Revelation 7 (BOGWICC)
1 Zitatha izi ndinaona angelo anayi atayima pa mbali zinayi za dziko lapansi, atagwira mphepo zinayi za dziko lapansi kuletsa kuti mphepo iliyonse isawombe pa dziko kapena pa nyanja kapena pa mtengo uliwonse. 2 Kenaka ndinaona mngelo wina akuchokera kummawa, ali ndi chidindo cha Mulungu wamoyo. Iye anafuwulira angelo anayi aja amene anapatsidwa mphamvu yowononga dziko ndi nyanja kuti, 3 “Musawononge dziko, nyanja ndi mitengo kufikira titalemba chizindikiro pa mphumi za atumiki a Mulungu wathu.” 4 Choncho ndinamva chiwerengero cha amene ankayenera kulembedwa chizindikiro aja. Analipo okwanira 144,000 kuchokera ku mafuko onse a Israeli. 5 Ochokera fuko la Yuda analipo 12,000 amene analembedwa chizindikiro.Ochokera fuko la Rubeni analipo 12,000;ochokera fuko la Gadi analipo 12,000; 6 ochokera fuko la Aseri analipo 12,000;ochokera fuko la Nafutali analipo 12,000;ochokera fuko la Manase analipo 12,000; 7 ochokera fuko la Simeoni analipo 12,000;ochokera fuko la Levi analipo 12,000;ochokera fuko la Isakara analipo 12,000; 8 ochokera fuko la Zebuloni analipo 12,000;ochokera fuko la Yosefe analipo 12,000;ochokera fuko la Benjamini analipo 12,000. 9 Zitatha izi ndinayangʼana patsogolo panga ndipo ndinaona gulu lalikulu la anthu loti munthu sangathe kuliwerenga lochokera dziko lililonse, fuko lililonse, mtundu wa anthu uliwonse ndi chiyankhulo chilichonse, atayima patsogolo pa mpando waufumu, pamaso pa Mwana Wankhosa. Iwo anali atavala mikanjo yoyera ndi kunyamula nthambi za kanjedza mʼmanja mwawo. 10 Ndipo ankafuwula mokweza kuti:“Chipulumutso chimachokera kwa Mulungu wathu,wokhala pa mpando waufumundi kwa Mwana Wankhosa.” 11 “Angelo onse anayimirira kuzungulira mpando waufumu uja, kuzunguliranso akuluakulu aja ndi zamoyo zinayi zija. Angelo aja anadzigwetsa pansi chafufumimba patsogolo pa mpando waufumu napembedza Mulungu. 12 Iwo anati,“Ameni!Matamando ndi ulemerero,nzeru, mayamiko, ulemu,ulamuliro ndi mphamvuzikhale kwa Mulungu wathu kunthawi zanthawi,Ameni!” 13 Pamenepo mmodzi wa akuluakulu aja anandifunsa kuti, “Kodi avala mikanjo yoyerawa ndani ndipo akuchokera kuti?” 14 Ine ndinayankha kuti, “Mbuye wanga mukudziwa ndinu.”Tsono iye anandiwuza kuti, “Amenewa ndi amene anatuluka mʼmazunzo aakulu aja. Anachapa mikanjo yawo naziyeretsa mʼmagazi a Mwana Wankhosa. 15 Nʼchifukwa chake,“iwowa ali patsogolo pa mpando waufumu wa Mulungundipo akutumikira usana ndi usiku mʼNyumba ya Mulungu;ndipo Iye wokhala pa mpando waufumuadzawaphimba ndi tenti yake. 16 ‘Iwowa sadzamvanso njala,sadzamvanso ludzu,dzuwa kapena kutentha kulikonsesikudzawawotcha.’ 17 Pakuti Mwana Wankhosa amene ali pakati pa mpando waufumuadzakhala mʼbusa wawo.‘Iye adzawatsogolera ku akasupe a madzi amoyo.’‘Ndipo Mulungu adzawapukuta misozi yonse mʼmaso mwawo.’ ”
In Other Versions
Revelation 7 in the ANGEFD
Revelation 7 in the ANTPNG2D
Revelation 7 in the AS21
Revelation 7 in the BAGH
Revelation 7 in the BBPNG
Revelation 7 in the BBT1E
Revelation 7 in the BDS
Revelation 7 in the BEV
Revelation 7 in the BHAD
Revelation 7 in the BIB
Revelation 7 in the BLPT
Revelation 7 in the BNT
Revelation 7 in the BNTABOOT
Revelation 7 in the BNTLV
Revelation 7 in the BOATCB
Revelation 7 in the BOATCB2
Revelation 7 in the BOBCV
Revelation 7 in the BOCNT
Revelation 7 in the BOECS
Revelation 7 in the BOHCB
Revelation 7 in the BOHCV
Revelation 7 in the BOHLNT
Revelation 7 in the BOHNTLTAL
Revelation 7 in the BOICB
Revelation 7 in the BOILNTAP
Revelation 7 in the BOITCV
