Isaiah 57 (BOGWICC)
1 Anthu olungama amafa,ndipo palibe amene amalingalira mu mtima mwake;anthu odzipereka amatengedwa,ndipo palibe amene amamvetsa chifukwa chake.Anthu olungama amatengedwakuti tsoka lisawagwere. 2 Iwo amene amakhala moyo wolungamaamafa mwamtendere;amapeza mpumulo pamene agona mu imfa. 3 “Bwerani kuno, anthu ochita zoyipa,inu muli ngati zidzukulu za mkazi wachigololo ndi wadama! 4 Kodi inu mukuseka yani?Kodi mukumunena ndanindi kupotoza pakamwa panu?Kodi inu si ana owukira,zidzukulu za anthu abodza? 5 Inu mumapembedza mafano pamene mumalobodoka ndi zilakolako zanu pakati pa mitengo ya thundu,ndiponso pa tsinde pa mtengo uliwonse wa nthambi zambiri.Mumapereka ana anu ngati nsembe mu zigwandiponso mʼmingʼalu ya mʼmatanthwe. 6 Mafano a pakati pa miyala yosalala ya mu zigwa ndiye chuma chanu. Inde, ndiye gawo lanu.Mumapereka chopereka cha chakumwa kwa mafanowo,ndipo mumaperekanso chopereka cha chakudya.Kodi zimenezizingandichititse kuti ndikukomereni mtima? 7 Inu munayiwala bedi lanu pa phiri lalitali ndi looneka kutali.Mumapita kumeneko kukapereka nsembe zanu. 8 Mʼnyumba mwanu mwayikamafano kuseri kwa zitseko ndiponso pa mphuthu.Mwandisiya Ine, mwavula zovala zanu.Bedi lanu mwalikulitsa ndipo mwakwera ndi zibwenzi zanu,ndiye mwazilipira kuti mugone nazo.Kumene mwakwaniritsa zilakolako zanu zoyipa. 9 Mumapita kukapembedza fano la Moleki mutatenga mafutandi zonunkhira zochuluka.Munachita kutumiza akazembe anu kutali;inu ngakhale munapita ku manda kwenikweniko! 10 Inu mumatopa ndi maulendo anu,koma simunathe kunena kuti, ‘Nʼzopanda phindu.’Munapezako kumeneko zokhumba zanunʼchifukwa chake simunalefuke. 11 “Kodi ndani amene mwachita naye mantha ndi kumuopa,kotero kuti mwakhala mukundinamiza,ndipo Ine simundikumbukira nʼkomwe,kapena kuganizirapo mʼmitima yanu za Ine?Kodi mwaleka kundiopa chifukwa chotindakhala chete nthawi yayitali? 12 Koma ndaonetsa poyera ntchito zanu zomwe mumati nʼzolungama,ndi mafano anu kuti nʼzosathandiza. 13 Pamene mufuwula kupempha thandizo,mafano anu amene munasonkhanitsawo ndiyetu akupulumutseni!Mphepo idzanyamula mafano anu onsewo,mpweya chabe udzawulutsa mafanowo.Koma munthu amene amadalira ineadzalandira dziko lokhalamo.Phiri langa lopatulika lidzakhala lakelake.” 14 Ndipo panamveka mawu akuti,“Undani, undani, konzani msewu!Chotsani zotchinga pa njira yoyendamo anthu anga.” 15 Pakuti Iye amene ali Wamkulu ndi Wopambanazonse,amene alipo nthawi zonse, amene dzina lake ndi Woyerayo,akunena kuti, “Ndimakhala pamalo aulemu ndi opatulika,koma ndimakhalanso ndi munthu wodzichepetsa ndi wosweka mtimakuti odzichepetsawo ndiwalimbitsendi kuwachotsa mantha osweka mtima. 16 Sindidzawatsutsa anthu mpaka muyayakapena kuwapsera mtima nthawi zonse,popeza kuti ndinalenga anthu angandi kuwapatsa mpweya wamoyo. 17 Ine ndinakwiya kwambiri chifukwa cha tchimo lawo ladyera;ndinawalanga ndi kuwafulatira mokwiya,koma iwo anapitirirabe kuchita ntchito zawo zoyipa. 18 Ndaona zochita zawo, komabe ndidzawachiritsa;kuwapumulitsa ndi kuwapatsa mtendere, 19 anthu olira a mu Israeli adzanditamanda ndi milomo yawo.Anthu amene ali kutali ndi apafupi pomwe ndidzawapatsa mtendere,”“Ndipo ndidzawachiritsa.”Akutero Yehova. 20 Koma anthu oyipa ali ngati nyanja yowinduka,yosatha kukhala bata,mafunde ake amaponya matope ndi ndere. 21 “Palibe mtendere kwa oyipa,” akutero Mulungu wanga.
