Isaiah 48 (BOGWICC)
1 “Mverani izi, inu nyumba ya Yakobo,inu amene amakutchani dzina lanu Israeli,ndinu a fuko la Yuda,inu mumalumbira mʼdzina la Yehova,ndi kupemphera kwa Mulungu wa Israeli,ngakhale osati mʼchoonadi kapena mʼchilungamo. 2 Komabe inu mumadzitcha nzika za mzinda wopatulikandipo mumadalira Mulungu wa Israeli,amene dzina lake ndi Yehova Wamphamvuzonse: 3 Zimene zinachitika poyamba ndinalosera kalekale,zinatuluka mʼkamwa mwanga ndipo ndinazilengeza;tsono mwadzidzidzi ndinachitapo kanthu ndipo zinachitikadi. 4 Pakuti Ine ndinadziwa kuti iwe ndiwe nkhutukumvewa nkhongo gwaa,wa mutu wowuma. 5 Ine ndinakuwuziratu zinthu izi kalekale lomwe;zisanachitike ndinazilengezeratu kwa iwekuti unganene kuti,‘Fano langa ndilo lachita zimenezi,kapena kuti fano langa losema ndi kamulungu kanga kachitsulo ndiwo analamula kuti zimenezi zichitike.’ 6 Inu munamva zinthu zimenezi.Kodi inu simungazivomereze? “Kuyambira tsopano mpaka mʼtsogolo ndidzakuwuzani zinthu zatsopanozinthu zobisika zimene simunazidziwe konse. 7 Zinthu zimenezi zikulengedwa tsopano lino, osati kalekale;munali musanazimve mpaka lero lino.Choncho inu simunganene kuti,‘Zimenezi ndiye ayi, ndinazidziwa kale.’ 8 Inu simunazimvepo kapena kuzidziwa;makutu anu sanali otsekuka.Tsono Ine ndinadziwa bwino kuti ndinu anthu achiwembu ndi kutichiyambire ubwana wanu munatchedwa owukira. 9 Ine ndikuchedwetsa mkwiyo wanga chifukwa cha dzina langa.Ndikukulezerani ukali wanga kuti anthu andilemekeze.Sindidzakuwonongani kotheratu. 10 Taonani, ndinakuyeretsani ngati siliva;ndinakuyesani mʼngʼanjo yamasautso. 11 Chifukwa cha ulemu wanga, chifukwa cha ulemu wanga Ine ndikuchita zimenezi.Ndingalole bwanji kuti ndinyozeke?Ulemerero wanga sindidzawupereka kwa wina. 12 “Tamvera Ine, iwe Yakobo,Israeli, amene ndinakuyitana:Mulungu uja Woyambandi Wotsiriza ndine. 13 Inde dzanja langa linamanga maziko a dziko lapansi,dzanja langa lamanja linafunyulula mlengalenga.Ndi mawu anga ndinalenga kumwambandi dziko lapansi. 14 “Sonkhanani pamodzi inu nonse ndipo mvetserani:Ndani mwa mafano anu amene analoseratu za zinthu izi?Wokondedwa wa Yehova uja adzachitazomwe Iye anakonzera Babuloni;dzanja lake lidzalimbana ndi Kaldeya. 15 Ine, Inetu, ndayankhula;ndi kumuyitanandidzamubweretsa ndinendipo adzakwaniritsa zolinga zake. 16 “Bwerani pafupi ndipo mvetserani izi:“Kuyambira pachiyambi sindinayankhule mobisa;pa nthawi imene zinkachitika zimenezi Ine ndinali pomwepo.” Ndipo tsopano Ambuye Yehova wandipatsa Mzimu wakendi kundituma. 17 Yehova, Mpulumutsi wanu,Woyerayo wa Israeli akuti,“Ine ndine Yehova Mulungu wanu,amene ndimakuphunzitsa kuti upindule,ndimakutsogolera pa njira yoyenera kuyitsata. 18 Ngati iwe ukanangosamalira zolamulira zanga,bwenzi mtendere wako ukanakhala ngati mtsinje,ndi chipulumutso chako ngati mafunde a pa nyanja. 19 Zidzukulu zako zikanachuluka ngati mchenga,ana ako akanachuluka ngati fumbi;dzina lawo silikanachotsedwa pamaso pangandipo silikanafafanizidwa konse.” 20 Tulukani mʼdziko la Babuloni!Thawani dziko la Kaldeya!Lengezani zimenezi ndi mawu a chisangalalondipo muzilalikirempaka kumathero a dziko lapansi;muzinena kuti, “Yehova wawombola Yakobo mtumiki wake.” 21 Iwo sanamve ludzu pamene Yehova ankawatsogolera mʼchipululu;anawapatsa madzi otuluka mʼthanthwe;anangʼamba thanthwelo ndipomunatuluka madzi. 22 “Palibe mtendere kwa anthu ochimwa,” akutero Yehova.