Revelation 7 in the BOKCV
Revelation 7 in the BOKCV2
Revelation 7 in the BOKHWOG
Revelation 7 in the BOKSSV
Revelation 7 in the BOLCB
Revelation 7 in the BOLCB2
Revelation 7 in the BOMCV
Revelation 7 in the BONAV
Revelation 7 in the BONCB
Revelation 7 in the BONLT
Revelation 7 in the BONUT2
Revelation 7 in the BOPLNT
Revelation 7 in the BOSCB
Revelation 7 in the BOSNC
Revelation 7 in the BOTLNT
Revelation 7 in the BOVCB
Revelation 7 in the BOYCB
Revelation 7 in the BPBB
Revelation 7 in the BPH
Revelation 7 in the BSB
Revelation 7 in the CCB
Revelation 7 in the CUV
Revelation 7 in the CUVS
Revelation 7 in the DBT
Revelation 7 in the DGDNT
Revelation 7 in the DHNT
Revelation 7 in the DNT
Revelation 7 in the ELBE
Revelation 7 in the EMTV
Revelation 7 in the ESV
Revelation 7 in the FBV
Revelation 7 in the FEB
Revelation 7 in the GGMNT
Revelation 7 in the GNT
Revelation 7 in the HARY
Revelation 7 in the HNT
Revelation 7 in the IRVA
Revelation 7 in the IRVB
Revelation 7 in the IRVG
Revelation 7 in the IRVH
Revelation 7 in the IRVK
Revelation 7 in the IRVM
Revelation 7 in the IRVM2
Revelation 7 in the IRVO
Revelation 7 in the IRVP
Revelation 7 in the IRVT
Revelation 7 in the IRVT2
Revelation 7 in the IRVU
Revelation 7 in the ISVN
Revelation 7 in the JSNT
Revelation 7 in the KAPI
Revelation 7 in the KBT1ETNIK
Revelation 7 in the KBV
Revelation 7 in the KJV
Revelation 7 in the KNFD
Revelation 7 in the LBA
Revelation 7 in the LBLA
Revelation 7 in the LNT
Revelation 7 in the LSV
Revelation 7 in the MAAL
Revelation 7 in the MBV
Revelation 7 in the MBV2
Revelation 7 in the MHNT
Revelation 7 in the MKNFD
Revelation 7 in the MNG
Revelation 7 in the MNT
Revelation 7 in the MNT2
Revelation 7 in the MRS1T
Revelation 7 in the NAA
Revelation 7 in the NASB
Revelation 7 in the NBLA
Revelation 7 in the NBS
Revelation 7 in the NBVTP
Revelation 7 in the NET2
Revelation 7 in the NIV11
Revelation 7 in the NNT
Revelation 7 in the NNT2
Revelation 7 in the NNT3
Revelation 7 in the PDDPT
Revelation 7 in the PFNT
Revelation 7 in the RMNT
Revelation 7 in the SBIAS
Revelation 7 in the SBIBS
Revelation 7 in the SBIBS2
Revelation 7 in the SBICS
Revelation 7 in the SBIDS
Revelation 7 in the SBIGS
Revelation 7 in the SBIHS
Revelation 7 in the SBIIS
Revelation 7 in the SBIIS2
Revelation 7 in the SBIIS3
Revelation 7 in the SBIKS
Revelation 7 in the SBIKS2
Revelation 7 in the SBIMS
Revelation 7 in the SBIOS
Revelation 7 in the SBIPS
Revelation 7 in the SBISS
Revelation 7 in the SBITS
Revelation 7 in the SBITS2
Revelation 7 in the SBITS3
Revelation 7 in the SBITS4
Revelation 7 in the SBIUS
Revelation 7 in the SBIVS
Revelation 7 in the SBT
Revelation 7 in the SBT1E
Revelation 7 in the SCHL
Revelation 7 in the SNT
Revelation 7 in the SUSU
Revelation 7 in the SUSU2
Revelation 7 in the SYNO
Revelation 7 in the TBIAOTANT
Revelation 7 in the TBT1E
Revelation 7 in the TBT1E2
Revelation 7 in the TFTIP
Revelation 7 in the TFTU
Revelation 7 in the TGNTATF3T
Revelation 7 in the THAI
Revelation 7 in the TNFD
Revelation 7 in the TNT
Revelation 7 in the TNTIK
Revelation 7 in the TNTIL
Revelation 7 in the TNTIN
Revelation 7 in the TNTIP
Revelation 7 in the TNTIZ
Revelation 7 in the TOMA
Revelation 7 in the TTENT
Revelation 7 in the UBG
Revelation 7 in the UGV
Revelation 7 in the UGV2
Revelation 7 in the UGV3
Revelation 7 in the VBL
Revelation 7 in the VDCC
Revelation 7 in the YALU
Revelation 7 in the YAPE
Revelation 7 in the YBVTP
Revelation 7 in the ZBP