Exodus 15 (BOGWICC)
1 Ndipo Mose ndi Aisraeli anayimbira Yehova nyimbo iyi:“Ine ndidzayimbira Yehovapakuti wakwezeka mʼchigonjetso.Kavalo ndi wokwera wake,Iye wawaponya mʼnyanja. 2 Yehova ndiye mphamvu yanga ndi nyimbo yanga;ndiye chipulumutso changa.Iye ndiye Mulungu wanga, ndipo ndidzamutamanda,Mulungu wa makolo anga, ine ndidzamukweza. 3 Yehova ndi wankhondo;Yehova ndilo dzina lake. 4 Magaleta a Farao ndi asilikali ake ankhondoIye wawaponya mʼnyanja.Akatswiri ankhondo amphamvu a Faraoamizidwa mʼNyanja Yofiira. 5 Nyanja yakuya inawaphimba;Iwo anamira pansi ngati mwala.” 6 Yehova, dzanja lanu lamanjandi laulemerero chifukwa cha mphamvu zake.Ndithu Yehova, dzanja lanu lamanjalinaphwanya mdani. 7 Ndi ulemerero wanu waukulu,munagonjetsa okutsutsani.Inu munatumiza mkwiyo wanu waukulu;ndipo unawapsereza ngati udzu. 8 Ndi mpweya wotuluka mʼmphuno mwanumadzi anawunjikana pamodzi.Nyanja yakuya ija inasandukamadzi owuma gwaa kufika pansi. 9 Mdaniyo anati,“Ine ndidzawalondola, ndipo ndidzawagwira.Ndidzagawa chuma chawo;ndiye chokhumba changa chidzakwaniritsidwa.Ine ndidzasolola lupanga langa,ndi mkono wanga ndidzawawononga.” 10 Koma Inu munawuzira mphepo yanu,ndipo nyanja inawaphimba.Iwo anamira ngati chitsulomʼmadzi amphamvu. 11 Ndithu Yehova, pakati pa milungu,ndani afanana nanu? Inu amene muli woyera,ndiponso wotamandika wolemekezeka,chifukwa cha ntchito zanu,zazikulu ndi zodabwitsa? 12 Munatambasula dzanja lanu lamanjandipo dziko linawameza. 13 Ndi chikondi chanu chosasinthika mudzatsogoleraanthu amene munawawombola.Ndi mphamvu zanu munawatsogoleraku malo anu woyera. 14 Anthu amitundu ina anamva za mbiriyi ndipo ananjenjemera ndi mantha,mantha woopsa agwira anthu a dziko la Filisiti. 15 Tsopano mafumu a ku Edomu agwidwa ndi mantha aakulu,otsogolera a dziko la Mowabu akunjenjemera ndi mantha,ndipo anthu a ku Kanaani asungunuka ndi mantha. 16 Onse agwidwa ndi mantha woopsa.Popeza anaona mphamvu zanu zazikulu,iwo ayima chilili ngati mwala mpaka anthu anu,Inu Yehova atadutsa;inde mpaka atadutsa anthu amene munawagula. 17 Inu mudzawalowetsa ndi kuwakhazikitsapa phiri lanu.Pa malo pamene Inu Yehova munawapanga kuti muzikhalapo;malo wopatulika amene Inu Ambuye munawakonza ndi manja anu. 18 “Yehova adzalamulampaka muyaya.” 19 Akavalo a Farao, magaleta ndi oyendetsa akavalo atalowa mʼnyanja, Yehova anawabwezera madziwo mʼnyanja ndi kuwamiza, koma Aisraeli anawoloka nyanjayo powuma. 20 Ndipo Miriamu mneneri wamkazi, mlongo wa Aaroni anatenga zoyimbira ndipo akazi onse anamutsatira pambuyo, akuyimba ndi zoyimbira ndi kuvina. 21 Miriamu anawayimbira nyimbo iyi:“Imbirani Yehova,chifukwa iye wapambana.Kavalo ndi wokwerapo wakeIye wawamiza mʼnyanja.” 22 Ndipo Mose anatsogolera Israeli kuchoka ku nyanja yofiira ndi kupita ku chipululu cha Suri. Anayenda mʼchipululu masiku atatu wosapeza madzi. 23 Ndipo anafika ku Mara. Koma sanathe kumwa madzi akumeneko chifukwa anali owawa. (Ndi chifukwa chake malowo amatchedwa Mara). 24 Tsono anthu aja anadandaulira Mose ndi kumufunsa kuti, “Kodi tikumwa chiyani?” 25 Ndipo Mose anapemphera kwa Yehova, ndipo Yehova anamuonetsa kamtengo. Iye anakaponya mʼmadzimo ndipo madzi anakhala abwino.Kumeneko Yehova anawayikira lamulo ndi maweruziro. Kumenekonso Yehova anawayesa. 26 Yehova anati, “Ngati inu mudzamvetsa bwino mawu anga, kuchita zolungama, kumvera malamulo anga ndi kusamalitsa zimene ndikukuwuzani ndiye kuti Ine sindidzayika pa inu matenda amene ndinayika pa anthu a ku Igupto popeza ndine Yehova amene ndimakuchiritsani.” 27 Kenaka anafika ku Elimu, kumene kunali akasupe khumi ndi awiri ndi mitengo ya migwalangwa makumi asanu ndi awiri, ndipo anamanga misasa yawo kumeneko pafupi ndi madzi.
