Joel 1 (BOGWICC)
1 Yehova anayankhula ndi Yoweli mwana wa Petueli. 2 Inu akuluakulu, imvani izi;mvetserani, nonse amene mumakhala mʼdziko.Kodi zinthu zokhala ngati izi zinayamba zaonekapo mʼnthawi yanu,kapena mʼnthawi ya makolo anu? 3 Muwafotokozere ana anu,ndipo ana anuwo afotokozere ana awo,ndipo ana awo adzafotokozere mʼbado winawo. 4 Chimene dzombe losamera mapiko lasiyadzombe lowuluka ladya;chimene dzombe lowuluka lasiyadzombe lalingʼono ladya;chimene dzombe lalingʼono lasiyachilimamine wadya. 5 Dzukani, inu zidakwa ndipo mulire!Lirani mofuwula, inu nonse amene mumamwa vinyo;lirani mofuwula chifukwa cha vinyo watsopano,pakuti wachotsedwa pakamwa panu. 6 Mtundu wa anthu wathira nkhondo dziko langa,wamphamvu ndi wosawerengeka;uli ndi mano a mkango,zibwano za mkango waukazi. 7 Wawononga mphesa zangandipo wathyola mitengo yanga ya mkuyu.Wakungunula makungwa akendi kuwataya,kusiya nthambi zake zili mbee. 8 Lirani ngati namwali wovala chiguduli,chifukwa cha mwamuna wa utsikana wake. 9 Chopereka cha chakudya ndi cha chakumwasizikuperekedwa ku nyumba ya Yehova.Ansembe akulira,amene amatumikira pamaso pa Yehova. 10 Minda yaguga,nthaka yauma;tirigu wawonongeka,vinyo watsopano watha,mitengo ya mafuta yauma. 11 Khalani ndi nkhawa, inu alimi,lirani mofuwula inu alimi a mphesa;imvani chisoni chifukwa cha tirigu ndi barele,pakuti zokolola za mʼmunda zawonongeka. 12 Mpesa waumandipo mtengo wamkuyu wafota;makangadza, kanjedza ndi mitengo ya apulosi,mitengo yonse ya mʼmunda yauma.Ndithudi chimwemwe cha anthuchatheratu. 13 Inu ansembe, valani ziguduli ndipo lirani;lirani mofuwula, inu amene mumatumikira pa guwa lansembe.Bwerani, fundani ziguduli usiku wonse,inu amene mumatumikira pamaso pa Mulungu wanga;pakuti chopereka cha chakudya ndi cha chakumwasizikupezekanso mʼnyumba ya Mulungu wanu. 14 Lengezani tsiku lopatulika losala zakudya,itanani msonkhano wopatulika.Sonkhanitsani akuluakulundi anthu onse okhala mʼdzikoku nyumba ya Yehova Mulungu wanundipo alirire Yehova. 15 Kalanga ine tsikulo!Pakuti tsiku la Yehova layandikira;lidzabwera ngati chiwonongeko chochokera kwa Wamphamvuzonse. 16 Kodi chakudya chathu sichachotsedwaife tikuona?Kodi mʼnyumba ya Mulungu wathusimulibe chimwemwe ndi chisangalalo? 17 Mbewu zikunyalapoti pansi ndi powuma.Nyumba zosungiramo zinthu zawonongeka;nkhokwe zapasukapopeza tirigu wauma. 18 Taonani mmene zikulirira ziweto;ngʼombe zikungoyenda uku ndi ukuchifukwa zilibe msipu;ngakhalenso nkhosa zikusauka. 19 Kwa Inu Yehova ndilirira,pakuti moto wapsereza msipu wakuthengo,malawi amoto apsereza mitengo yonse ya mʼtchire. 20 Ngakhale nyama zakuthengo zikulirira Inu;timitsinje tonse taphwandipo moto wapsereza msipu wa kuthengo.
