, chachiwiri chinali ngati mwana wangʼombe, chachitatu chinali ndi nkhope ngati munthu, chachinayi chinali ngati chiwombankhanga chowuluka. 8 Chamoyo chilichonse chinali ndi mapiko asanu ndi limodzi, ndipo chinali ndi maso ponseponse ndi mʼkati mwa mapiko momwe. Usana ndi usiku zimanena mosalekeza kuti,“Woyera, woyera, woyerandi Ambuye Mulungu Wamphamvuzonse,amene munali, amene muli ndi amene mukubwera.” 9 Nthawi zonse zamoyozo zimapereka ulemerero, ulemu ndi mayamiko kwa uja wokhala pa mpando waufumu, amene ali ndi moyo wamuyaya. 10 Izi zikamachitika akuluakulu 24 aja amadzigwetsa pansi pamaso pa wokhala pa mpando waufumuyo, namupembedza wokhala ndi moyo wamuyayayo. Iwo amaponya pansi zipewa zawo zaufumu patsogolo pa mpando waufumu nati: 11 “Ndinu woyeneradi kulandira ulemerero ndi ulemu ndi mphamvu,Ambuye ndi Mulungu wathu,pakuti munalenga zinthu zonse,ndipo mwakufuna kwanuzinalengedwa monga zilili.”
In Other Versions
Revelation 4 in the ANGEFD
Revelation 4 in the ANTPNG2D
Revelation 4 in the AS21
Revelation 4 in the BAGH
Revelation 4 in the BBPNG
Revelation 4 in the BBT1E
Revelation 4 in the BDS
Revelation 4 in the BEV
Revelation 4 in the BHAD
Revelation 4 in the BIB
Revelation 4 in the BLPT
Revelation 4 in the BNT
Revelation 4 in the BNTABOOT
Revelation 4 in the BNTLV
Revelation 4 in the BOATCB
Revelation 4 in the BOATCB2
Revelation 4 in the BOBCV
Revelation 4 in the BOCNT
Revelation 4 in the BOECS
Revelation 4 in the BOHCB
Revelation 4 in the BOHCV
Revelation 4 in the BOHLNT
Revelation 4 in the BOHNTLTAL
Revelation 4 in the BOICB
Revelation 4 in the BOILNTAP
Revelation 4 in the BOITCV
Revelation 4 in the BOKCV
Revelation 4 in the BOKCV2
Revelation 4 in the BOKHWOG
Revelation 4 in the BOKSSV
Revelation 4 in the BOLCB
Revelation 4 in the BOLCB2
Revelation 4 in the BOMCV
Revelation 4 in the BONAV
Revelation 4 in the BONCB
Revelation 4 in the BONLT
Revelation 4 in the BONUT2
Revelation 4 in the BOPLNT
Revelation 4 in the BOSCB
Revelation 4 in the BOSNC
Revelation 4 in the BOTLNT
Revelation 4 in the BOVCB
Revelation 4 in the BOYCB
Revelation 4 in the BPBB
Revelation 4 in the BPH
Revelation 4 in the BSB
Revelation 4 in the CCB
Revelation 4 in the CUV
Revelation 4 in the CUVS
Revelation 4 in the DBT
Revelation 4 in the DGDNT
Revelation 4 in the DHNT
Revelation 4 in the DNT
Revelation 4 in the ELBE
Revelation 4 in the EMTV
Revelation 4 in the ESV
Revelation 4 in the FBV
Revelation 4 in the FEB
Revelation 4 in the GGMNT
Revelation 4 in the GNT
Revelation 4 in the HARY
Revelation 4 in the HNT
Revelation 4 in the IRVA
Revelation 4 in the IRVB
Revelation 4 in the IRVG
Revelation 4 in the IRVH
Revelation 4 in the IRVK
Revelation 4 in the IRVM
Revelation 4 in the IRVM2
Revelation 4 in the IRVO
Revelation 4 in the IRVP
Revelation 4 in the IRVT
Revelation 4 in the IRVT2
Revelation 4 in the IRVU
Revelation 4 in the ISVN
Revelation 4 in the JSNT
Revelation 4 in the KAPI
Revelation 4 in the KBT1ETNIK
Revelation 4 in the KBV
Revelation 4 in the KJV
Revelation 4 in the KNFD
Revelation 4 in the LBA
Revelation 4 in the LBLA
Revelation 4 in the LNT
Revelation 4 in the LSV
Revelation 4 in the MAAL
Revelation 4 in the MBV
Revelation 4 in the MBV2
Revelation 4 in the MHNT
Revelation 4 in the MKNFD
Revelation 4 in the MNG
Revelation 4 in the MNT
Revelation 4 in the MNT2
Revelation 4 in the MRS1T
Revelation 4 in the NAA
Revelation 4 in the NASB
Revelation 4 in the NBLA
Revelation 4 in the NBS
Revelation 4 in the NBVTP
Revelation 4 in the NET2
Revelation 4 in the NIV11
Revelation 4 in the NNT
Revelation 4 in the NNT2
Revelation 4 in the NNT3
Revelation 4 in the PDDPT
Revelation 4 in the PFNT
Revelation 4 in the RMNT
Revelation 4 in the SBIAS
Revelation 4 in the SBIBS
Revelation 4 in the SBIBS2
Revelation 4 in the SBICS
Revelation 4 in the SBIDS
Revelation 4 in the SBIGS
Revelation 4 in the SBIHS
Revelation 4 in the SBIIS
Revelation 4 in the SBIIS2
Revelation 4 in the SBIIS3
Revelation 4 in the SBIKS
Revelation 4 in the SBIKS2
Revelation 4 in the SBIMS
Revelation 4 in the SBIOS
Revelation 4 in the SBIPS
Revelation 4 in the SBISS
Revelation 4 in the SBITS
Revelation 4 in the SBITS2
Revelation 4 in the SBITS3
Revelation 4 in the SBITS4
Revelation 4 in the SBIUS
Revelation 4 in the SBIVS
Revelation 4 in the SBT
Revelation 4 in the SBT1E
Revelation 4 in the SCHL
Revelation 4 in the SNT
Revelation 4 in the SUSU
Revelation 4 in the SUSU2
Revelation 4 in the SYNO
Revelation 4 in the TBIAOTANT
Revelation 4 in the TBT1E
Revelation 4 in the TBT1E2
Revelation 4 in the TFTIP
Revelation 4 in the TFTU
Revelation 4 in the TGNTATF3T
Revelation 4 in the THAI
Revelation 4 in the TNFD
Revelation 4 in the TNT
Revelation 4 in the TNTIK
Revelation 4 in the TNTIL
Revelation 4 in the TNTIN
Revelation 4 in the TNTIP
Revelation 4 in the TNTIZ
Revelation 4 in the TOMA
Revelation 4 in the TTENT
Revelation 4 in the UBG
Revelation 4 in the UGV
Revelation 4 in the UGV2
Revelation 4 in the UGV3
Revelation 4 in the VBL
Revelation 4 in the VDCC
Revelation 4 in the YALU
Revelation 4 in the YAPE
Revelation 4 in the YBVTP
Revelation 4 in the ZBP