Zephaniah 3 (BOGWICC)
1 Tsoka kwa mzinda wa anthu opondereza,owukira ndi odetsedwa! 2 Sumvera aliyense,sulandira chidzudzulo.Sumadalira Yehova,suyandikira pafupi ndi Mulungu wake. 3 Akuluakulu ake ali ngati mikango yobuma,olamulira ake ndi olusa ngati mimbulu ya nthawi ya madzulo,zimene pofika mmawa sizisiya chilichonse. 4 Aneneri ake ndi odzikuza;anthu achinyengo.Ansembe ake amadetsa malo opatulikandipo amaphwanya lamulo. 5 Yehova amene ali pakati pawo ndi wolungama;Iye salakwa.Tsiku ndi tsiku amaweruza molungama,ndipo tsiku lililonse salephera,komabe ochita zoyipa sachita manyazi nʼkomwe. 6 “Ndachotseratu mitundu ya anthu;ndagwetsa malinga awo.Ndipo sindinasiye ndi mmodzi yemwe mʼmisewu mwawo,popanda aliyense wodutsa.Mizinda yawo yawonongedwa;palibe aliyense adzatsalemo. 7 Ndinati,‘Ndithudi, anthu a mu mzindawu adzandiopandi kumvera kudzudzula kwanga!’Ndipo sindidzawononga nyumba zawo,kapena kuwalanganso.Koma iwo anali okonzekakuchita mwachinyengo zinthu zonse zimene amachita. 8 Choncho mundidikire,” akutero Yehova,“chifukwa cha tsiku limene ndidzaperekera umboni.Ndatsimikiza kusonkhanitsa pamodzi mitundu ya anthu,kusonkhanitsa maufumundi kutsanulira ukali wanga pa iwo;mkwiyo wanga wonse woopsa.Dziko lonse lidzatenthedwandi moto wa mkwiyo wa nsanje yanga. 9 “Pamenepo ndidzayeretsa milomo ya anthu a mitundu yonsekuti anthu onsewo ayitane dzina la Yehovandi kumutumikira Iye pamodzi. 10 Kuchokera kutsidya kwa mitsinje ya ku Kusianthu anga ondipembedza, omwazikana,adzandibweretsera zopereka. 11 Tsiku limenelo simudzachita manyazichifukwa cha zoyipa zonse munandichitira,popeza ndidzachotsa onse mu mzinda uwuamene amakondwera chifukwa cha kunyada kwawo.Simudzakhalanso odzikuzamʼphiri langa lopatulika. 12 Koma ndidzasiya pakati panuanthu ofatsa ndi odzichepetsa,amene amadalira dzina la Yehova. 13 Aisraeli otsala sadzachitanso zolakwika;sadzayankhulanso zonama,ngakhale chinyengo sichidzatuluka mʼkamwa mwawo.Adzadya ndi kugonandipo palibe amene adzawachititse mantha.” 14 Imba, iwe mwana wamkazi wa Ziyoni;fuwula mokweza, iwe Israeli!Sangalala ndi kukondwera ndi mtima wako wonse,iwe mwana wamkazi wa Yerusalemu! 15 Yehova wachotsa chilango chako,wabweza mdani wako.Yehova, Mfumu ya Israeli, ali pakati pako;sudzaopanso chilichonse. 16 Pa tsiku limenelo adzanena kwa Yerusalemu kuti,“Usaope, iwe Ziyoni;usafowoke. 17 Yehova Mulungu wako ali pakati pako,ali ndi mphamvu yopulumutsa.Adzakondwera kwambiri mwa iwe,adzakukhalitsa chete ndi chikondi chake,adzayimba mokondwera chifukwa cha iwe.” 18 “Ndidzakuchotserani zowawaza pa zikondwerero zoyikika;nʼzolemetsa ndi zochititsa manyazi. 19 Taonani, nthawi imeneyo ndidzathana ndionse amene anakuponderezani;ndidzapulumutsa olumalandi kusonkhanitsa amene anamwazika.Ndidzawayamikira ndi kuwachitira ulemumʼdziko lililonse mmene anachititsidwa manyazi. 20 Pa nthawi imeneyo ndidzakusonkhanitsani;pa nthawi imeneyo ndidzakubweretsani ku mudzi kwanu.Ndidzakuyamikirani ndi kukuchitirani ulemupakati pa mitundu ya anthu a dziko lapansipamene ndidzabwezeretsa mtendere wanuinu mukuona,”akutero Yehova.
