Jeremiah 13 (BOGWICC)
1 Yehova anandiwuza kuti, “Pita kagule lamba wansalu yosalala ndipo ukavale mʼchiwuno mwako, koma usakamuviyike mʼmadzi.” 2 Choncho ndinakagula lambayo, monga momwe anandiwuzira Yehova, ndipo ndinamanga mʼchiwuno mwanga. 3 Kenaka Yehova anandiyankhulanso kachiwiri kuti, 4 “Tenga lamba amene unagula ndi kuvala mʼchiwuno mwako uja. Tsono pita ku mtsinje wa Yufurate ndipo ukamubise lambayo mʼmingʼalu ya mʼmatanthwe.” 5 Ndipo ndinapitadi ndi kukabisa lambayo ku Yufurate, monga anenera Yehova. 6 Patapita masiku ambiri Yehova anandiwuzanso kuti, “Pitanso ku Yufurate ndipo ukatenge lamba amene ndinakuwuza kuti ukamubise kumeneko.” 7 Choncho ndinapita ku Yufurate kukafukula lambayo ndi kumuchotsa pamalo pamene ndinamubisa, koma nthawi imeneyi nʼkuti lambayo atawonongeka kotheratu ndipo analibenso ntchito. 8 Pamenepo Yehova anandiwuza kuti, 9 “Izi ndi zimene ine ndikunena: ‘Umu ndi mmene ndidzawonongere zimene akunyadira kwambiri a ku Yuda ndi a ku Yerusalemu. 10 Anthuwa ndi oyipa. Iwo akana kumvera mawu anga. Mʼmalo mwake amawumirira kutsata milungu ina, kuyitumikira ndi kuyipembedza. Anthu amenewa adzakhala ngati lamba wopanda ntchitoyu. 11 Monga momwe lamba amakanirira mʼchiwuno cha munthu, momwemonso ndinakonza kuti nyumba yonse ya Israeli ndi nyumba yonse ya Yuda indikangamire Ine kuti akhale anthu anga, kuti azitamanda dzina langa ndi kulemekeza Ine. Koma iwo sanamvere,’ akutero Yehova. 12 “Awuze anthuwo kuti, ‘Yehova Mulungu wa Israeli akuti: Mtsuko uliwonse adzawudzaza ndi vinyo.’ Ndipo ngati iwo anena kwa iwe kuti, ‘Kodi ngati ife sitikudziwa kuti mtsuko uliwonse udzadzazidwa ndi vinyo?’ 13 Tsono iwe uwawuze kuti, Yehova akuti ‘Ine ndidzaledzeretsa anthu onse okhala mʼdziko muno, kuyambira mafumu amene amakhala pa mpando waufumu wa Davide, ansembe, aneneri, pamodzi ndi anthu onse amene akukhala mu Yerusalemu. 14 Ndidzawagundanitsa mitu kuti aphwanyane okhaokha ngati mitsuko, makolo ndi ana awo, akutero Yehova. Sindidzawamvera chisoni kapena kuwachitira chifundo kapena kukhudzidwa nawo kuti ndileke kuwawononga.’ ” 15 Imvani inu Aisraeli ndipo tcherani khutu,musadzitukumule,pakuti ndi Yehova amene akuyankhula. 16 Lemekezani Yehova Mulungu wanuasanagwetse mdima,mapazi anu asanayambe kupunthwamʼchisisira chamʼmapiri.Asanasandutse kuwalamukuyembekezerako kukhalamdima wandiweyani. 17 Koma ngati simumvera,ndidzalira kwambirichifukwa cha kunyada kwanu.Mʼmaso mwangamwadzaza ndi misozi yowawachifukwa nkhosa za Yehova zatengedwa ukapolo. 18 Uza mfumu pamodzi ndi amayi ake kuti,“Tsikani pa mipando yaufumuyo,pakuti zipewa zanu zaufumu zokongolazozagwa pansi.” 