2 Thessalonians 2 (BOGWICC)

1 Pa za kubweranso kwa Ambuye athu Yesu Khristu ndiponso za kusonkhana kwathu kuti tikumane naye, abale, tikukupemphani 2 kuti musagwedezeke msanga mʼmaganizo kapena kuopsezedwa ndi uneneri, mbiri kapena kalata yokhala ngati yachokera kwa ife, yonena kuti tsiku lija la Ambuye linafika kale. 3 Musalole kuti wina aliyense akunamizeni mwa njira ina iliyonse. Pakuti tsikulo lisanafike, kudzakhala mpatuko waukulu kwambiri, ndipo kudzaoneka munthu woyipitsitsa uja, munthu woyenera kuwonongedwayo. 4 Iyeyo adzatsutsa ndi kudziyika pamwamba pa chilichonse chimene anthu amachitcha mulungu kapena amachipembedza. Iyeyo adzadzikhazika mʼNyumba ya Mulungu ndi kudzitcha Mulungu. 5 Kodi simukukumbukira kuti pamene ndinali nanu pamodzi ndinkakuwuzani zimenezi? 6 Ndipo tsopano mukudziwa chimene chikumuletsa kuonekera, koma adzawululika pa nthawi yake yoyenera. 7 Pakuti mphamvu yobisika yoyipitsitsa ikugwira ntchito ngakhale tsopano; koma amene akutchinga mphamvuyo adzapitiriza kutero mpaka pamene wotchingayo adzachotsedwe. 8 Ndipo kenaka woyipitsitsayo adzaonekera, amene Ambuye Yesu adzamugonjetsa ndi mpweya otuluka mʼkamwa mwake ndi kumuwononga ndi ulemerero wa kubwera kwake. 9 Woyipitsitsayo adzabwera ndi mphamvu za Satana. Adzaonetsa mphamvu zake pochita zizindikiro ndi zodabwitsa zachinyengo. 10 Iye adzagwiritsa ntchito mtundu uliwonse wachinyengo kupusitsa amene akuwonongeka. Iwo akuwonongeka chifukwa akukana kukonda choonadi ndi kuti apulumutsidwe. 11 Chifukwa cha chimenechi, Mulungu akuwatumizira chinyengo chachikulu kuti akhulupirire bodza. 12 Choncho adzalangidwa onse amene sanakhulupirire choonadi, koma anakondwera mu zoyipa. 13 Koma tiyenera kuyamika Mulungu chifukwa cha inu abale okondedwa mwa Ambuye, pakuti Mulungu anakusankhani pachiyambi pomwe kuti mupulumuke chifukwa cha ntchito yoyeretsa ya Mzimu ndi chikhulupiriro chanu mʼchoonadi. 14 Iye anakuyitanirani zimenezi kudzera mwa uthenga wathu wabwino, kuti mulandire nawo ulemerero wa Ambuye athu Yesu Khristu. 15 Kotero tsono, abale, imani mwamphamvu ndi kugwiritsa ziphunzitso zimene tinakupatsani kudzera mʼmawu apakamwa kapena kudzera mʼkalata. 16 Ambuye athu Yesu Khristu mwini ndi Mulungu Atate wathu, amene anatikonda ife ndipo mwachisomo chake anatipatsa kulimba mtima kwamuyaya ndi chiyembekezo chabwino, 17 akulimbikitseni ndi kukupatsani mphamvu yogwirira ntchito ndi kuyankhula zabwino zilizonse.