In Other Versions
Isaiah 57 in the ANGEFD
Isaiah 57 in the ANTPNG2D
Isaiah 57 in the AS21
Isaiah 57 in the BAGH
Isaiah 57 in the BBPNG
Isaiah 57 in the BBT1E
Isaiah 57 in the BDS
Isaiah 57 in the BEV
Isaiah 57 in the BHAD
Isaiah 57 in the BIB
Isaiah 57 in the BLPT
Isaiah 57 in the BNT
Isaiah 57 in the BNTABOOT
Isaiah 57 in the BNTLV
Isaiah 57 in the BOATCB
Isaiah 57 in the BOATCB2
Isaiah 57 in the BOBCV
Isaiah 57 in the BOCNT
Isaiah 57 in the BOECS
Isaiah 57 in the BOHCB
Isaiah 57 in the BOHCV
Isaiah 57 in the BOHLNT
Isaiah 57 in the BOHNTLTAL
Isaiah 57 in the BOICB
Isaiah 57 in the BOILNTAP
Isaiah 57 in the BOITCV
Isaiah 57 in the BOKCV
Isaiah 57 in the BOKCV2
Isaiah 57 in the BOKHWOG
Isaiah 57 in the BOKSSV
Isaiah 57 in the BOLCB
Isaiah 57 in the BOLCB2
Isaiah 57 in the BOMCV
Isaiah 57 in the BONAV
Isaiah 57 in the BONCB
Isaiah 57 in the BONLT
Isaiah 57 in the BONUT2
Isaiah 57 in the BOPLNT
Isaiah 57 in the BOSCB
Isaiah 57 in the BOSNC
Isaiah 57 in the BOTLNT
Isaiah 57 in the BOVCB
Isaiah 57 in the BOYCB
Isaiah 57 in the BPBB
Isaiah 57 in the BPH
Isaiah 57 in the BSB
Isaiah 57 in the CCB
Isaiah 57 in the CUV
Isaiah 57 in the CUVS
Isaiah 57 in the DBT
Isaiah 57 in the DGDNT
Isaiah 57 in the DHNT
Isaiah 57 in the DNT
Isaiah 57 in the ELBE
Isaiah 57 in the EMTV
Isaiah 57 in the ESV
Isaiah 57 in the FBV
Isaiah 57 in the FEB
Isaiah 57 in the GGMNT
Isaiah 57 in the GNT
Isaiah 57 in the HARY
Isaiah 57 in the HNT
Isaiah 57 in the IRVA
Isaiah 57 in the IRVB
Isaiah 57 in the IRVG
Isaiah 57 in the IRVH
Isaiah 57 in the IRVK
Isaiah 57 in the IRVM
Isaiah 57 in the IRVM2
Isaiah 57 in the IRVO
Isaiah 57 in the IRVP
Isaiah 57 in the IRVT
Isaiah 57 in the IRVT2
Isaiah 57 in the IRVU
Isaiah 57 in the ISVN
Isaiah 57 in the JSNT
Isaiah 57 in the KAPI
Isaiah 57 in the KBT1ETNIK
Isaiah 57 in the KBV
Isaiah 57 in the KJV
Isaiah 57 in the KNFD
Isaiah 57 in the LBA
Isaiah 57 in the LBLA
Isaiah 57 in the LNT
Isaiah 57 in the LSV
Isaiah 57 in the MAAL
Isaiah 57 in the MBV
Isaiah 57 in the MBV2
Isaiah 57 in the MHNT
Isaiah 57 in the MKNFD
Isaiah 57 in the MNG
Isaiah 57 in the MNT
Isaiah 57 in the MNT2
Isaiah 57 in the MRS1T
Isaiah 57 in the NAA
Isaiah 57 in the NASB
Isaiah 57 in the NBLA
Isaiah 57 in the NBS
Isaiah 57 in the NBVTP
Isaiah 57 in the NET2
Isaiah 57 in the NIV11
Isaiah 57 in the NNT
Isaiah 57 in the NNT2
Isaiah 57 in the NNT3
Isaiah 57 in the PDDPT
Isaiah 57 in the PFNT
Isaiah 57 in the RMNT
Isaiah 57 in the SBIAS
Isaiah 57 in the SBIBS
Isaiah 57 in the SBIBS2
Isaiah 57 in the SBICS
Isaiah 57 in the SBIDS
Isaiah 57 in the SBIGS
Isaiah 57 in the SBIHS
Isaiah 57 in the SBIIS
Isaiah 57 in the SBIIS2
Isaiah 57 in the SBIIS3
Isaiah 57 in the SBIKS
Isaiah 57 in the SBIKS2
Isaiah 57 in the SBIMS
Isaiah 57 in the SBIOS
Isaiah 57 in the SBIPS
Isaiah 57 in the SBISS
Isaiah 57 in the SBITS
Isaiah 57 in the SBITS2
Isaiah 57 in the SBITS3
Isaiah 57 in the SBITS4
Isaiah 57 in the SBIUS
Isaiah 57 in the SBIVS
Isaiah 57 in the SBT
Isaiah 57 in the SBT1E
Isaiah 57 in the SCHL
Isaiah 57 in the SNT
Isaiah 57 in the SUSU
Isaiah 57 in the SUSU2
Isaiah 57 in the SYNO
Isaiah 57 in the TBIAOTANT
Isaiah 57 in the TBT1E
Isaiah 57 in the TBT1E2
Isaiah 57 in the TFTIP
Isaiah 57 in the TFTU
Isaiah 57 in the TGNTATF3T
Isaiah 57 in the THAI
Isaiah 57 in the TNFD
Isaiah 57 in the TNT
Isaiah 57 in the TNTIK
Isaiah 57 in the TNTIL
Isaiah 57 in the TNTIN
Isaiah 57 in the TNTIP
Isaiah 57 in the TNTIZ
Isaiah 57 in the TOMA
Isaiah 57 in the TTENT
Isaiah 57 in the UBG
Isaiah 57 in the UGV
Isaiah 57 in the UGV2
Isaiah 57 in the UGV3
Isaiah 57 in the VBL
Isaiah 57 in the VDCC
Isaiah 57 in the YALU
Isaiah 57 in the YAPE
Isaiah 57 in the YBVTP
Isaiah 57 in the ZBP