19 Mizinda ya ku Negevi yatsekedwandipo palibe wina woti nʼkuyitsekula.Yuda yense watengedwa kupita ku ukapolo,watengedwa yense ukapolo. 20 Tukula maso ako kuti uwoneamene akubwera kuchokera kumpoto.Kodi nkhosa zimene anakusungitsa zili kuti,nkhosa zanu zokongola zija? 21 Kodi udzanena chiyani pamene [Yehova] adzakuyikiraanthu amene unkanena kuti ndi abale ako akukugonjetsa ndi kukulamulira?Kodi sudzamva zowawangati za mayi pa nthawi yake yochira? 22 Ndipo ngati udzadzifunsa kuti,“Kodi zimenezi zandichitikira chifukwa chiyani?”Ndi chifukwa cha machimo anu ambirikuti zovala zanu zingʼambikendiponso kuti akuchitireni nkhanza. 23 Kodi wa dziko la Kusi nʼkusintha khungu lake,kapena kambuku kusintha mawanga ake?Inunso amene munazolowera kuchitazoyipa simungathe kusintha. 24 “Ine ndidzakumwazani ngati mankhusuamene amawuluka ndi mphepo ya ku chipululu. 25 Limeneli ndiye gawo lanu,chilango chimene ndakukonzeranichifukwa chondiyiwala Inendi kutumikira milungu yabodza,akutero Yehova. 26 Ine ndidzakwinya zovala zanu mpaka ku masokuti umaliseche wanu uwonekere. 27 Ndaona zonyansa zanu: zigololo zanu, kutchetcherera kwanundi ziwerewere zanu,zochitika pa mapiri ndi mʼminda.Tsoka iwe Yerusalemu!Udzakhala wosayeretsedwapa zachipembedzo mpaka liti?”
In Other Versions
Jeremiah 13 in the ANGEFD
Jeremiah 13 in the ANTPNG2D
Jeremiah 13 in the AS21
Jeremiah 13 in the BAGH
Jeremiah 13 in the BBPNG
Jeremiah 13 in the BBT1E
Jeremiah 13 in the BDS
Jeremiah 13 in the BEV
Jeremiah 13 in the BHAD
Jeremiah 13 in the BIB
Jeremiah 13 in the BLPT
Jeremiah 13 in the BNT
Jeremiah 13 in the BNTABOOT
Jeremiah 13 in the BNTLV
Jeremiah 13 in the BOATCB
Jeremiah 13 in the BOATCB2
Jeremiah 13 in the BOBCV
Jeremiah 13 in the BOCNT
Jeremiah 13 in the BOECS
Jeremiah 13 in the BOHCB
Jeremiah 13 in the BOHCV
Jeremiah 13 in the BOHLNT
Jeremiah 13 in the BOHNTLTAL
Jeremiah 13 in the BOICB
Jeremiah 13 in the BOILNTAP
Jeremiah 13 in the BOITCV
Jeremiah 13 in the BOKCV
Jeremiah 13 in the BOKCV2
Jeremiah 13 in the BOKHWOG
Jeremiah 13 in the BOKSSV
Jeremiah 13 in the BOLCB
Jeremiah 13 in the BOLCB2
Jeremiah 13 in the BOMCV
Jeremiah 13 in the BONAV
Jeremiah 13 in the BONCB
Jeremiah 13 in the BONLT
Jeremiah 13 in the BONUT2
Jeremiah 13 in the BOPLNT
Jeremiah 13 in the BOSCB
Jeremiah 13 in the BOSNC
Jeremiah 13 in the BOTLNT
Jeremiah 13 in the BOVCB
Jeremiah 13 in the BOYCB
Jeremiah 13 in the BPBB
Jeremiah 13 in the BPH
Jeremiah 13 in the BSB
Jeremiah 13 in the CCB
Jeremiah 13 in the CUV
Jeremiah 13 in the CUVS
Jeremiah 13 in the DBT
Jeremiah 13 in the DGDNT
Jeremiah 13 in the DHNT
Jeremiah 13 in the DNT
Jeremiah 13 in the ELBE
