Hosea 2 (BOGWICC)

1 “Nena kwa abale ako kuti, ‘Ndinu anthu anga,’ kwa alongo ako kuti ‘Ndinu okondedwa anga.’ ” 2 “Dzudzulani amayi anu, adzudzuleni iwo,pakuti si mkazi wanga,ndipo ine sindine mwamuna wake.Iyeyo achotse maonekedwe adama pa nkhope yake,ndi kusakhulupirika pa mawere ake. 3 Akapanda kutero ndidzamuvula,ndipo adzakhala wamaliseche monga tsiku limene anabadwa;ndidzamuwumitsa ngati chipululu,adzakhala ngati dziko lopanda madzi,ndi kumupha ndi ludzu. 4 Sindidzaonetsa chikondi changa pa ana ake,chifukwa ndi ana a mʼchiwerewere. 5 Amayi awo akhala akuchita zachiwerewerendipo anawabereka anawo akuchita zinthu zochititsa manyazi.Iwo anati, ‘Ine ndidzatsatira zibwenzi zanga,zimene zimandipatsa chakudya ndi madzi,ubweya ndi thonje, mafuta ndi chakumwa.’ 6 Choncho njira yake ndidzayitseka ndi minga;ndidzamuzinga ndi khoma kotero kuti sadzapezanso njira yotulukira. 7 Adzathamangira zibwenzi zake koma sadzazipeza;adzazifunafuna koma sadzazipeza.Pamenepo iye adzati,‘Ndibwerera kwa mwamuna wanga woyamba uja,pakuti ndinali pabwino ndi iyeyo kusiyanitsa ndi pano.’ 8 Iye sanazindikire kuti ndine amenendinkamupatsa tirigu, vinyo watsopano ndi mafuta.Ndine amene ndinkamukhuthulira siliva ndi golide,zimene ankapangira mafano a Baala. 9 “Choncho Ine ndidzamulanda tirigu wanga pa nthawi yokolola,ndi vinyo wanga watsopano pa nthawi yopsinya mphesa.Ndidzamulanda ubweya ndi thonje langa,zomwe akanaphimba nazo umaliseche wake. 10 Motero tsopano ndidzaonetsa maliseche akepamaso pa zibwenzi zake;palibe ndi mmodzi yemwe adzamupulumutse mʼmanja mwanga. 11 Ndidzathetsa zikondwerero zake zonse:zikondwerero zake za chaka ndi chaka, za mwezi watsopano,za pa masiku a Sabata ndi maphwando ake onse a pa masiku okhazikitsidwa. 12 Ndidzawononga mitengo yake ya mpesa ndi mitengo yake yamkuyu,imene iye ankanena kuti inali malipiro ake ochokera kwa zibwenzi zake.Ndidzayisandutsa chithukuluzi,ndipo zirombo zakuthengo zidzadya zipatsozo. 13 Ndidzamulanga chifukwa cha masikuamene anafukiza lubani kwa Abaala;anadzikongoletsa povala mphete ndi mikanda yamtengowapatalindipo anathamangira zibwenzi zake,koma Ine anandiyiwala,”akutero Yehova. 14 “Koma tsopano ndidzamukopa mkaziyo;ndidzapita naye ku chipululundipo ndidzamuyankhula mwachikondi. 15 Kumeneko ndidzamubwezera minda yake ya mpesa,ndipo ndidzasandutsa Chigwa cha Akori kukhala khomo la chiyembekezo.Kumeneko iye adzayimba nyimbo monga mʼmasiku a ubwana wake,monga tsiku limene anatuluka ku Igupto. 16 “Tsiku limeneli,” Yehova akuti,“udzandiyitana kuti, ‘Amuna anga;’sudzandiyitananso kuti, ‘Mbuye wanga.’ 17 Ndidzachotsa mayina a Abaala pakamwa pake;sadzatchulanso mayina awo popemphera. 18 Tsiku limenelo ndidzachita panganondi zirombo zakuthengo ndi mbalame zamumlengalengandiponso zolengedwa zokwawa pansi kuti ziyanjane ndi anthu anga.Ndidzachotsa mʼdzikomo uta,lupanga ndi zida zonse zankhondo,kuti onse apumule mwamtendere. 19 Ndidzakutomera kuti ukhale mkazi wanga mpaka muyaya;ndidzakutomera mwachilungamo, mwaungwiro,mwachikondi ndi mwachifundo. 20 Ndidzakutomera mokhulupirikandipo udzadziwa Yehova. 21 “Tsiku limenelo Ine ndidzayankha,”akutero Yehova.“Ndidzayankha mlengalenga pempho lake lofuna mitambondipo mvula idzagwa pa dziko lapansi; 22 ndipo nthaka idzamvera kupempha kwa tirigu,vinyo ndi mafuta,ndipo zidzamvera Yezireeli. 23 Ndidzadzala Israeli mʼdziko kuti akhale wanga:ndidzaonetsa chikondi changa kwa anthu amene ndinkawatchula dzina loti, ‘Sakondedwa.’Ndidzawawuza amene ndinkawatchula dzina loti, ‘Si anthu anga,’ kuti, ‘Ndinu anthu wanga;’ndipo adzanena kuti, ‘ndinu Mulungu wathu,’ ”

