Isaiah 38 (BOGWICC)
1 Nthawi imeneyo Mfumu Hezekiya anadwala ndipo anali pafupi kufa. Mneneri Yesaya mwana wa Amozi anapita kukamuona ndipo anati “Yehova akuti: Konza bwino nyumba yako, pakuti ukufa; suchira.” 2 Hezekiya anatembenuka nayangʼana kukhoma, napemphera kwa Yehova kuti, 3 “Inu Yehova, kumbukirani momwe ndayendera pamaso panu mokhulupirika ndi modzipereka ndipo ndakhala ndikuchita zabwino pamaso panu.” Ndipo Hezekiya analira mosweka mtima. 4 Ndipo Yehova analamula Yesaya kuti: 5 “Pita kwa Hezekiya ndipo ukamuwuze kuti, ‘Yehova, Mulungu wa kholo lake Davide akuti: Ndamva pemphero lako ndipo misozi yako ndayiona; ndidzakuwonjezera zaka 15 pa moyo wako. 6 Ndipo ndidzakupulumutsa, iwe pamodzi ndi mzindawu mʼdzanja la mfumu ya ku Asiriya, Ine ndidzawuteteza mzindawu. 7 “ ‘Ichi ndi chizindikiro cha Yehova kwa iwe kutsimikiza kuti Yehova adzachita zimene walonjeza: 8 Chithunzithunzi chimene dzuwa likuchititsa pa makwerero a Ahazi ndidzachibweza mʼmbuyo makwerero khumi.’ ” Ndipo chithunzithunzi chinabwerera mʼmbuyo makwerero khumi. 9 Ndakatulo ya Hezekiya mfumu ya ku Yuda imene analemba atadwala ndi kuchira: 10 Ine ndinaganiza kutindidzapita ku dziko la akufapamene moyo ukukoma. 11 Ndinaganiza kuti, “Sindidzaonanso Yehova,mʼdziko la anthu amoyo,sindidzaonanso mtundu wa anthukapena kukhala pamodzi ndi amene amakhala pa dziko lapansi lino. 12 Nyumba yanga yasasukandipo yachotsedwa.Ngati tenti ya mʼbusa mwapindapinda moyo wanga,ngati munthu wowomba nsalu;kuyambira usana mpaka usiku mwakhala mukundisiya. 13 Ndinkalira kupempha chithandizo usiku wonse mpaka mmawa;koma Inu Yehova munaphwanya mafupa anga ngati mkango,ndipo mwakhala mukundisiya. 14 Ndinkalira ngati namzeze kapena chumba,ndinkabuwula ngati nkhunda yodandaula.Maso anga anatopa nʼkuyangʼana mlengalenga.Inu Ambuye, ine ndili mʼmavuto bwerani mudzandithandize!” 15 Koma ine ndinganene chiyani?Yehova wayankhula nane, ndipo Iye ndiye wachita zimenezi.Chifukwa cha kuwawa kwa mtima wanga,ine ndidzayenda modzichepetsa masiku amoyo wanga onse. 16 Ambuye, masiku anga ali mʼmanja mwanu.Mzimu wanga upeza moyo mwa Inu.Munandichiritsa ndikundikhalitsa ndi moyo. 17 Ndithudi, ine ndinamva zowawa zoterekuti ndikhale ndi moyo;Inu munandisungakuti ndisapite ku dzenje la chiwonongekochifukwa mwakhululukiramachimo anga onse. 18 Pakuti akumanda sangathe kukutamandani,akufa sangayimbe nyimbo yokutamandani.Iwo amene akutsikira ku dzenjesangakukhulupirireni. 19 Amoyo, amoyo okha ndiwo amakutamandani,monga mmene ndikuchitira ine lero lino;abambo amawuza ana awo zakukhulupirika kwanu. 20 Yehova watipulumutsa.Tiyeni tiyimbe ndi zoyimbira za zingwemasiku onse a moyo wathumʼNyumba ya Yehova. 21 Yesaya anati, “Anthu atenge mʼbulu wankhunyu ndipo apake pa chithupsacho ndipo Hezekiya adzachira.” 22 Hezekiya nʼkuti atafunsa kuti, “Kodi chizindikiro chako nʼchiyani chotsimikiza kuti ndidzapita ku Nyumba ya Yehova?”