In Other Versions
Joel 1 in the ANGEFD
Joel 1 in the ANTPNG2D
Joel 1 in the AS21
Joel 1 in the BAGH
Joel 1 in the BBPNG
Joel 1 in the BBT1E
Joel 1 in the BDS
Joel 1 in the BEV
Joel 1 in the BHAD
Joel 1 in the BIB
Joel 1 in the BLPT
Joel 1 in the BNT
Joel 1 in the BNTABOOT
Joel 1 in the BNTLV
Joel 1 in the BOATCB
Joel 1 in the BOATCB2
Joel 1 in the BOBCV
Joel 1 in the BOCNT
Joel 1 in the BOECS
Joel 1 in the BOHCB
Joel 1 in the BOHCV
Joel 1 in the BOHLNT
Joel 1 in the BOHNTLTAL
Joel 1 in the BOICB
Joel 1 in the BOILNTAP
Joel 1 in the BOITCV
Joel 1 in the BOKCV
Joel 1 in the BOKCV2
Joel 1 in the BOKHWOG
Joel 1 in the BOKSSV
Joel 1 in the BOLCB
Joel 1 in the BOLCB2
Joel 1 in the BOMCV
Joel 1 in the BONAV
Joel 1 in the BONCB
Joel 1 in the BONLT
Joel 1 in the BONUT2
Joel 1 in the BOPLNT
Joel 1 in the BOSCB
Joel 1 in the BOSNC
Joel 1 in the BOTLNT
Joel 1 in the BOVCB
Joel 1 in the BOYCB
Joel 1 in the BPBB
Joel 1 in the BPH
Joel 1 in the BSB
Joel 1 in the CCB
Joel 1 in the CUV
Joel 1 in the CUVS
Joel 1 in the DBT
Joel 1 in the DGDNT
Joel 1 in the DHNT
Joel 1 in the DNT
Joel 1 in the ELBE
Joel 1 in the EMTV
Joel 1 in the ESV
Joel 1 in the FBV
Joel 1 in the FEB
Joel 1 in the GGMNT
Joel 1 in the GNT
Joel 1 in the HARY
Joel 1 in the HNT
Joel 1 in the IRVA
Joel 1 in the IRVB
Joel 1 in the IRVG
Joel 1 in the IRVH
Joel 1 in the IRVK
Joel 1 in the IRVM
Joel 1 in the IRVM2
Joel 1 in the IRVO
Joel 1 in the IRVP
Joel 1 in the IRVT
Joel 1 in the IRVT2
Joel 1 in the IRVU
Joel 1 in the ISVN
Joel 1 in the JSNT
Joel 1 in the KAPI
Joel 1 in the KBT1ETNIK
Joel 1 in the KBV
Joel 1 in the KJV
Joel 1 in the KNFD
Joel 1 in the LBA
Joel 1 in the LBLA
Joel 1 in the LNT
Joel 1 in the LSV
Joel 1 in the MAAL
Joel 1 in the MBV
Joel 1 in the MBV2
Joel 1 in the MHNT
Joel 1 in the MKNFD
Joel 1 in the MNG
Joel 1 in the MNT
Joel 1 in the MNT2
Joel 1 in the MRS1T
Joel 1 in the NAA
Joel 1 in the NASB
Joel 1 in the NBLA
Joel 1 in the NBS
Joel 1 in the NBVTP
Joel 1 in the NET2
Joel 1 in the NIV11
Joel 1 in the NNT
Joel 1 in the NNT2
Joel 1 in the NNT3
Joel 1 in the PDDPT
Joel 1 in the PFNT
Joel 1 in the RMNT
Joel 1 in the SBIAS
Joel 1 in the SBIBS
Joel 1 in the SBIBS2
Joel 1 in the SBICS
Joel 1 in the SBIDS
Joel 1 in the SBIGS
Joel 1 in the SBIHS
Joel 1 in the SBIIS
Joel 1 in the SBIIS2
Joel 1 in the SBIIS3
Joel 1 in the SBIKS
Joel 1 in the SBIKS2
Joel 1 in the SBIMS
Joel 1 in the SBIOS
Joel 1 in the SBIPS
Joel 1 in the SBISS
Joel 1 in the SBITS
Joel 1 in the SBITS2
Joel 1 in the SBITS3
Joel 1 in the SBITS4
Joel 1 in the SBIUS
Joel 1 in the SBIVS
Joel 1 in the SBT
Joel 1 in the SBT1E
Joel 1 in the SCHL
Joel 1 in the SNT
Joel 1 in the SUSU
Joel 1 in the SUSU2
Joel 1 in the SYNO
Joel 1 in the TBIAOTANT
Joel 1 in the TBT1E
Joel 1 in the TBT1E2
Joel 1 in the TFTIP
Joel 1 in the TFTU
Joel 1 in the TGNTATF3T
Joel 1 in the THAI
Joel 1 in the TNFD
Joel 1 in the TNT
Joel 1 in the TNTIK
Joel 1 in the TNTIL
Joel 1 in the TNTIN
Joel 1 in the TNTIP
Joel 1 in the TNTIZ
Joel 1 in the TOMA
Joel 1 in the TTENT
Joel 1 in the UBG
Joel 1 in the UGV
Joel 1 in the UGV2
Joel 1 in the UGV3
Joel 1 in the VBL
Joel 1 in the VDCC
Joel 1 in the YALU
Joel 1 in the YAPE
Joel 1 in the YBVTP
Joel 1 in the ZBP