Zephaniah 2 (BOGWICC)
1 Sonkhanani pamodzi, sonkhanani pamodzi,inu mtundu wochititsa manyazi, 2 isanafike nthawi yachiweruzo,nthawi yanu isanawuluke ngati mungu,usanakufikeni mkwiyo woopsa wa Yehova,tsiku la ukali wa Yehova lisanafike pa inu. 3 Funafunani Yehova, inu nonse odzichepetsa a mʼdziko,inu amene mumachita zimene amakulamulani.Funafunani chilungamo, funafunani kudzichepetsa;mwina mudzatetezedwapa tsiku la mkwiyo wa Yehova. 4 Gaza adzasiyidwandipo Asikeloni adzasanduka bwinja.Nthawi yamasana Asidodi adzakhala wopanda anthundipo Ekroni adzazulidwa. 5 Tsoka inu okhala mʼmbali mwa nyanja,inu mtundu wa Akereti;mawu a Yehova akutsutsaiwe Kanaani, dziko la Afilisti.“Ndidzakuwonongandipo palibe amene adzatsale.” 6 Dziko la mʼmbali mwa nyanja, kumene kumakhala Akereti,lidzakhala malo a abusa ndi la makola a nkhosa. 7 Malowa adzakhala a anthu otsala a nyumba ya Yuda;adzapezako msipu.Nthawi ya madzulo adzagonamʼnyumba za Asikeloni.Yehova Mulungu wawo adzawasamalira;adzabwezeretsa mtendere wawo. 8 “Ndamva kunyoza kwa Mowabundi chipongwe cha Amoni,amene ananyoza anthu angandi kuopseza kuti alanda dziko lawo. 9 Choncho, pali Ine Wamoyo,”akutero Yehova Wamphamvuzonse, Mulungu wa Israeli,“Ndithu, Mowabu adzasanduka ngati Sodomu,Amoni adzasanduka ngati Gomora;malo a zomeramera ndi maenje a mchere,dziko la bwinja mpaka muyaya.Anthu anga otsala adzawafunkha;opulumuka a mtundu wanga adzalandira dziko lawo.” 10 Ichi ndi chimene adzalandire chifukwa cha kunyada kwawo,chifukwa chonyoza ndi kuchitira chipongwe anthu a Yehova Wamphamvuzonse. 11 Yehova adzawachititsa mantha kwambiripamene adzawononga milungu yonse ya mʼdzikomo.Ndipo mitundu ya anthu pa dziko lonse idzamulambira,uliwonse ku dziko la kwawo. 12 “Inunso anthu a ku Kusi,mudzaphedwa ndi lupanga.” 13 Yehova adzatambasulira dzanja lake kumpotondi kuwononga Asiriya,kusiya Ninive atawonongekeratundi owuma ngati chipululu. 14 Nkhosa ndi ngʼombe zidzagona pansi kumeneko,pamodzi ndi nyama zakuthengo za mtundu uliwonse.Akadzidzi a mʼchipululu ndi akanunguadzakhala pa nsanamira zake.Kulira kwawo kudzamveka mʼmazenera,mʼmakomo mwawo mudzakhala zinyalala zokhazokha,nsanamira za mkungudza zidzakhala poonekera. 15 Umenewu ndiye mzinda wosasamalaumene kale unali wotetezedwa.Unkanena kuti mu mtima mwake,“Ine ndine, ndipo palibenso wina wondiposa.”Taonani lero wasanduka bwinja,kokhala nyama zakutchire!Onse owudutsa akuwunyozandi kupukusa mitu yawo.
In Other Versions
Zephaniah 2 in the ANGEFD
Zephaniah 2 in the ANTPNG2D
Zephaniah 2 in the AS21
Zephaniah 2 in the BAGH
Zephaniah 2 in the BBPNG
Zephaniah 2 in the BBT1E
Zephaniah 2 in the BDS
Zephaniah 2 in the BEV
Zephaniah 2 in the BHAD
Zephaniah 2 in the BIB
Zephaniah 2 in the BLPT
Zephaniah 2 in the BNT
Zephaniah 2 in the BNTABOOT
Zephaniah 2 in the BNTLV
Zephaniah 2 in the BOATCB
Zephaniah 2 in the BOATCB2
Zephaniah 2 in the BOBCV
Zephaniah 2 in the BOCNT
Zephaniah 2 in the BOECS
Zephaniah 2 in the BOHCB
Zephaniah 2 in the BOHCV
Zephaniah 2 in the BOHLNT
Zephaniah 2 in the BOHNTLTAL
Zephaniah 2 in the BOICB
Zephaniah 2 in the BOILNTAP
Zephaniah 2 in the BOITCV
Zephaniah 2 in the BOKCV
Zephaniah 2 in the BOKCV2
Zephaniah 2 in the BOKHWOG
Zephaniah 2 in the BOKSSV