In Other Versions
Isaiah 38 in the ANGEFD
Isaiah 38 in the ANTPNG2D
Isaiah 38 in the AS21
Isaiah 38 in the BAGH
Isaiah 38 in the BBPNG
Isaiah 38 in the BBT1E
Isaiah 38 in the BDS
Isaiah 38 in the BEV
Isaiah 38 in the BHAD
Isaiah 38 in the BIB
Isaiah 38 in the BLPT
Isaiah 38 in the BNT
Isaiah 38 in the BNTABOOT
Isaiah 38 in the BNTLV
Isaiah 38 in the BOATCB
Isaiah 38 in the BOATCB2
Isaiah 38 in the BOBCV
Isaiah 38 in the BOCNT
Isaiah 38 in the BOECS
Isaiah 38 in the BOHCB
Isaiah 38 in the BOHCV
Isaiah 38 in the BOHLNT
Isaiah 38 in the BOHNTLTAL
Isaiah 38 in the BOICB
Isaiah 38 in the BOILNTAP
Isaiah 38 in the BOITCV
Isaiah 38 in the BOKCV
Isaiah 38 in the BOKCV2
Isaiah 38 in the BOKHWOG
Isaiah 38 in the BOKSSV
Isaiah 38 in the BOLCB
Isaiah 38 in the BOLCB2
Isaiah 38 in the BOMCV
Isaiah 38 in the BONAV
Isaiah 38 in the BONCB
Isaiah 38 in the BONLT
Isaiah 38 in the BONUT2
Isaiah 38 in the BOPLNT
Isaiah 38 in the BOSCB
Isaiah 38 in the BOSNC
Isaiah 38 in the BOTLNT
Isaiah 38 in the BOVCB
Isaiah 38 in the BOYCB
Isaiah 38 in the BPBB
Isaiah 38 in the BPH
Isaiah 38 in the BSB
Isaiah 38 in the CCB
Isaiah 38 in the CUV
Isaiah 38 in the CUVS
Isaiah 38 in the DBT
Isaiah 38 in the DGDNT
Isaiah 38 in the DHNT
Isaiah 38 in the DNT
Isaiah 38 in the ELBE
Isaiah 38 in the EMTV
Isaiah 38 in the ESV
Isaiah 38 in the FBV
Isaiah 38 in the FEB
Isaiah 38 in the GGMNT
Isaiah 38 in the GNT
Isaiah 38 in the HARY
Isaiah 38 in the HNT
Isaiah 38 in the IRVA
Isaiah 38 in the IRVB
Isaiah 38 in the IRVG
Isaiah 38 in the IRVH
Isaiah 38 in the IRVK
Isaiah 38 in the IRVM
Isaiah 38 in the IRVM2
Isaiah 38 in the IRVO
Isaiah 38 in the IRVP
Isaiah 38 in the IRVT
Isaiah 38 in the IRVT2
Isaiah 38 in the IRVU
Isaiah 38 in the ISVN
Isaiah 38 in the JSNT
Isaiah 38 in the KAPI
Isaiah 38 in the KBT1ETNIK
Isaiah 38 in the KBV
Isaiah 38 in the KJV
Isaiah 38 in the KNFD
Isaiah 38 in the LBA
Isaiah 38 in the LBLA
Isaiah 38 in the LNT
Isaiah 38 in the LSV
Isaiah 38 in the MAAL
Isaiah 38 in the MBV
Isaiah 38 in the MBV2
Isaiah 38 in the MHNT
Isaiah 38 in the MKNFD
Isaiah 38 in the MNG
Isaiah 38 in the MNT
Isaiah 38 in the MNT2
Isaiah 38 in the MRS1T
Isaiah 38 in the NAA
Isaiah 38 in the NASB
Isaiah 38 in the NBLA
Isaiah 38 in the NBS
Isaiah 38 in the NBVTP
Isaiah 38 in the NET2
Isaiah 38 in the NIV11
Isaiah 38 in the NNT
Isaiah 38 in the NNT2
Isaiah 38 in the NNT3
Isaiah 38 in the PDDPT
Isaiah 38 in the PFNT
Isaiah 38 in the RMNT
Isaiah 38 in the SBIAS
Isaiah 38 in the SBIBS
Isaiah 38 in the SBIBS2
Isaiah 38 in the SBICS
Isaiah 38 in the SBIDS
Isaiah 38 in the SBIGS
Isaiah 38 in the SBIHS
Isaiah 38 in the SBIIS
Isaiah 38 in the SBIIS2
Isaiah 38 in the SBIIS3
Isaiah 38 in the SBIKS
Isaiah 38 in the SBIKS2
Isaiah 38 in the SBIMS
Isaiah 38 in the SBIOS
Isaiah 38 in the SBIPS
Isaiah 38 in the SBISS
Isaiah 38 in the SBITS
Isaiah 38 in the SBITS2
Isaiah 38 in the SBITS3
Isaiah 38 in the SBITS4
Isaiah 38 in the SBIUS
Isaiah 38 in the SBIVS
Isaiah 38 in the SBT
Isaiah 38 in the SBT1E
Isaiah 38 in the SCHL
Isaiah 38 in the SNT
Isaiah 38 in the SUSU
Isaiah 38 in the SUSU2
Isaiah 38 in the SYNO
Isaiah 38 in the TBIAOTANT
Isaiah 38 in the TBT1E
Isaiah 38 in the TBT1E2
Isaiah 38 in the TFTIP
Isaiah 38 in the TFTU
Isaiah 38 in the TGNTATF3T
Isaiah 38 in the THAI
Isaiah 38 in the TNFD
Isaiah 38 in the TNT
Isaiah 38 in the TNTIK
Isaiah 38 in the TNTIL
Isaiah 38 in the TNTIN
Isaiah 38 in the TNTIP
Isaiah 38 in the TNTIZ
Isaiah 38 in the TOMA
Isaiah 38 in the TTENT
Isaiah 38 in the UBG
Isaiah 38 in the UGV
Isaiah 38 in the UGV2
Isaiah 38 in the UGV3
Isaiah 38 in the VBL
Isaiah 38 in the VDCC
Isaiah 38 in the YALU
Isaiah 38 in the YAPE
Isaiah 38 in the YBVTP
Isaiah 38 in the ZBP