In Other Versions

Hosea 2 in the ANGEFD

Hosea 2 in the ANTPNG2D

Hosea 2 in the AS21

Hosea 2 in the BAGH

Hosea 2 in the BBPNG

Hosea 2 in the BBT1E

Hosea 2 in the BDS

Hosea 2 in the BEV

Hosea 2 in the BHAD

Hosea 2 in the BIB

Hosea 2 in the BLPT

Hosea 2 in the BNT

Hosea 2 in the BNTABOOT

Hosea 2 in the BNTLV

Hosea 2 in the BOATCB

Hosea 2 in the BOATCB2

Hosea 2 in the BOBCV

Hosea 2 in the BOCNT

Hosea 2 in the BOECS

Hosea 2 in the BOHCB

Hosea 2 in the BOHCV

Hosea 2 in the BOHLNT

Hosea 2 in the BOHNTLTAL

Hosea 2 in the BOICB

Hosea 2 in the BOILNTAP

Hosea 2 in the BOITCV

Hosea 2 in the BOKCV

Hosea 2 in the BOKCV2

Hosea 2 in the BOKHWOG

Hosea 2 in the BOKSSV

Hosea 2 in the BOLCB

Hosea 2 in the BOLCB2

Hosea 2 in the BOMCV

Hosea 2 in the BONAV

Hosea 2 in the BONCB

Hosea 2 in the BONLT

Hosea 2 in the BONUT2

Hosea 2 in the BOPLNT

Hosea 2 in the BOSCB

Hosea 2 in the BOSNC

Hosea 2 in the BOTLNT

Hosea 2 in the BOVCB

Hosea 2 in the BOYCB

Hosea 2 in the BPBB

Hosea 2 in the BPH

Hosea 2 in the BSB

Hosea 2 in the CCB

Hosea 2 in the CUV

Hosea 2 in the CUVS

Hosea 2 in the DBT

Hosea 2 in the DGDNT

Hosea 2 in the DHNT

Hosea 2 in the DNT

Hosea 2 in the ELBE

Hosea 2 in the EMTV

Hosea 2 in the ESV

Hosea 2 in the FBV

Hosea 2 in the FEB

Hosea 2 in the GGMNT

Hosea 2 in the GNT

Hosea 2 in the HARY

Hosea 2 in the HNT

Hosea 2 in the IRVA

Hosea 2 in the IRVB

Hosea 2 in the IRVG

Hosea 2 in the IRVH

Hosea 2 in the IRVK

Hosea 2 in the IRVM

Hosea 2 in the IRVM2

Hosea 2 in the IRVO

Hosea 2 in the IRVP

Hosea 2 in the IRVT

Hosea 2 in the IRVT2

Hosea 2 in the IRVU

Hosea 2 in the ISVN

Hosea 2 in the JSNT

Hosea 2 in the KAPI

Hosea 2 in the KBT1ETNIK

Hosea 2 in the KBV

Hosea 2 in the KJV

Hosea 2 in the KNFD

Hosea 2 in the LBA

Hosea 2 in the LBLA

Hosea 2 in the LNT

Hosea 2 in the LSV

Hosea 2 in the MAAL

Hosea 2 in the MBV

Hosea 2 in the MBV2

Hosea 2 in the MHNT

Hosea 2 in the MKNFD

Hosea 2 in the MNG

Hosea 2 in the MNT

Hosea 2 in the MNT2

Hosea 2 in the MRS1T

Hosea 2 in the NAA

Hosea 2 in the NASB

Hosea 2 in the NBLA

Hosea 2 in the NBS

Hosea 2 in the NBVTP

Hosea 2 in the NET2

Hosea 2 in the NIV11

Hosea 2 in the NNT

Hosea 2 in the NNT2

Hosea 2 in the NNT3

Hosea 2 in the PDDPT

Hosea 2 in the PFNT

Hosea 2 in the RMNT

Hosea 2 in the SBIAS

Hosea 2 in the SBIBS

Hosea 2 in the SBIBS2

Hosea 2 in the SBICS

Hosea 2 in the SBIDS

Hosea 2 in the SBIGS

Hosea 2 in the SBIHS

Hosea 2 in the SBIIS

Hosea 2 in the SBIIS2

Hosea 2 in the SBIIS3

Hosea 2 in the SBIKS

Hosea 2 in the SBIKS2

Hosea 2 in the SBIMS

Hosea 2 in the SBIOS

Hosea 2 in the SBIPS

Hosea 2 in the SBISS

Hosea 2 in the SBITS

Hosea 2 in the SBITS2

Hosea 2 in the SBITS3

Hosea 2 in the SBITS4

Hosea 2 in the SBIUS

Hosea 2 in the SBIVS

Hosea 2 in the SBT

Hosea 2 in the SBT1E

Hosea 2 in the SCHL

Hosea 2 in the SNT

Hosea 2 in the SUSU

Hosea 2 in the SUSU2

Hosea 2 in the SYNO

Hosea 2 in the TBIAOTANT

Hosea 2 in the TBT1E

Hosea 2 in the TBT1E2

Hosea 2 in the TFTIP

Hosea 2 in the TFTU

Hosea 2 in the TGNTATF3T

Hosea 2 in the THAI

Hosea 2 in the TNFD

Hosea 2 in the TNT

Hosea 2 in the TNTIK

Hosea 2 in the TNTIL

Hosea 2 in the TNTIN

Hosea 2 in the TNTIP

Hosea 2 in the TNTIZ

Hosea 2 in the TOMA

Hosea 2 in the TTENT

Hosea 2 in the UBG

Hosea 2 in the UGV

Hosea 2 in the UGV2

Hosea 2 in the UGV3

Hosea 2 in the VBL

Hosea 2 in the VDCC

Hosea 2 in the YALU

Hosea 2 in the YAPE

Hosea 2 in the YBVTP

Hosea 2 in the ZBP