Jeremiah 30 (BOGWICC)
1 Yehova anawuza Yeremiya kuti, 2 “Ine Yehova, Mulungu wa Israeli ndikuti, ‘Lemba mʼbuku mawu onse amene ndakuwuza. 3 Nthawi ikubwera pamene ndidzachotse anthu anga, Israeli ndi Yuda kuchokera ku ukapolo ndi kuwabwezera dziko limene ndinapatsa makolo awo,’ akutero Yehova.” 4 Nawa mawu amene Yehova anayankhula ndi anthu a ku Israeli ndi Yuda: 5 “Yehova akuti:“Ndamva kulira chifukwa cha nkhawa,ndamva kulira kwa mantha popeza palibe mtendere. 6 Tsono khalani pansi ndi kudzifunsa kuti:Kodi munthu wamwamuna angathe kubereka mwana?Nanga nʼchifukwa chiyani ndikuona munthu aliyense wamwamunaatagwira manja ake pa mimba pake ngati mayi pa nthawi yake yochira?Chifukwa chiyani nkhope iliyonse ili yakugwa? 7 Mayo ine! Tsiku limeneli ndi lalikulu kwambiri!Sipadzakhala lina lofanana nalo.Idzakhala nthawi ya masautso kwa Yakobo,koma adzapulumuka ku masautsowo.” 8 Yehova Wamphamvuzonse akuti, “Pa tsiku limenelo,ndidzathyola goli la ukapolo mʼkhosi mwawondipo ndidzadula zingwe zowamanga;Aisraeli sadzakhalanso akapolo a alendo. 9 Mʼmalo mwake, adzatumikira Yehova Mulungu wawondiponso Davide mfumu yawo,amene ndidzawasankhira. 10 “ ‘Tsono usachite mantha, iwe mtumiki wanga Yakobo;usade nkhawa, iwe Israeli,’akutero Yehova.‘Ndithu ndidzakupulumutsa kuchokera ku dziko lakutali,zidzukulu zako kuchokera ku dziko la ukapolo wawo.Yakobo adzabwerera ndipo adzakhala modekha pa mtendere,ndipo palibe amene adzamuchititsa mantha. 11 Ine ndili nanu ndipo ndidzakupulumutsani,’akutero Yehova.‘Ngakhale ndidzawononga kotheratu mitundu yonse ya anthukumene ndinakubalalitsirani,koma inu sindidzakuwonongani kotheratu.Sindidzakulekani kuti mukhale osalangidwa.Koma ndidzakulangani mwachilungamo.’ ” 12 Yehova akuti,“Chilonda chanu nʼchosachizika,bala lanu ndi lonyeka. 13 Palibe amene angathe kukutetezani pa mlandu wanu,palibe chiyembekezo choti inu nʼkuchira,palibe mankhwala ochiritsa inu. 14 Abwenzi anu onse akuyiwalani;sasamalanso za inu.Ndakukanthani ngati mmene mdani akanachitira.Ndipo ndakulangani mwa nkhanza,chifukwa machimo anu ndi ambiri,ndipo kulakwa kwanu ndi kwakukulu. 15 Chifukwa chiyani mukulira nacho chilonda chanu?Bala lanu silingapole ayi.Ine ndakuchitani zimenezi chifukwa machimo anu ndi ambirindipo kulakwa kwanu nʼkwakukulu. 16 “Tsono onse amene anakuwonongani, nawonso adzawonongedwa;adani anu onse adzapita ku ukapolo.Iwo amene anafunkha zinthu zanu, zinthu zawo zidzafunkhidwanso;onse amene anakusakazani nawonso adzasakazidwa. 17 Ndidzachiza matenda anundi kupoletsa zilonda zanu,akutero Yehova,‘chifukwa mukutchedwa anthu otayika.Amati, ndi anthu a ku Ziyoni awa amene alibe wowasamala.’ ” 18 Yehova akuti,“Ndidzabwera nalo banja la Yakobo ku dziko lawondipo ndidzachitira chifundo malo ake okhalamo;mzinda wa Yerusalemu udzamangidwanso pa bwinja pake,nyumba yaufumu idzamangidwanso pa malo pake penipeni. 19 Anthuwo adzayimba nyimbo zoyamika Yehovandipo kudzamveka phokoso lachisangalalo.Ndidzawachulukitsa,ndipo chiwerengero chawo sichidzatsika;ndidzawapatsa ulemerero,ndipo sadzanyozedwanso. 20 Ana awo adzakhalanso monga mmene analili kale,ndipo gulu lawo ndidzalikhazikitsa pamaso panga;ndidzalanga onse owazunza. 21 Mtsogoleri wawo adzakhala mmodzi mwa iwo.Wodzawalamulira adzachokera pakati pawo.Choncho ndidzawakokera kufupi ndi Ine ndipo iye adzandiyandikira.Ndani angalimbe mtima payekha kuyandikana nanepopanda kuyitanidwa?”akutero Yehova. 22 “Choncho inu mudzakhala anthu anga,ndipo Ine ndidzakhala Mulungu wanu.” 23 Taonani ukali wa Yehova wowombangati mphepo ya mkuntho.Mphepo ya namondweikuwomba pa mitu ya anthu oyipa. 24 Mkwiyo woopsa wa Yehova sudzachokampaka atakwaniritsa zolingaza mu mtima mwake.Mudzamvetsa zimenezimasiku akubwerawo.
In Other Versions
Jeremiah 30 in the ANGEFD
Jeremiah 30 in the ANTPNG2D
Jeremiah 30 in the AS21
Jeremiah 30 in the BAGH
Jeremiah 30 in the BBPNG
Jeremiah 30 in the BBT1E
Jeremiah 30 in the BDS
Jeremiah 30 in the BEV
Jeremiah 30 in the BHAD
Jeremiah 30 in the BIB
Jeremiah 30 in the BLPT
Jeremiah 30 in the BNT
Jeremiah 30 in the BNTABOOT
Jeremiah 30 in the BNTLV
Jeremiah 30 in the BOATCB
Jeremiah 30 in the BOATCB2
Jeremiah 30 in the BOBCV
Jeremiah 30 in the BOCNT
Jeremiah 30 in the BOECS
Jeremiah 30 in the BOHCB
Jeremiah 30 in the BOHCV
Jeremiah 30 in the BOHLNT
Jeremiah 30 in the BOHNTLTAL
Jeremiah 30 in the BOICB
Jeremiah 30 in the BOILNTAP
Jeremiah 30 in the BOITCV
Jeremiah 30 in the BOKCV
Jeremiah 30 in the BOKCV2
Jeremiah 30 in the BOKHWOG
Jeremiah 30 in the BOKSSV
Jeremiah 30 in the BOLCB
Jeremiah 30 in the BOLCB2
Jeremiah 30 in the BOMCV
Jeremiah 30 in the BONAV
Jeremiah 30 in the BONCB
Jeremiah 30 in the BONLT
Jeremiah 30 in the BONUT2
Jeremiah 30 in the BOPLNT
Jeremiah 30 in the BOSCB
Jeremiah 30 in the BOSNC
Jeremiah 30 in the BOTLNT
Jeremiah 30 in the BOVCB
Jeremiah 30 in the BOYCB
Jeremiah 30 in the BPBB
Jeremiah 30 in the BPH
Jeremiah 30 in the BSB
Jeremiah 30 in the CCB
Jeremiah 30 in the CUV
Jeremiah 30 in the CUVS
Jeremiah 30 in the DBT
Jeremiah 30 in the DGDNT
Jeremiah 30 in the DHNT
Jeremiah 30 in the DNT
Jeremiah 30 in the ELBE
Jeremiah 30 in the EMTV
Jeremiah 30 in the ESV
Jeremiah 30 in the FBV
