Job 31 (BOGWICC)

1 “Ndinachita pangano ndi maso angakuti sindidzapenya namwali momusirira. 2 Kodi Mulungu kumwambako wandisungira zotani?Kodi cholowa changa chochokera kwa Wamphamvuzonse kumwambako nʼchotani? 3 Kodi si chiwonongeko kwa anthu oyipa,tsoka kwa iwo amene amachita zolakwa? 4 Kodi Mulungu saona zochita zanga,ndi kudziwa mayendedwe anga? 5 “Ngati ndachita zinthu mwachiphamaso,kapena kufulumira kukachita zachinyengo, 6 Mulungu andiyeze ndi muyeso wake wolungamandipo Iye adzadziwa kuti ine ndine wosalakwa, 7 ngati mayendedwe anga asempha njira,ngati mtima wanga wakhumbira zimene maso anga aona,kapena ngati ndachita choyipa chilichonse. 8 Pamenepo ena adye zimene ndinadzala,ndipo zomera zanga zizulidwe. 9 “Ngati mtima wanga unakopekapo ndi mkazi,ndipo ngati ndinalakalaka mkazi wa mnansi wanga, 10 pamenepo mkazi wanga aphikire mwamuna wina chakudya,ndipo amuna ena azigona naye. 11 Pakuti zimenezo zikanakhala zochititsa manyazi,tchimo loyenera kulangidwa nalo. 12 Ndi moto umene umayaka mpaka chiwonongeko;ukanapsereza zokolola zanga. 13 “Ngati ndinkapondereza mlandu wa akapolo anga aamuna kapena aakazi,pamene ankabwera kwa ine ndi milandu yawo, 14 ndidzatani pamene Mulungu adzanditsutsa?Nanga ndidzayankha chiyani akadzandifunsa? 15 Kodi amene anapanga ine mʼmimba mwa amayi anga si yemwe anapanganso iwo?Kodi si mmodzi yemweyo amene anatipanga tonsefe mʼmimba mwa amayi athu? 16 “Ngati ndinawamana aumphawi zinthu zimene ankazikhumba,kapena kuwagwiritsa fuwa lamoto akazi amasiye amene amafuna thandizo kwa ine, 17 ngati chakudya changa ndinadya ndekha,wosagawirako mwana wamasiye, 18 chonsechotu kuyambira unyamata wanga ndinamulera monga abambo ake,ndipo moyo wanga wonse ndakhala ndikusamalira akazi amasiye, 19 ngati ndinaona wina aliyense akuzunzika ndi usiwa,kapena munthu wosauka alibe chofunda, 20 ndipo ngati iyeyo sananditamandepochifukwa chomufunditsa ndi nsalu ya ubweya wankhosa, 21 ngati ndinaopsezapo mwana wamasiye,poganiza kuti ndinali ndi mphamvu mʼbwalo la milandu, 22 pamenepo phewa langa lipokonyeke,mkono wanga ukonyoke polumikizira pake. 23 Popeza ine ndinaopa kwambiri chiwonongeko chochokera kwa Mulungu,ndinachitanso mantha ndi ulemerero wake, sindikanatha kuchita zinthu zimenezi. 24 “Ngati ndinayika mtima wanga pa chumakapena kunena kwa golide wabwino kwambiri kuti, ‘Iwe ndiye chitetezo changa,’ 25 ngati ndinakondwera chifukwa choti chuma changa chinali chambiri,zinthu zimene manja anga anazipeza, 26 ngati pamene ndinaona dzuwa likuwala,kapena mwezi ukuyenda mwa ulemerero wake, 27 ndipo kuti mtima wanga unakopeka nazonʼkuyika dzanja langa pakamwa mozilemekeza, 28 pamenepo zimenezinso zikanakhala machimo oti ndilangidwe nawo,chifukwa ndikanakhala wosakhulupirika kwa Mulungu wakumwamba. 29 “Ngati ndinasangalala ndi kuwonongeka kwa mdani wanga,kapena kusekera mavuto pamene mavuto anamugwera, 30 ine sindinachimwe ndi pakamwa pangapotulutsa matemberero a mdani wanga kuti awonongeke, 31 ngati anthu amene ndimakhala nawo mʼnyumba mwanga sananenepo kuti,‘Kodi ndani amene sakhuta ndi chakudya cha Yobu?’ 32 Komatu mlendo sindinamusiye pa msewu usiku wonse,pakuti khomo langa linali lotsekuka nthawi zonse kwa alendo, 33 ngati ndinabisa tchimo langa monga amachitira anthu ena,kubisa kulakwa mu mtima mwanga 34 chifukwa choopa gulu la anthu,ndi kuchita mantha ndi mnyozo wa mafukokotero ndinakhala chete ndipo sindinatuluke panja. 35 “Aa, pakanakhala wina wondimva!Tsopano ndikutsiriza mawu anga odzitetezera. Wamphamvuzonse andiyankhe;mdani wanga achite kulemba pa kalata mawu ake ondineneza. 36 Ndithu ine ndikanakoleka kalatayo pa phewa langa,ndikanayivala kumutu ngati chipewa chaufumu. 37 Ndikanamufotokozera zonse zimene ndinachita;ndikanafika pamaso pake ngati kalonga. 38 “Ngati minda yanga ikulira monditsutsa inendipo malo ake onse osalimidwa anyowa ndi misozi, 39 ngati ndinadya za mʼminda mwake osapereka ndalamakapena kukhumudwitsa anthu olima mʼmindamo, 40 pamenepo mʼmindamo mumere namsongole mʼmalo mwa tirigundi udzu mʼmalo mwa barele.”Mawu a Yobu athera pano.

