2 Timothy 1 (BOGWICC)
1 Paulo mtumwi wa Khristu Yesu mwa chifuniro cha Mulungu. Anandituma kuti ndilalike za lonjezo la moyo umene uli mwa Khristu Yesu. 2 Kwa Timoteyo, mwana wanga wokondedwa:Chisomo, chifundo ndi mtendere zochokera kwa Mulungu Atate ndi Ambuye athu Yesu Khristu. 3 Ndikuyamika Mulungu amene ndimamutumikira ndi chikumbumtima chosatsutsika, monga momwe ankachitira makolo anga. Usiku ndi usana ndimakukumbukira mosalekeza mʼmapemphero anga. 4 Ndikamakumbukira misozi yako, ndimalakalaka nditakuona kuti ndidzazidwe ndi chimwemwe. 5 Ndakumbukira za chikhulupiriro chako choona chimene chinayamba mwa agogo ako a Loisi ndi mwa amayi ako Yunike ndipo ndikutsimikiza mtima kuti chilinso mwa iwe. 6 Nʼchifukwa chake ndikukukumbutsa kuti upemerere monga amachitira moto, mphatso imene Mulungu anakupatsa nditakusanjika manja. 7 Pakuti Mzimu amene Mulungu anatipatsa, si Mzimu wotipatsa manyazi, koma Mzimu wotipatsa mphamvu, chikondi ndi kudzisunga. 8 Choncho usachite manyazi kuchitira umboni Ambuye athu, kapena kuchita manyazi chifukwa cha ine wamʼndende. Koma umve nane zowawa chifukwa cha Uthenga Wabwino, mothandizidwa ndi mphamvu za Mulungu. 9 Iye anatipulumutsa ndipo anatiyitanira ku moyo oyera mtima, osati chifukwa cha chilichonse chimene tinachita, koma chifukwa cha chikonzero ndi chisomo chake. Chisomo chimenechi anatipatsa ife mwa Khristu Yesu nthawi isanayambe. 10 Koma tsopano Mulungu watiwululira kudzera mʼkuoneka kwa Mpulumutsi wathu, Khristu Yesu, amene anathetsa mphamvu za imfa ndipo mwa Uthenga Wabwino anaonetsa poyera moyo umene sungafe. 11 Ine ndinasankhidwa kukhala wamthenga, ndi mtumwi ndi mphunzitsi wa Uthenga Wabwinowu. 12 Nʼchifukwa chake ndikuvutika monga ndililimu. Komabe zimenezi sizikundichititsa manyazi, popeza ndikumudziwa amene ndamukhulupirira ndipo ndikutsimikiza mtima kuti akhoza kusamalira chimene ndinamusungitsa mpaka tsiku lijalo. 13 Zimene unamva kwa ine, uzisunge kuti zikhale chitsanzo cha chiphunzitso choona, mwa chikhulupiriro ndi chikondi mwa Khristu Yesu. 14 Samalira bwino zokoma zimene anakusungitsa. Uzisamalire mothandizidwa ndi Mzimu Woyera amene amakhala mwa ife. 15 Iwe udziwa kuti onse a mʼchigawo cha Asiya anandithawa, kuphatikizapo Fugelo ndi Herimogene omwe. 16 Mulungu achitire chifundo banja lonse la Onesiforo chifukwa ankandisangalatsa kawirikawiri ndipo sankachita nane manyazi ngakhale ndinali womangidwa ndi maunyolo. 17 Mʼmalo mwake, atangofika ku Roma, anandifunafuna ndipo anandipeza. 18 Ambuye amulole kuti adzalandire chifundo kwa Ambuye pa tsiku lijalo! Ukudziwa bwino momwe iye anandithandizira mʼnjira zosiyanasiyana ku Efeso.