Jeremiah 13 in the EMTV
Jeremiah 13 in the ESV
Jeremiah 13 in the FBV
Jeremiah 13 in the FEB
Jeremiah 13 in the GGMNT
Jeremiah 13 in the GNT
Jeremiah 13 in the HARY
Jeremiah 13 in the HNT
Jeremiah 13 in the IRVA
Jeremiah 13 in the IRVB
Jeremiah 13 in the IRVG
Jeremiah 13 in the IRVH
Jeremiah 13 in the IRVK
Jeremiah 13 in the IRVM
Jeremiah 13 in the IRVM2
Jeremiah 13 in the IRVO
Jeremiah 13 in the IRVP
Jeremiah 13 in the IRVT
Jeremiah 13 in the IRVT2
Jeremiah 13 in the IRVU
Jeremiah 13 in the ISVN
Jeremiah 13 in the JSNT
Jeremiah 13 in the KAPI
Jeremiah 13 in the KBT1ETNIK
Jeremiah 13 in the KBV
Jeremiah 13 in the KJV
Jeremiah 13 in the KNFD
Jeremiah 13 in the LBA
Jeremiah 13 in the LBLA
Jeremiah 13 in the LNT
Jeremiah 13 in the LSV
Jeremiah 13 in the MAAL
Jeremiah 13 in the MBV
Jeremiah 13 in the MBV2
Jeremiah 13 in the MHNT
Jeremiah 13 in the MKNFD
Jeremiah 13 in the MNG
Jeremiah 13 in the MNT
Jeremiah 13 in the MNT2
Jeremiah 13 in the MRS1T
Jeremiah 13 in the NAA
Jeremiah 13 in the NASB
Jeremiah 13 in the NBLA
Jeremiah 13 in the NBS
Jeremiah 13 in the NBVTP
Jeremiah 13 in the NET2
Jeremiah 13 in the NIV11
Jeremiah 13 in the NNT
Jeremiah 13 in the NNT2
Jeremiah 13 in the NNT3
Jeremiah 13 in the PDDPT
Jeremiah 13 in the PFNT
Jeremiah 13 in the RMNT
Jeremiah 13 in the SBIAS
Jeremiah 13 in the SBIBS
Jeremiah 13 in the SBIBS2
Jeremiah 13 in the SBICS
Jeremiah 13 in the SBIDS
Jeremiah 13 in the SBIGS
Jeremiah 13 in the SBIHS
Jeremiah 13 in the SBIIS
Jeremiah 13 in the SBIIS2
Jeremiah 13 in the SBIIS3
Jeremiah 13 in the SBIKS
Jeremiah 13 in the SBIKS2
Jeremiah 13 in the SBIMS
Jeremiah 13 in the SBIOS
Jeremiah 13 in the SBIPS
Jeremiah 13 in the SBISS
Jeremiah 13 in the SBITS
Jeremiah 13 in the SBITS2
Jeremiah 13 in the SBITS3
Jeremiah 13 in the SBITS4
Jeremiah 13 in the SBIUS
Jeremiah 13 in the SBIVS
Jeremiah 13 in the SBT
Jeremiah 13 in the SBT1E
Jeremiah 13 in the SCHL
Jeremiah 13 in the SNT
Jeremiah 13 in the SUSU
Jeremiah 13 in the SUSU2
Jeremiah 13 in the SYNO
Jeremiah 13 in the TBIAOTANT
Jeremiah 13 in the TBT1E
Jeremiah 13 in the TBT1E2
Jeremiah 13 in the TFTIP
Jeremiah 13 in the TFTU
Jeremiah 13 in the TGNTATF3T
Jeremiah 13 in the THAI
Jeremiah 13 in the TNFD
Jeremiah 13 in the TNT
Jeremiah 13 in the TNTIK
Jeremiah 13 in the TNTIL
Jeremiah 13 in the TNTIN
Jeremiah 13 in the TNTIP
Jeremiah 13 in the TNTIZ
Jeremiah 13 in the TOMA
Jeremiah 13 in the TTENT
Jeremiah 13 in the UBG
Jeremiah 13 in the UGV
Jeremiah 13 in the UGV2
Jeremiah 13 in the UGV3
Jeremiah 13 in the VBL
Jeremiah 13 in the VDCC
Jeremiah 13 in the YALU
Jeremiah 13 in the YAPE
Jeremiah 13 in the YBVTP
Jeremiah 13 in the ZBP