In Other Versions
Zephaniah 3 in the ANGEFD
Zephaniah 3 in the ANTPNG2D
Zephaniah 3 in the AS21
Zephaniah 3 in the BAGH
Zephaniah 3 in the BBPNG
Zephaniah 3 in the BBT1E
Zephaniah 3 in the BDS
Zephaniah 3 in the BEV
Zephaniah 3 in the BHAD
Zephaniah 3 in the BIB
Zephaniah 3 in the BLPT
Zephaniah 3 in the BNT
Zephaniah 3 in the BNTABOOT
Zephaniah 3 in the BNTLV
Zephaniah 3 in the BOATCB
Zephaniah 3 in the BOATCB2
Zephaniah 3 in the BOBCV
Zephaniah 3 in the BOCNT
Zephaniah 3 in the BOECS
Zephaniah 3 in the BOHCB
Zephaniah 3 in the BOHCV
Zephaniah 3 in the BOHLNT
Zephaniah 3 in the BOHNTLTAL
Zephaniah 3 in the BOICB
Zephaniah 3 in the BOILNTAP
Zephaniah 3 in the BOITCV
Zephaniah 3 in the BOKCV
Zephaniah 3 in the BOKCV2
Zephaniah 3 in the BOKHWOG
Zephaniah 3 in the BOKSSV
Zephaniah 3 in the BOLCB
Zephaniah 3 in the BOLCB2
Zephaniah 3 in the BOMCV
Zephaniah 3 in the BONAV
Zephaniah 3 in the BONCB
Zephaniah 3 in the BONLT
Zephaniah 3 in the BONUT2
Zephaniah 3 in the BOPLNT
Zephaniah 3 in the BOSCB
Zephaniah 3 in the BOSNC
Zephaniah 3 in the BOTLNT
Zephaniah 3 in the BOVCB
Zephaniah 3 in the BOYCB
Zephaniah 3 in the BPBB
Zephaniah 3 in the BPH
Zephaniah 3 in the BSB
Zephaniah 3 in the CCB
Zephaniah 3 in the CUV
Zephaniah 3 in the CUVS
Zephaniah 3 in the DBT
Zephaniah 3 in the DGDNT
Zephaniah 3 in the DHNT
Zephaniah 3 in the DNT
Zephaniah 3 in the ELBE
Zephaniah 3 in the EMTV
Zephaniah 3 in the ESV
Zephaniah 3 in the FBV
Zephaniah 3 in the FEB
Zephaniah 3 in the GGMNT
Zephaniah 3 in the GNT
Zephaniah 3 in the HARY
Zephaniah 3 in the HNT
Zephaniah 3 in the IRVA
Zephaniah 3 in the IRVB
Zephaniah 3 in the IRVG
Zephaniah 3 in the IRVH
Zephaniah 3 in the IRVK
Zephaniah 3 in the IRVM
Zephaniah 3 in the IRVM2
Zephaniah 3 in the IRVO
Zephaniah 3 in the IRVP
Zephaniah 3 in the IRVT
Zephaniah 3 in the IRVT2
Zephaniah 3 in the IRVU
Zephaniah 3 in the ISVN
Zephaniah 3 in the JSNT
Zephaniah 3 in the KAPI
Zephaniah 3 in the KBT1ETNIK
Zephaniah 3 in the KBV
Zephaniah 3 in the KJV
Zephaniah 3 in the KNFD
Zephaniah 3 in the LBA
Zephaniah 3 in the LBLA
Zephaniah 3 in the LNT
Zephaniah 3 in the LSV
Zephaniah 3 in the MAAL
Zephaniah 3 in the MBV
Zephaniah 3 in the MBV2
Zephaniah 3 in the MHNT
Zephaniah 3 in the MKNFD
Zephaniah 3 in the MNG
Zephaniah 3 in the MNT
Zephaniah 3 in the MNT2
Zephaniah 3 in the MRS1T
Zephaniah 3 in the NAA
Zephaniah 3 in the NASB
Zephaniah 3 in the NBLA
Zephaniah 3 in the NBS
Zephaniah 3 in the NBVTP
Zephaniah 3 in the NET2
Zephaniah 3 in the NIV11
Zephaniah 3 in the NNT
Zephaniah 3 in the NNT2
Zephaniah 3 in the NNT3
Zephaniah 3 in the PDDPT
Zephaniah 3 in the PFNT
Zephaniah 3 in the RMNT
Zephaniah 3 in the SBIAS
Zephaniah 3 in the SBIBS
Zephaniah 3 in the SBIBS2
Zephaniah 3 in the SBICS
Zephaniah 3 in the SBIDS
Zephaniah 3 in the SBIGS
Zephaniah 3 in the SBIHS
Zephaniah 3 in the SBIIS
Zephaniah 3 in the SBIIS2
Zephaniah 3 in the SBIIS3
Zephaniah 3 in the SBIKS
Zephaniah 3 in the SBIKS2
Zephaniah 3 in the SBIMS
Zephaniah 3 in the SBIOS
Zephaniah 3 in the SBIPS
Zephaniah 3 in the SBISS
Zephaniah 3 in the SBITS
Zephaniah 3 in the SBITS2
Zephaniah 3 in the SBITS3
Zephaniah 3 in the SBITS4
Zephaniah 3 in the SBIUS
Zephaniah 3 in the SBIVS
Zephaniah 3 in the SBT
Zephaniah 3 in the SBT1E
Zephaniah 3 in the SCHL
Zephaniah 3 in the SNT
Zephaniah 3 in the SUSU
Zephaniah 3 in the SUSU2
Zephaniah 3 in the SYNO
Zephaniah 3 in the TBIAOTANT
Zephaniah 3 in the TBT1E
Zephaniah 3 in the TBT1E2
Zephaniah 3 in the TFTIP
Zephaniah 3 in the TFTU
Zephaniah 3 in the TGNTATF3T
Zephaniah 3 in the THAI
Zephaniah 3 in the TNFD
Zephaniah 3 in the TNT
Zephaniah 3 in the TNTIK
Zephaniah 3 in the TNTIL
Zephaniah 3 in the TNTIN
Zephaniah 3 in the TNTIP
Zephaniah 3 in the TNTIZ
Zephaniah 3 in the TOMA
Zephaniah 3 in the TTENT
Zephaniah 3 in the UBG
Zephaniah 3 in the UGV
Zephaniah 3 in the UGV2
Zephaniah 3 in the UGV3
Zephaniah 3 in the VBL
Zephaniah 3 in the VDCC
Zephaniah 3 in the YALU
Zephaniah 3 in the YAPE
Zephaniah 3 in the YBVTP
Zephaniah 3 in the ZBP