In Other Versions
Isaiah 48 in the ANGEFD
Isaiah 48 in the ANTPNG2D
Isaiah 48 in the AS21
Isaiah 48 in the BAGH
Isaiah 48 in the BBPNG
Isaiah 48 in the BBT1E
Isaiah 48 in the BDS
Isaiah 48 in the BEV
Isaiah 48 in the BHAD
Isaiah 48 in the BIB
Isaiah 48 in the BLPT
Isaiah 48 in the BNT
Isaiah 48 in the BNTABOOT
Isaiah 48 in the BNTLV
Isaiah 48 in the BOATCB
Isaiah 48 in the BOATCB2
Isaiah 48 in the BOBCV
Isaiah 48 in the BOCNT
Isaiah 48 in the BOECS
Isaiah 48 in the BOHCB
Isaiah 48 in the BOHCV
Isaiah 48 in the BOHLNT
Isaiah 48 in the BOHNTLTAL
Isaiah 48 in the BOICB
Isaiah 48 in the BOILNTAP
Isaiah 48 in the BOITCV
Isaiah 48 in the BOKCV
Isaiah 48 in the BOKCV2
Isaiah 48 in the BOKHWOG
Isaiah 48 in the BOKSSV
Isaiah 48 in the BOLCB
Isaiah 48 in the BOLCB2
Isaiah 48 in the BOMCV
Isaiah 48 in the BONAV
Isaiah 48 in the BONCB
Isaiah 48 in the BONLT
Isaiah 48 in the BONUT2
Isaiah 48 in the BOPLNT
Isaiah 48 in the BOSCB
Isaiah 48 in the BOSNC
Isaiah 48 in the BOTLNT
Isaiah 48 in the BOVCB
Isaiah 48 in the BOYCB
Isaiah 48 in the BPBB
Isaiah 48 in the BPH
Isaiah 48 in the BSB
Isaiah 48 in the CCB
Isaiah 48 in the CUV
Isaiah 48 in the CUVS
Isaiah 48 in the DBT
Isaiah 48 in the DGDNT
Isaiah 48 in the DHNT
Isaiah 48 in the DNT
Isaiah 48 in the ELBE
Isaiah 48 in the EMTV
Isaiah 48 in the ESV
Isaiah 48 in the FBV
Isaiah 48 in the FEB
Isaiah 48 in the GGMNT
Isaiah 48 in the GNT
Isaiah 48 in the HARY
Isaiah 48 in the HNT
Isaiah 48 in the IRVA
Isaiah 48 in the IRVB
Isaiah 48 in the IRVG
Isaiah 48 in the IRVH
Isaiah 48 in the IRVK
Isaiah 48 in the IRVM
Isaiah 48 in the IRVM2
Isaiah 48 in the IRVO
Isaiah 48 in the IRVP
Isaiah 48 in the IRVT
Isaiah 48 in the IRVT2
Isaiah 48 in the IRVU
Isaiah 48 in the ISVN
Isaiah 48 in the JSNT
Isaiah 48 in the KAPI
Isaiah 48 in the KBT1ETNIK
Isaiah 48 in the KBV
Isaiah 48 in the KJV
Isaiah 48 in the KNFD
Isaiah 48 in the LBA
Isaiah 48 in the LBLA
Isaiah 48 in the LNT
Isaiah 48 in the LSV
Isaiah 48 in the MAAL
Isaiah 48 in the MBV
Isaiah 48 in the MBV2
Isaiah 48 in the MHNT
Isaiah 48 in the MKNFD
Isaiah 48 in the MNG
Isaiah 48 in the MNT
Isaiah 48 in the MNT2
Isaiah 48 in the MRS1T
Isaiah 48 in the NAA
Isaiah 48 in the NASB
Isaiah 48 in the NBLA
Isaiah 48 in the NBS
Isaiah 48 in the NBVTP
Isaiah 48 in the NET2
Isaiah 48 in the NIV11
Isaiah 48 in the NNT
Isaiah 48 in the NNT2
Isaiah 48 in the NNT3
Isaiah 48 in the PDDPT
Isaiah 48 in the PFNT
Isaiah 48 in the RMNT
Isaiah 48 in the SBIAS
Isaiah 48 in the SBIBS
Isaiah 48 in the SBIBS2
Isaiah 48 in the SBICS
Isaiah 48 in the SBIDS
Isaiah 48 in the SBIGS
Isaiah 48 in the SBIHS
Isaiah 48 in the SBIIS
Isaiah 48 in the SBIIS2
Isaiah 48 in the SBIIS3
Isaiah 48 in the SBIKS
Isaiah 48 in the SBIKS2
Isaiah 48 in the SBIMS
Isaiah 48 in the SBIOS
Isaiah 48 in the SBIPS
Isaiah 48 in the SBISS
Isaiah 48 in the SBITS
Isaiah 48 in the SBITS2
Isaiah 48 in the SBITS3
Isaiah 48 in the SBITS4
Isaiah 48 in the SBIUS
Isaiah 48 in the SBIVS
Isaiah 48 in the SBT
Isaiah 48 in the SBT1E
Isaiah 48 in the SCHL
Isaiah 48 in the SNT
Isaiah 48 in the SUSU
Isaiah 48 in the SUSU2
Isaiah 48 in the SYNO
Isaiah 48 in the TBIAOTANT
Isaiah 48 in the TBT1E
Isaiah 48 in the TBT1E2
Isaiah 48 in the TFTIP
Isaiah 48 in the TFTU
Isaiah 48 in the TGNTATF3T
Isaiah 48 in the THAI
Isaiah 48 in the TNFD
Isaiah 48 in the TNT
Isaiah 48 in the TNTIK
Isaiah 48 in the TNTIL
Isaiah 48 in the TNTIN
Isaiah 48 in the TNTIP
Isaiah 48 in the TNTIZ
Isaiah 48 in the TOMA
Isaiah 48 in the TTENT
Isaiah 48 in the UBG
Isaiah 48 in the UGV
Isaiah 48 in the UGV2
Isaiah 48 in the UGV3
Isaiah 48 in the VBL
Isaiah 48 in the VDCC
Isaiah 48 in the YALU
Isaiah 48 in the YAPE
Isaiah 48 in the YBVTP
Isaiah 48 in the ZBP