In Other Versions

Job 31 in the ANGEFD

Job 31 in the ANTPNG2D

Job 31 in the AS21

Job 31 in the BAGH

Job 31 in the BBPNG

Job 31 in the BBT1E

Job 31 in the BDS

Job 31 in the BEV

Job 31 in the BHAD

Job 31 in the BIB

Job 31 in the BLPT

Job 31 in the BNT

Job 31 in the BNTABOOT

Job 31 in the BNTLV

Job 31 in the BOATCB

Job 31 in the BOATCB2

Job 31 in the BOBCV

Job 31 in the BOCNT

Job 31 in the BOECS

Job 31 in the BOHCB

Job 31 in the BOHCV

Job 31 in the BOHLNT

Job 31 in the BOHNTLTAL

Job 31 in the BOICB

Job 31 in the BOILNTAP

Job 31 in the BOITCV

Job 31 in the BOKCV

Job 31 in the BOKCV2

Job 31 in the BOKHWOG

Job 31 in the BOKSSV

Job 31 in the BOLCB

Job 31 in the BOLCB2

Job 31 in the BOMCV

Job 31 in the BONAV

Job 31 in the BONCB

Job 31 in the BONLT

Job 31 in the BONUT2

Job 31 in the BOPLNT

Job 31 in the BOSCB

Job 31 in the BOSNC

Job 31 in the BOTLNT

Job 31 in the BOVCB

Job 31 in the BOYCB

Job 31 in the BPBB

Job 31 in the BPH

Job 31 in the BSB

Job 31 in the CCB

Job 31 in the CUV

Job 31 in the CUVS

Job 31 in the DBT

Job 31 in the DGDNT

Job 31 in the DHNT

Job 31 in the DNT

Job 31 in the ELBE

Job 31 in the EMTV

Job 31 in the ESV

Job 31 in the FBV

Job 31 in the FEB

Job 31 in the GGMNT

Job 31 in the GNT

Job 31 in the HARY

Job 31 in the HNT

Job 31 in the IRVA

Job 31 in the IRVB

Job 31 in the IRVG

Job 31 in the IRVH

Job 31 in the IRVK

Job 31 in the IRVM

Job 31 in the IRVM2

Job 31 in the IRVO

Job 31 in the IRVP

Job 31 in the IRVT

Job 31 in the IRVT2

Job 31 in the IRVU

Job 31 in the ISVN

Job 31 in the JSNT

Job 31 in the KAPI

Job 31 in the KBT1ETNIK

Job 31 in the KBV

Job 31 in the KJV

Job 31 in the KNFD

Job 31 in the LBA

Job 31 in the LBLA

Job 31 in the LNT

Job 31 in the LSV

Job 31 in the MAAL

Job 31 in the MBV

Job 31 in the MBV2

Job 31 in the MHNT

Job 31 in the MKNFD

Job 31 in the MNG

Job 31 in the MNT

Job 31 in the MNT2

Job 31 in the MRS1T

Job 31 in the NAA

Job 31 in the NASB

Job 31 in the NBLA

Job 31 in the NBS

Job 31 in the NBVTP

Job 31 in the NET2

Job 31 in the NIV11

Job 31 in the NNT

Job 31 in the NNT2

Job 31 in the NNT3

Job 31 in the PDDPT

Job 31 in the PFNT

Job 31 in the RMNT

Job 31 in the SBIAS

Job 31 in the SBIBS

Job 31 in the SBIBS2

Job 31 in the SBICS

Job 31 in the SBIDS

Job 31 in the SBIGS

Job 31 in the SBIHS

Job 31 in the SBIIS

Job 31 in the SBIIS2

Job 31 in the SBIIS3

Job 31 in the SBIKS

Job 31 in the SBIKS2

Job 31 in the SBIMS

Job 31 in the SBIOS

Job 31 in the SBIPS

Job 31 in the SBISS

Job 31 in the SBITS

Job 31 in the SBITS2

Job 31 in the SBITS3

Job 31 in the SBITS4

Job 31 in the SBIUS

Job 31 in the SBIVS

Job 31 in the SBT

Job 31 in the SBT1E

Job 31 in the SCHL

Job 31 in the SNT

Job 31 in the SUSU

Job 31 in the SUSU2

Job 31 in the SYNO

Job 31 in the TBIAOTANT

Job 31 in the TBT1E

Job 31 in the TBT1E2

Job 31 in the TFTIP

Job 31 in the TFTU

Job 31 in the TGNTATF3T

Job 31 in the THAI

Job 31 in the TNFD

Job 31 in the TNT

Job 31 in the TNTIK

Job 31 in the TNTIL

Job 31 in the TNTIN

Job 31 in the TNTIP

Job 31 in the TNTIZ

Job 31 in the TOMA

Job 31 in the TTENT

Job 31 in the UBG

Job 31 in the UGV

Job 31 in the UGV2

Job 31 in the UGV3

Job 31 in the VBL

Job 31 in the VDCC

Job 31 in the YALU

Job 31 in the YAPE

Job 31 in the YBVTP

Job 31 in the ZBP