In Other Versions

2 Thessalonians 2 in the ANGEFD

2 Thessalonians 2 in the ANTPNG2D

2 Thessalonians 2 in the AS21

2 Thessalonians 2 in the BAGH

2 Thessalonians 2 in the BBPNG

2 Thessalonians 2 in the BBT1E

2 Thessalonians 2 in the BDS

2 Thessalonians 2 in the BEV

2 Thessalonians 2 in the BHAD

2 Thessalonians 2 in the BIB

2 Thessalonians 2 in the BLPT

2 Thessalonians 2 in the BNT

2 Thessalonians 2 in the BNTABOOT

2 Thessalonians 2 in the BNTLV

2 Thessalonians 2 in the BOATCB

2 Thessalonians 2 in the BOATCB2

2 Thessalonians 2 in the BOBCV

2 Thessalonians 2 in the BOCNT

2 Thessalonians 2 in the BOECS

2 Thessalonians 2 in the BOHCB

2 Thessalonians 2 in the BOHCV

2 Thessalonians 2 in the BOHLNT

2 Thessalonians 2 in the BOHNTLTAL

2 Thessalonians 2 in the BOICB

2 Thessalonians 2 in the BOILNTAP

2 Thessalonians 2 in the BOITCV

2 Thessalonians 2 in the BOKCV

2 Thessalonians 2 in the BOKCV2

2 Thessalonians 2 in the BOKHWOG

2 Thessalonians 2 in the BOKSSV

2 Thessalonians 2 in the BOLCB

2 Thessalonians 2 in the BOLCB2

2 Thessalonians 2 in the BOMCV

2 Thessalonians 2 in the BONAV

2 Thessalonians 2 in the BONCB

2 Thessalonians 2 in the BONLT

2 Thessalonians 2 in the BONUT2

2 Thessalonians 2 in the BOPLNT

2 Thessalonians 2 in the BOSCB

2 Thessalonians 2 in the BOSNC

2 Thessalonians 2 in the BOTLNT

2 Thessalonians 2 in the BOVCB

2 Thessalonians 2 in the BOYCB

2 Thessalonians 2 in the BPBB

2 Thessalonians 2 in the BPH

2 Thessalonians 2 in the BSB

2 Thessalonians 2 in the CCB

2 Thessalonians 2 in the CUV

2 Thessalonians 2 in the CUVS

2 Thessalonians 2 in the DBT

2 Thessalonians 2 in the DGDNT

2 Thessalonians 2 in the DHNT

2 Thessalonians 2 in the DNT

2 Thessalonians 2 in the ELBE

2 Thessalonians 2 in the EMTV

2 Thessalonians 2 in the ESV

2 Thessalonians 2 in the FBV

2 Thessalonians 2 in the FEB

2 Thessalonians 2 in the GGMNT

2 Thessalonians 2 in the GNT

2 Thessalonians 2 in the HARY

2 Thessalonians 2 in the HNT

2 Thessalonians 2 in the IRVA

2 Thessalonians 2 in the IRVB

2 Thessalonians 2 in the IRVG

2 Thessalonians 2 in the IRVH

2 Thessalonians 2 in the IRVK

2 Thessalonians 2 in the IRVM

2 Thessalonians 2 in the IRVM2

2 Thessalonians 2 in the IRVO

2 Thessalonians 2 in the IRVP

2 Thessalonians 2 in the IRVT

2 Thessalonians 2 in the IRVT2

2 Thessalonians 2 in the IRVU

2 Thessalonians 2 in the ISVN

2 Thessalonians 2 in the JSNT

2 Thessalonians 2 in the KAPI

2 Thessalonians 2 in the KBT1ETNIK

2 Thessalonians 2 in the KBV

2 Thessalonians 2 in the KJV

2 Thessalonians 2 in the KNFD

2 Thessalonians 2 in the LBA

2 Thessalonians 2 in the LBLA

2 Thessalonians 2 in the LNT

2 Thessalonians 2 in the LSV

2 Thessalonians 2 in the MAAL

2 Thessalonians 2 in the MBV

2 Thessalonians 2 in the MBV2

2 Thessalonians 2 in the MHNT

2 Thessalonians 2 in the MKNFD

2 Thessalonians 2 in the MNG

2 Thessalonians 2 in the MNT

2 Thessalonians 2 in the MNT2

2 Thessalonians 2 in the MRS1T

2 Thessalonians 2 in the NAA

2 Thessalonians 2 in the NASB

2 Thessalonians 2 in the NBLA

2 Thessalonians 2 in the NBS

2 Thessalonians 2 in the NBVTP

2 Thessalonians 2 in the NET2

2 Thessalonians 2 in the NIV11

2 Thessalonians 2 in the NNT

2 Thessalonians 2 in the NNT2

2 Thessalonians 2 in the NNT3

2 Thessalonians 2 in the PDDPT

2 Thessalonians 2 in the PFNT

2 Thessalonians 2 in the RMNT

2 Thessalonians 2 in the SBIAS

2 Thessalonians 2 in the SBIBS

2 Thessalonians 2 in the SBIBS2

2 Thessalonians 2 in the SBICS

2 Thessalonians 2 in the SBIDS

2 Thessalonians 2 in the SBIGS

2 Thessalonians 2 in the SBIHS

2 Thessalonians 2 in the SBIIS

2 Thessalonians 2 in the SBIIS2

2 Thessalonians 2 in the SBIIS3

2 Thessalonians 2 in the SBIKS

2 Thessalonians 2 in the SBIKS2

2 Thessalonians 2 in the SBIMS

2 Thessalonians 2 in the SBIOS

2 Thessalonians 2 in the SBIPS

2 Thessalonians 2 in the SBISS

2 Thessalonians 2 in the SBITS

2 Thessalonians 2 in the SBITS2

2 Thessalonians 2 in the SBITS3

2 Thessalonians 2 in the SBITS4

2 Thessalonians 2 in the SBIUS

2 Thessalonians 2 in the SBIVS

2 Thessalonians 2 in the SBT

2 Thessalonians 2 in the SBT1E

2 Thessalonians 2 in the SCHL

2 Thessalonians 2 in the SNT

2 Thessalonians 2 in the SUSU

2 Thessalonians 2 in the SUSU2

2 Thessalonians 2 in the SYNO

2 Thessalonians 2 in the TBIAOTANT

2 Thessalonians 2 in the TBT1E

2 Thessalonians 2 in the TBT1E2

2 Thessalonians 2 in the TFTIP

2 Thessalonians 2 in the TFTU

2 Thessalonians 2 in the TGNTATF3T

2 Thessalonians 2 in the THAI

2 Thessalonians 2 in the TNFD

2 Thessalonians 2 in the TNT

2 Thessalonians 2 in the TNTIK

2 Thessalonians 2 in the TNTIL

2 Thessalonians 2 in the TNTIN

2 Thessalonians 2 in the TNTIP

2 Thessalonians 2 in the TNTIZ

2 Thessalonians 2 in the TOMA

2 Thessalonians 2 in the TTENT

2 Thessalonians 2 in the UBG

2 Thessalonians 2 in the UGV

2 Thessalonians 2 in the UGV2

2 Thessalonians 2 in the UGV3

2 Thessalonians 2 in the VBL

2 Thessalonians 2 in the VDCC

2 Thessalonians 2 in the YALU

2 Thessalonians 2 in the YAPE

2 Thessalonians 2 in the YBVTP

2 Thessalonians 2 in the ZBP