In Other Versions
2 Timothy 1 in the ANGEFD
2 Timothy 1 in the ANTPNG2D
2 Timothy 1 in the AS21
2 Timothy 1 in the BAGH
2 Timothy 1 in the BBPNG
2 Timothy 1 in the BBT1E
2 Timothy 1 in the BDS
2 Timothy 1 in the BEV
2 Timothy 1 in the BHAD
2 Timothy 1 in the BIB
2 Timothy 1 in the BLPT
2 Timothy 1 in the BNT
2 Timothy 1 in the BNTABOOT
2 Timothy 1 in the BNTLV
2 Timothy 1 in the BOATCB
2 Timothy 1 in the BOATCB2
2 Timothy 1 in the BOBCV
2 Timothy 1 in the BOCNT
2 Timothy 1 in the BOECS
2 Timothy 1 in the BOHCB
2 Timothy 1 in the BOHCV
2 Timothy 1 in the BOHLNT
2 Timothy 1 in the BOHNTLTAL
2 Timothy 1 in the BOICB
2 Timothy 1 in the BOILNTAP
2 Timothy 1 in the BOITCV
2 Timothy 1 in the BOKCV
2 Timothy 1 in the BOKCV2
2 Timothy 1 in the BOKHWOG
2 Timothy 1 in the BOKSSV
2 Timothy 1 in the BOLCB
2 Timothy 1 in the BOLCB2
2 Timothy 1 in the BOMCV
2 Timothy 1 in the BONAV
2 Timothy 1 in the BONCB
2 Timothy 1 in the BONLT
2 Timothy 1 in the BONUT2
2 Timothy 1 in the BOPLNT
2 Timothy 1 in the BOSCB
2 Timothy 1 in the BOSNC
2 Timothy 1 in the BOTLNT
2 Timothy 1 in the BOVCB
2 Timothy 1 in the BOYCB
2 Timothy 1 in the BPBB
2 Timothy 1 in the BPH
2 Timothy 1 in the BSB
2 Timothy 1 in the CCB
2 Timothy 1 in the CUV
2 Timothy 1 in the CUVS
2 Timothy 1 in the DBT
2 Timothy 1 in the DGDNT
2 Timothy 1 in the DHNT
2 Timothy 1 in the DNT
2 Timothy 1 in the ELBE
2 Timothy 1 in the EMTV
2 Timothy 1 in the ESV
2 Timothy 1 in the FBV
2 Timothy 1 in the FEB
2 Timothy 1 in the GGMNT
2 Timothy 1 in the GNT
2 Timothy 1 in the HARY
2 Timothy 1 in the HNT
2 Timothy 1 in the IRVA
2 Timothy 1 in the IRVB
2 Timothy 1 in the IRVG
2 Timothy 1 in the IRVH
2 Timothy 1 in the IRVK
2 Timothy 1 in the IRVM
2 Timothy 1 in the IRVM2
2 Timothy 1 in the IRVO
2 Timothy 1 in the IRVP
2 Timothy 1 in the IRVT
2 Timothy 1 in the IRVT2
2 Timothy 1 in the IRVU
2 Timothy 1 in the ISVN
2 Timothy 1 in the JSNT
2 Timothy 1 in the KAPI
2 Timothy 1 in the KBT1ETNIK
2 Timothy 1 in the KBV
2 Timothy 1 in the KJV
2 Timothy 1 in the KNFD
2 Timothy 1 in the LBA
2 Timothy 1 in the LBLA
2 Timothy 1 in the LNT
2 Timothy 1 in the LSV
2 Timothy 1 in the MAAL
2 Timothy 1 in the MBV
2 Timothy 1 in the MBV2
2 Timothy 1 in the MHNT
2 Timothy 1 in the MKNFD
2 Timothy 1 in the MNG
2 Timothy 1 in the MNT
2 Timothy 1 in the MNT2
2 Timothy 1 in the MRS1T
2 Timothy 1 in the NAA
2 Timothy 1 in the NASB
2 Timothy 1 in the NBLA
2 Timothy 1 in the NBS
2 Timothy 1 in the NBVTP
2 Timothy 1 in the NET2
2 Timothy 1 in the NIV11
2 Timothy 1 in the NNT
2 Timothy 1 in the NNT2
2 Timothy 1 in the NNT3
2 Timothy 1 in the PDDPT
2 Timothy 1 in the PFNT
2 Timothy 1 in the RMNT
2 Timothy 1 in the SBIAS
2 Timothy 1 in the SBIBS
2 Timothy 1 in the SBIBS2
2 Timothy 1 in the SBICS
2 Timothy 1 in the SBIDS
2 Timothy 1 in the SBIGS
2 Timothy 1 in the SBIHS
2 Timothy 1 in the SBIIS
2 Timothy 1 in the SBIIS2
2 Timothy 1 in the SBIIS3
2 Timothy 1 in the SBIKS
2 Timothy 1 in the SBIKS2
2 Timothy 1 in the SBIMS
2 Timothy 1 in the SBIOS
2 Timothy 1 in the SBIPS
2 Timothy 1 in the SBISS
2 Timothy 1 in the SBITS
2 Timothy 1 in the SBITS2
2 Timothy 1 in the SBITS3
2 Timothy 1 in the SBITS4
2 Timothy 1 in the SBIUS
2 Timothy 1 in the SBIVS
2 Timothy 1 in the SBT
2 Timothy 1 in the SBT1E
2 Timothy 1 in the SCHL
2 Timothy 1 in the SNT
2 Timothy 1 in the SUSU
2 Timothy 1 in the SUSU2
2 Timothy 1 in the SYNO
2 Timothy 1 in the TBIAOTANT
2 Timothy 1 in the TBT1E
2 Timothy 1 in the TBT1E2
2 Timothy 1 in the TFTIP
2 Timothy 1 in the TFTU
2 Timothy 1 in the TGNTATF3T
2 Timothy 1 in the THAI
2 Timothy 1 in the TNFD
2 Timothy 1 in the TNT
2 Timothy 1 in the TNTIK
2 Timothy 1 in the TNTIL
2 Timothy 1 in the TNTIN
2 Timothy 1 in the TNTIP
2 Timothy 1 in the TNTIZ
2 Timothy 1 in the TOMA
2 Timothy 1 in the TTENT
2 Timothy 1 in the UBG
2 Timothy 1 in the UGV
2 Timothy 1 in the UGV2
2 Timothy 1 in the UGV3
2 Timothy 1 in the VBL
2 Timothy 1 in the VDCC
2 Timothy 1 in the YALU
2 Timothy 1 in the YAPE
2 Timothy 1 in the YBVTP
2 Timothy 1 in the ZBP