In Other Versions
Exodus 15 in the ANGEFD
Exodus 15 in the ANTPNG2D
Exodus 15 in the AS21
Exodus 15 in the BAGH
Exodus 15 in the BBPNG
Exodus 15 in the BBT1E
Exodus 15 in the BDS
Exodus 15 in the BEV
Exodus 15 in the BHAD
Exodus 15 in the BIB
Exodus 15 in the BLPT
Exodus 15 in the BNT
Exodus 15 in the BNTABOOT
Exodus 15 in the BNTLV
Exodus 15 in the BOATCB
Exodus 15 in the BOATCB2
Exodus 15 in the BOBCV
Exodus 15 in the BOCNT
Exodus 15 in the BOECS
Exodus 15 in the BOHCB
Exodus 15 in the BOHCV
Exodus 15 in the BOHLNT
Exodus 15 in the BOHNTLTAL
Exodus 15 in the BOICB
Exodus 15 in the BOILNTAP
Exodus 15 in the BOITCV
Exodus 15 in the BOKCV
Exodus 15 in the BOKCV2
Exodus 15 in the BOKHWOG
Exodus 15 in the BOKSSV
Exodus 15 in the BOLCB
Exodus 15 in the BOLCB2
Exodus 15 in the BOMCV
Exodus 15 in the BONAV
Exodus 15 in the BONCB
Exodus 15 in the BONLT
Exodus 15 in the BONUT2
Exodus 15 in the BOPLNT
Exodus 15 in the BOSCB
Exodus 15 in the BOSNC
Exodus 15 in the BOTLNT
Exodus 15 in the BOVCB
Exodus 15 in the BOYCB
Exodus 15 in the BPBB
Exodus 15 in the BPH
Exodus 15 in the BSB
Exodus 15 in the CCB
Exodus 15 in the CUV
Exodus 15 in the CUVS
Exodus 15 in the DBT
Exodus 15 in the DGDNT
Exodus 15 in the DHNT
Exodus 15 in the DNT
Exodus 15 in the ELBE
Exodus 15 in the EMTV
Exodus 15 in the ESV
Exodus 15 in the FBV
Exodus 15 in the FEB
Exodus 15 in the GGMNT
Exodus 15 in the GNT
Exodus 15 in the HARY
Exodus 15 in the HNT
Exodus 15 in the IRVA
Exodus 15 in the IRVB
Exodus 15 in the IRVG
Exodus 15 in the IRVH
Exodus 15 in the IRVK
Exodus 15 in the IRVM
Exodus 15 in the IRVM2
Exodus 15 in the IRVO
Exodus 15 in the IRVP
Exodus 15 in the IRVT
Exodus 15 in the IRVT2
Exodus 15 in the IRVU
Exodus 15 in the ISVN
Exodus 15 in the JSNT
Exodus 15 in the KAPI
Exodus 15 in the KBT1ETNIK
Exodus 15 in the KBV
Exodus 15 in the KJV
Exodus 15 in the KNFD
Exodus 15 in the LBA
Exodus 15 in the LBLA
Exodus 15 in the LNT
Exodus 15 in the LSV
Exodus 15 in the MAAL
Exodus 15 in the MBV
Exodus 15 in the MBV2
Exodus 15 in the MHNT
Exodus 15 in the MKNFD
Exodus 15 in the MNG
Exodus 15 in the MNT
Exodus 15 in the MNT2
Exodus 15 in the MRS1T
Exodus 15 in the NAA
Exodus 15 in the NASB
Exodus 15 in the NBLA
Exodus 15 in the NBS
Exodus 15 in the NBVTP
Exodus 15 in the NET2
Exodus 15 in the NIV11
Exodus 15 in the NNT
Exodus 15 in the NNT2
Exodus 15 in the NNT3
Exodus 15 in the PDDPT
Exodus 15 in the PFNT
Exodus 15 in the RMNT
Exodus 15 in the SBIAS
Exodus 15 in the SBIBS
Exodus 15 in the SBIBS2
Exodus 15 in the SBICS
Exodus 15 in the SBIDS
Exodus 15 in the SBIGS
Exodus 15 in the SBIHS
Exodus 15 in the SBIIS
Exodus 15 in the SBIIS2
Exodus 15 in the SBIIS3
Exodus 15 in the SBIKS
Exodus 15 in the SBIKS2
Exodus 15 in the SBIMS
Exodus 15 in the SBIOS
Exodus 15 in the SBIPS
Exodus 15 in the SBISS
Exodus 15 in the SBITS
Exodus 15 in the SBITS2
Exodus 15 in the SBITS3
Exodus 15 in the SBITS4
Exodus 15 in the SBIUS
Exodus 15 in the SBIVS
Exodus 15 in the SBT
Exodus 15 in the SBT1E
Exodus 15 in the SCHL
Exodus 15 in the SNT
Exodus 15 in the SUSU
Exodus 15 in the SUSU2
Exodus 15 in the SYNO
Exodus 15 in the TBIAOTANT
Exodus 15 in the TBT1E
Exodus 15 in the TBT1E2
Exodus 15 in the TFTIP
Exodus 15 in the TFTU
Exodus 15 in the TGNTATF3T
Exodus 15 in the THAI
Exodus 15 in the TNFD
Exodus 15 in the TNT
Exodus 15 in the TNTIK
Exodus 15 in the TNTIL
Exodus 15 in the TNTIN
Exodus 15 in the TNTIP
Exodus 15 in the TNTIZ
Exodus 15 in the TOMA
Exodus 15 in the TTENT
Exodus 15 in the UBG
Exodus 15 in the UGV
Exodus 15 in the UGV2
Exodus 15 in the UGV3
Exodus 15 in the VBL
Exodus 15 in the VDCC
Exodus 15 in the YALU
Exodus 15 in the YAPE
Exodus 15 in the YBVTP
Exodus 15 in the ZBP