Jeremiah 30 in the FEB
Jeremiah 30 in the GGMNT
Jeremiah 30 in the GNT
Jeremiah 30 in the HARY
Jeremiah 30 in the HNT
Jeremiah 30 in the IRVA
Jeremiah 30 in the IRVB
Jeremiah 30 in the IRVG
Jeremiah 30 in the IRVH
Jeremiah 30 in the IRVK
Jeremiah 30 in the IRVM
Jeremiah 30 in the IRVM2
Jeremiah 30 in the IRVO
Jeremiah 30 in the IRVP
Jeremiah 30 in the IRVT
Jeremiah 30 in the IRVT2
Jeremiah 30 in the IRVU
Jeremiah 30 in the ISVN
Jeremiah 30 in the JSNT
Jeremiah 30 in the KAPI
Jeremiah 30 in the KBT1ETNIK
Jeremiah 30 in the KBV
Jeremiah 30 in the KJV
Jeremiah 30 in the KNFD
Jeremiah 30 in the LBA
Jeremiah 30 in the LBLA
Jeremiah 30 in the LNT
Jeremiah 30 in the LSV
Jeremiah 30 in the MAAL
Jeremiah 30 in the MBV
Jeremiah 30 in the MBV2
Jeremiah 30 in the MHNT
Jeremiah 30 in the MKNFD
Jeremiah 30 in the MNG
Jeremiah 30 in the MNT
Jeremiah 30 in the MNT2
Jeremiah 30 in the MRS1T
Jeremiah 30 in the NAA
Jeremiah 30 in the NASB
Jeremiah 30 in the NBLA
Jeremiah 30 in the NBS
Jeremiah 30 in the NBVTP
Jeremiah 30 in the NET2
Jeremiah 30 in the NIV11
Jeremiah 30 in the NNT
Jeremiah 30 in the NNT2
Jeremiah 30 in the NNT3
Jeremiah 30 in the PDDPT
Jeremiah 30 in the PFNT
Jeremiah 30 in the RMNT
Jeremiah 30 in the SBIAS
Jeremiah 30 in the SBIBS
Jeremiah 30 in the SBIBS2
Jeremiah 30 in the SBICS
Jeremiah 30 in the SBIDS
Jeremiah 30 in the SBIGS
Jeremiah 30 in the SBIHS
Jeremiah 30 in the SBIIS
Jeremiah 30 in the SBIIS2
Jeremiah 30 in the SBIIS3
Jeremiah 30 in the SBIKS
Jeremiah 30 in the SBIKS2
Jeremiah 30 in the SBIMS
Jeremiah 30 in the SBIOS
Jeremiah 30 in the SBIPS
Jeremiah 30 in the SBISS
Jeremiah 30 in the SBITS
Jeremiah 30 in the SBITS2
Jeremiah 30 in the SBITS3
Jeremiah 30 in the SBITS4
Jeremiah 30 in the SBIUS
Jeremiah 30 in the SBIVS
Jeremiah 30 in the SBT
Jeremiah 30 in the SBT1E
Jeremiah 30 in the SCHL
Jeremiah 30 in the SNT
Jeremiah 30 in the SUSU
Jeremiah 30 in the SUSU2
Jeremiah 30 in the SYNO
Jeremiah 30 in the TBIAOTANT
Jeremiah 30 in the TBT1E
Jeremiah 30 in the TBT1E2
Jeremiah 30 in the TFTIP
Jeremiah 30 in the TFTU
Jeremiah 30 in the TGNTATF3T
Jeremiah 30 in the THAI
Jeremiah 30 in the TNFD
Jeremiah 30 in the TNT
Jeremiah 30 in the TNTIK
Jeremiah 30 in the TNTIL
Jeremiah 30 in the TNTIN
Jeremiah 30 in the TNTIP
Jeremiah 30 in the TNTIZ
Jeremiah 30 in the TOMA
Jeremiah 30 in the TTENT
Jeremiah 30 in the UBG
Jeremiah 30 in the UGV
Jeremiah 30 in the UGV2
Jeremiah 30 in the UGV3
Jeremiah 30 in the VBL
Jeremiah 30 in the VDCC
Jeremiah 30 in the YALU
Jeremiah 30 in the YAPE
Jeremiah 30 in the YBVTP
Jeremiah 30 in the ZBP