Zephaniah 2 in the BOLCB
Zephaniah 2 in the BOLCB2
Zephaniah 2 in the BOMCV
Zephaniah 2 in the BONAV
Zephaniah 2 in the BONCB
Zephaniah 2 in the BONLT
Zephaniah 2 in the BONUT2
Zephaniah 2 in the BOPLNT
Zephaniah 2 in the BOSCB
Zephaniah 2 in the BOSNC
Zephaniah 2 in the BOTLNT
Zephaniah 2 in the BOVCB
Zephaniah 2 in the BOYCB
Zephaniah 2 in the BPBB
Zephaniah 2 in the BPH
Zephaniah 2 in the BSB
Zephaniah 2 in the CCB
Zephaniah 2 in the CUV
Zephaniah 2 in the CUVS
Zephaniah 2 in the DBT
Zephaniah 2 in the DGDNT
Zephaniah 2 in the DHNT
Zephaniah 2 in the DNT
Zephaniah 2 in the ELBE
Zephaniah 2 in the EMTV
Zephaniah 2 in the ESV
Zephaniah 2 in the FBV
Zephaniah 2 in the FEB
Zephaniah 2 in the GGMNT
Zephaniah 2 in the GNT
Zephaniah 2 in the HARY
Zephaniah 2 in the HNT
Zephaniah 2 in the IRVA
Zephaniah 2 in the IRVB
Zephaniah 2 in the IRVG
Zephaniah 2 in the IRVH
Zephaniah 2 in the IRVK
Zephaniah 2 in the IRVM
Zephaniah 2 in the IRVM2
Zephaniah 2 in the IRVO
Zephaniah 2 in the IRVP
Zephaniah 2 in the IRVT
Zephaniah 2 in the IRVT2
Zephaniah 2 in the IRVU
Zephaniah 2 in the ISVN
Zephaniah 2 in the JSNT
Zephaniah 2 in the KAPI
Zephaniah 2 in the KBT1ETNIK
Zephaniah 2 in the KBV
Zephaniah 2 in the KJV
Zephaniah 2 in the KNFD
Zephaniah 2 in the LBA
Zephaniah 2 in the LBLA
Zephaniah 2 in the LNT
Zephaniah 2 in the LSV
Zephaniah 2 in the MAAL
Zephaniah 2 in the MBV
Zephaniah 2 in the MBV2
Zephaniah 2 in the MHNT
Zephaniah 2 in the MKNFD
Zephaniah 2 in the MNG
Zephaniah 2 in the MNT
Zephaniah 2 in the MNT2
Zephaniah 2 in the MRS1T
Zephaniah 2 in the NAA
Zephaniah 2 in the NASB
Zephaniah 2 in the NBLA
Zephaniah 2 in the NBS
Zephaniah 2 in the NBVTP
Zephaniah 2 in the NET2
Zephaniah 2 in the NIV11
Zephaniah 2 in the NNT
Zephaniah 2 in the NNT2
Zephaniah 2 in the NNT3
Zephaniah 2 in the PDDPT
Zephaniah 2 in the PFNT
Zephaniah 2 in the RMNT
Zephaniah 2 in the SBIAS
Zephaniah 2 in the SBIBS
Zephaniah 2 in the SBIBS2
Zephaniah 2 in the SBICS
Zephaniah 2 in the SBIDS
Zephaniah 2 in the SBIGS
Zephaniah 2 in the SBIHS
Zephaniah 2 in the SBIIS
Zephaniah 2 in the SBIIS2
Zephaniah 2 in the SBIIS3
Zephaniah 2 in the SBIKS
Zephaniah 2 in the SBIKS2
Zephaniah 2 in the SBIMS
Zephaniah 2 in the SBIOS
Zephaniah 2 in the SBIPS
Zephaniah 2 in the SBISS
Zephaniah 2 in the SBITS
Zephaniah 2 in the SBITS2
Zephaniah 2 in the SBITS3
Zephaniah 2 in the SBITS4
Zephaniah 2 in the SBIUS
Zephaniah 2 in the SBIVS
Zephaniah 2 in the SBT
Zephaniah 2 in the SBT1E
Zephaniah 2 in the SCHL
Zephaniah 2 in the SNT
Zephaniah 2 in the SUSU
Zephaniah 2 in the SUSU2
Zephaniah 2 in the SYNO
Zephaniah 2 in the TBIAOTANT
Zephaniah 2 in the TBT1E
Zephaniah 2 in the TBT1E2
Zephaniah 2 in the TFTIP
Zephaniah 2 in the TFTU
Zephaniah 2 in the TGNTATF3T
Zephaniah 2 in the THAI
Zephaniah 2 in the TNFD
Zephaniah 2 in the TNT
Zephaniah 2 in the TNTIK
Zephaniah 2 in the TNTIL
Zephaniah 2 in the TNTIN
Zephaniah 2 in the TNTIP
Zephaniah 2 in the TNTIZ
Zephaniah 2 in the TOMA
Zephaniah 2 in the TTENT
Zephaniah 2 in the UBG
Zephaniah 2 in the UGV
Zephaniah 2 in the UGV2
Zephaniah 2 in the UGV3
Zephaniah 2 in the VBL
Zephaniah 2 in the VDCC
Zephaniah 2 in the YALU
Zephaniah 2 in the YAPE
Zephaniah 2 in the YBVTP
Zephaniah 2 in the ZBP